Ma zibusa anagulidwa ndi ndalama uphawi unakwana agalu achabe chabe pano anasiya kuyima pa choonadi ndalama basi zasokoneza mitu ma zibusa afake. Mukaphyaaaa zeni zeni.
Azi busa muopeni mulungu..onse amene anatenga gap pa imfa ya anthu awa mulungu akusanduseni masala pa dziko pano..akudalitseni..mulungu wathu ndi wamoyo
anthu ena akulu akulu akuyenera kumangidwa
Keep it up my brother ❤❤❤🎉
Remember that mulungu olenga kumwamba ndi dziko lapansi anali komweko kuchikangawako i insist and God is watching us from a distance
Ma zibusa anagulidwa ndi ndalama uphawi unakwana agalu achabe chabe pano anasiya kuyima pa choonadi ndalama basi zasokoneza mitu ma zibusa afake. Mukaphyaaaa zeni zeni.
@@chitanibenito1109 opemphera koma osati enieni
Nkhangaaaaaaaa Zaonaaaaaaa Mcp God is watching palibe chomwe mungachite nkhutheka😂😂😂😂😂😂😂 Mizimu yakwiya just know kuti 2025 paulendooooo
Azi busa muopeni mulungu..onse amene anatenga gap pa imfa ya anthu awa mulungu akusanduseni masala pa dziko pano..akudalitseni..mulungu wathu ndi wamoyo
Munthu ndi Namiwa basi osati zigawenga zothawira mutchire inu mukulakalaka uchifwamba basi.
Amene mitu yawo ikuyenda amakudziwani bwinobwino
Ntanyiwa, munanena kuti ikatuluka report mudzatulutsa lanu. Tulutsani lanu lija
Iwe ndiwe ukuwononga malwi ndi maliport anuwa aboza nthawi zonse kumangosusa z chilichose chomwe boma lingachite
😂😂😂😂😂
Pa nyapawo azibusawo
Agalu achabe chabe asatinyasepo apa ndi kupha ndi kuba kwawoko
Zazii akagwere ukoooo a chikangawa zabodza basi
Koma anthu muli ndi vuto,kodi report likhale ndendende chimene mukuganiza inuyo?
Anthu ambiri adziwa tsopano kut wosokoneza wamkuru ndinuyo kuposa enawa.
Not interested in listening to the lies in the so called report. Mabodza okhaokha
Chakwera watijayira kwambiri ngt ndiamene anatilenga
Am not convinced with the report at all you're not telling us the truth
God will vindicate Himself and He will judge himself
The one who is responsible for this tragedy