KOMATU LAWYER UYU ANAYMBA BWINO NGATI AKUKONDA UTM NANGA ONANI WAULURASO ZOMWE CHILIMA ANAPANGA

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 16 ม.ค. 2025

ความคิดเห็น • 44

  • @chrisschikozera7271
    @chrisschikozera7271 15 วันที่ผ่านมา

    I love that song 🎵....God bless u my brother we need u more than everything

  • @ismailkaputen
    @ismailkaputen 20 วันที่ผ่านมา +1

    Mdima umadana ndikuunika
    Keep it up Big Man
    You are A HERO bro.
    Tikufuna anthu oopa Mulungu ngati inu man
    Tiyeni man Pangan zosangalatsa Mulungu osati Munthu.
    Munthu ndi oipa kuposa Mkango

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh 19 วันที่ผ่านมา

    More fire bro

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du 17 วันที่ผ่านมา

    Chilima pena pake anali opoyila amalawi mumakonda munthu akafa koma kufika pafundo chilima ndi yemwe anabwelesa mavuto amene amalawi akuona pano😢😢😢

    • @cathyjossam7804
      @cathyjossam7804 16 วันที่ผ่านมา

      Ndipo Ali moyo tikamuda

  • @mustafakasende-z3h
    @mustafakasende-z3h 19 วันที่ผ่านมา

    UTM is my party , sindingaisiye, UTM more fire

  • @JacobMsukwa-q6v
    @JacobMsukwa-q6v 20 วันที่ผ่านมา

    ❤❤ what is wrong is wrong no matter what party you belongs but am UTM since Chilima formed the movement 💪💪.

  • @lungisanishezi1023
    @lungisanishezi1023 20 วันที่ผ่านมา

    Anthu amadana ndi chilungamo koma adha awa ndi achilungamo❤❤❤

  • @AliNtolera
    @AliNtolera 18 วันที่ผ่านมา

    Yes

  • @stevenNgulube-g7r
    @stevenNgulube-g7r 19 วันที่ผ่านมา

    Iwe ndakatundu I'm with you bro kukhala ndi anthu 5 ngati iweyo bwezi ziko lathu lilipatali

  • @MosesDicostar
    @MosesDicostar 20 วันที่ผ่านมา +1

    Mmmm 4 hrs koma 7 comment eeee athu mwakwiya ndi chilungamo 😂😂😂😂😂😂 more 🔥🔥🔥🔥 kamangira

  • @LukaSaka-w4v
    @LukaSaka-w4v 19 วันที่ผ่านมา

    Uli munthu wachilungamo those tizafwa very good Lawyer pitiliza kulalika

  • @fanymatchumbuza6125
    @fanymatchumbuza6125 13 วันที่ผ่านมา

    Uyu akungonditopesano ine mweee

  • @EneyaManda-r1p
    @EneyaManda-r1p 20 วันที่ผ่านมา

    He means NO HORSE NO RIDER

  • @RaphaelWinford-t7u
    @RaphaelWinford-t7u 20 วันที่ผ่านมา

    Ndiwe chitsilu kwambiri, ndevu zosakukhalazo, we don't have time kumava za munthu yemwe anatisiya kale....

  • @ChrissieNyasulu
    @ChrissieNyasulu 20 วันที่ผ่านมา +1

    Polimbana ndi akufa pokhapo ndakutsika chifukwa sangakiyankhe

    • @SamKaposa-i5c
      @SamKaposa-i5c 19 วันที่ผ่านมา

      😂😂😂😂😂

  • @JohnChiyazu
    @JohnChiyazu 20 วันที่ผ่านมา +2

    Utm moto kut 🔥 📛

  • @HerlbertKaalis
    @HerlbertKaalis 20 วันที่ผ่านมา

    SKS akadakhala ndi Moyo akadayakha yekha Komano akulu zitaye pano UTM ili manja mwa kabambe ndeno muyembekezele kapena kuona zipatso Za UTM Mbali yake chifukwa ikudziwa Kuti mistake imodzi sadzakondedwanso

  • @ChristopherManase-s1f
    @ChristopherManase-s1f 20 วันที่ผ่านมา

    Uyu akunena zooona. Utm ili ngati njoka yomwe ayidula mutu

  • @YonaPearson
    @YonaPearson 19 วันที่ผ่านมา

    Iwe ndichisilu kwambili mutu ngati chigumu

    • @SamKaposa-i5c
      @SamKaposa-i5c 19 วันที่ผ่านมา

      😂😂😂😂😂😂

  • @RoyNyangulu
    @RoyNyangulu 19 วันที่ผ่านมา

    A lawyer awa ndiachisilu kwambiri
    Akuti Ali ndi masters koma according to what he is saying here the guy seem to be a bush lawyer.
    Am always trying to listen to what he is always saying koma I get bored of him because he never makes sense pa zomwe akuyakhula.
    Here he is talking about chilima were was he when chilima was still alive kuti aziyakhula chilima Ali Manda.

  • @MalekanoChikaonda
    @MalekanoChikaonda 19 วันที่ผ่านมา

    Zachamba izi

  • @IreenMwachande
    @IreenMwachande 20 วันที่ผ่านมา

    Koma pano zikhala zopanda ntchito because munthui anamwalira nanga tingaimbe mlandu munthu okufa koma zimenezi mukanazitulutsa ali moyo zikanamveka bwino palibe olungama pansi pathambo

  • @StuwartKaunda
    @StuwartKaunda 20 วันที่ผ่านมา

    Mcp ndi akulu akulu amayakhula modeka ngozi zayambila pachilima

  • @ElizabethKalonga
    @ElizabethKalonga 19 วันที่ผ่านมา

    Pali nzeru koma nkhani ya anthu andale opha anthu mukuti nayo bwanji?

  • @BisiyeleJanuary
    @BisiyeleJanuary 20 วันที่ผ่านมา

    Kabweletsan nkhani zanzelu avitsilu inu

  • @LukaSaka-w4v
    @LukaSaka-w4v 19 วันที่ผ่านมา

    Ngozi yinayamba ndi kale ndipo kulibe wamysya ndi Urdu yekha koma zavuta apa ndi ndale

  • @jumasingano1950
    @jumasingano1950 15 วันที่ผ่านมา

    Umakwa iweo

  • @daviechannel8603
    @daviechannel8603 20 วันที่ผ่านมา

    Mmmmmmmm

  • @YonaPearson
    @YonaPearson 19 วันที่ผ่านมา

    Iwe umwamwa tonjani wanji kupusako ndi ndevu zakozo ngati apositole

    • @SamKaposa-i5c
      @SamKaposa-i5c 19 วันที่ผ่านมา

      😂😂😂😂😂😂😂

    • @kennedybanda
      @kennedybanda 18 วันที่ผ่านมา

      🤣🤣🤣🤣🤣🤣

  • @EsnartNkhoma-m2c
    @EsnartNkhoma-m2c 20 วันที่ผ่านมา +1

    Paza UTM pokhapo ndakutaya

  • @ismailkaputen
    @ismailkaputen 20 วันที่ผ่านมา

    MA comment akadachuluka akakamba zotukwana /zolaula yerrrrrr Amalawi Shame

  • @yasiniKalonga
    @yasiniKalonga 20 วันที่ผ่านมา

    Is not good to talk bad things about someone who's gonna ,coz by the time u talk Allah is punishing his soul 😢😢😢😢where were you while he was alive???

  • @matherochanza6821
    @matherochanza6821 20 วันที่ผ่านมา

    Poor language and rubbish information.Exposing judicial corruption is making you growing wings.People already knew that corruption is even in all arms of the government

  • @emmanuelhassan-v1s
    @emmanuelhassan-v1s 19 วันที่ผ่านมา

    Useless guy, what kind of lawyer are u? U call it, u did masters. Mr I can’t see logic on u.

    • @felistassumani
      @felistassumani 19 วันที่ผ่านมา

      He is not useless. How useful are you? Introduce a topic of discussion so that we can follow you.

  • @cynthiakananji1608
    @cynthiakananji1608 15 วันที่ผ่านมา

    Sikut tingamangokumvera zonse,your not God.osalimbana ndi anthu okufa .osabakila chipani chaa anthu okupha