No comment kwinako nditukwana kma you deserve award Mr game changer and 2025 Hassan kukhala president ndizasamuka ma Malawi basi votani moganiza a Malawi kwinako tizamwalira
RSA 😂😂😂😂 useless president answering about the prices of fertilizer in Malawi shame on you 😂😂😂😂 really chonde yikani makasu Anu Pasi, Chaka Chino cha 2024 😂😂😂😂 for now let's go and vote muzalima Chaka cha 2025 bwino pililani musafoke,musatope ,musawope you will never die with njala God he will make way for you just keep your vote in your heart ❤️ in Jesus name amen 🙏 believe me we are going to change the government soon, blood shedding, poverty, hunger crying 😂😂😂 they are going
Akuyakhula bwino kwabasi mosaopa Muthu mosanyengelela aliyese ❤
No comment kwinako nditukwana kma you deserve award Mr game changer and 2025 Hassan kukhala president ndizasamuka ma Malawi basi votani moganiza a Malawi kwinako tizamwalira
❤llllllllllllllllll
eeeeeeeee inuyo munabwera
komano kusiya zandare inuyotu mukukamba chilungamo mulungu azikutetezerani (yehova akupeweseni zoyipa zonse )
Amalawi otiudza akutiudza ndikutiunikira Koma Ngati tidzavotere Hassan chikangawa kukhala kidava ndipo tidzakhala pa mavuto adzaoneni
Game change more fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 makape a MCP ponyelela pa president ndi nduna zake akumpha mafiti oipa mtima ngati afisi
Ndimakunyadirani Mr game changer
Thwerenyenye, pangolin
I respect you Mr.
President chakwera si munthu koma ndi Fisi basi osamum era zomwe a MCP akunena ngati zonse zili bwino
Umakwana mbare game changer
Ndipo inu😢😢😢
Ndimakunyadilani game changer
Devaluation ikuchitikiramu basi wina mkumaganizanso zovotera chakwera? Nde kufoiratu
Zowona Game chenger
Pangolin❤❤❤❤❤
moti,kuchokela,pamenepaja,inuyo,lipoti,landege,simukulidziwa,ndiyeno,ngati,mumalidziwa,mumavomelelanji,kukhazikitsa,gulu,lofufu,mungozisiya,kumene,musatipusise,
9 of matter 1 of mind
tikamati,mcp,siyoyiseweletsa,mumayesabodza,ndikholo,lazipami,dpp,ndimwana,kwambili,olowela,pawindo
chakwela,sakuchoka,chifukwa,chazimenezo,mukunama,
kd,ndiwe,wakubanja,lachilima,iweyo,unali,patsogolo,kuthamangitsa,chilima,lelo,wakoma,,kupepha,mavoti,km,simuwina,
Zooonadi BG Inu dziyankhirani timAkunhadirani
❤❤❤
Uzavota kumene uliko kkk maloto achumba
Chikangawa
Fisi ndi fisi palibe chachilendo ndi yakupha basi
Muyambe kumanga akwa sudwe kd kuchira kuyakhura orakwa ndani kd kd tiziti kd mumanganiza mwana wa zake 5 akukupambanani kunganiza kd aMalawi mumawatenga zasatanic zopusa
Ambuye mutimenyere nkhondo patokha sitikwan8tsa
Athu tikulila njala nde titenga kt ndowa ya chimangayo 😂😂😂😂
km,zomatti,tizavotele,dpp,apa,ndiye,mukunama,tikudziwaso,kt,kabambe,ndiwa,dpp,mot,sangakhake,ndisapoti,yochuluka,ngati,yamanganya,manganya,ndidolo
mwakwana😅😅😅
timayembekezela,kt,unena,lipotilako,lenileni,ashiiiiiiiii
Ndingodikira APM boma alowe kuti akoze zinthu uyu simunthu chekwere ndikape olo mwana wanga antha kuposa zeru😂😂😂😂😂 ndikutitu mwana wanga womaliza kubadwa Atha kuposa zeru chekwera 😂😂😂😂
RSA 😂😂😂😂 useless president answering about the prices of fertilizer in Malawi shame on you 😂😂😂😂 really chonde yikani makasu Anu Pasi, Chaka Chino cha 2024 😂😂😂😂 for now let's go and vote muzalima Chaka cha 2025 bwino pililani musafoke,musatope ,musawope you will never die with njala God he will make way for you just keep your vote in your heart ❤️ in Jesus name amen 🙏 believe me we are going to change the government soon, blood shedding, poverty, hunger crying 😂😂😂 they are going
kuno,kumalawi,otsutsa,amawina,pakatha,zaka,26,isiyeni,mcp,idakusiyani,zaka26,ok
dpp,idalamulakale,boma,ndilomweli,sitikusintha
nangamunayambila,muja,lipoti,inuyo,mukudziwachilungamo,chake,bwanji,wosatsindika,pawailesi,kt,tikhulupilile,km,pa,,4n,ayi,,aliyese,athakula,,nkhulamomwe,angafunile,,kmawailesi,basi
Pangolin 🙏🙏🙏🙏🙏
Chakwera anapha Chilima chfukwa cha Conival basi
Game changer umakwana auze amenewo amanama kwambiri
Anthu opanda nzeru kukuwa koma sangachite kalikonse mantha okhaokha
Koma iwe Game changer Mulungu akuthangate mmoyo wako
😭😭😭anthu akugona ndinjala chimanga akachitenga kut
Palibe kumumanga musowa muyambe kumanga azikwanje ndi womwe anamphwanya ma galimoto a DDP mulungu akuziwa izi
One day is one day kuyankhura reality
Zachamba basi
Osamatchula mulungu pankhani zopusazo akulu mwamva!!!!!!!
Komadi amaneyu ndi President?
Katundu plus iponden fadah
tikavotela,mcp,
Pomwe zafikapa or chalwerayo alugonaso njara ndichifukwa akumayankhula zoduka mutu nanga angati tizigulitsa chimanga tichitenga kut
Since I was born have never seen a stupid leader like Chakwera.ukugona ndi njala ndiye ukatenga kuti zopusa zeni zeni
km,boma,sitikusintha,
Zoonad olakhula akuyankhula koma Pali ena ot akava zosez zimakhara kut zutulukila uko kwao ndikutsutsa koma please amalawi tisapangeso mistake kudzaikaso anthu awa serious tibwerera mu chipan chimodzi tsono musaiwale kut dziko lino ndilovutika ot kuika chipan chimodzi ichi kudza khara kovuta anthu kutukuka ndipo kugula ngakhare galimoto azikakufusa zambili mbili mwinas zidza khala ndiio okha bas ztsaz zambili tikuziona ndinthu ot tiyen tichenjele gaizi tisaipite zipan zina zomwe zbochitapo izii tiyen tikonde malawi uyu game changer akunena ambili akunena timoz Malawi.
Black box ili kuti itiuze zeni zeni
Very shallow thinking
Tikavota chikangawa watikwana
Aaaaa
This is DUMB!!!
Nkhan ya ndege tizaziwadi akachoka awa akuphawa
Munthu wopenga uyu
Kamtumbo Kako nawenso
Openga ndi amako
openga wamuonongela data yako openga ndiiweyo ukunvela zithu zaeni muli ndi phuma
@@MercyChiwaya-um6uskkkkk kom uko auze
Akanayankhul za Chimwendo km ndye kokhalirako mbeee wapenga ndi mwadxi wa Chilima nawes pj mulipo ambri
Ndimakunyadirani Mr game changer
Chakwera salibwino tiona ngati zisankho zikubwerazi ngati awine