NDE MWATI KUKUTULUKA REPORT? BOLA KUKAMBIDWAKO ZAMZERUTU

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 17 ธ.ค. 2024

ความคิดเห็น •

  • @ShabilKamwendo
    @ShabilKamwendo 3 วันที่ผ่านมา

    SKC ndi munthu osalakwa ndipo chakwela ngakhale mwapeleka ndalama zoti zikubiseni koma Kwa mulungu kulibe chisisi.ndipo zonse zomwe munapanga mulungu anali pomwepo koma one day is coming

  • @BusaGaniza
    @BusaGaniza 3 วันที่ผ่านมา

    Ndidzakhulupilira kuti ndiloona ngati wina atamangidwa kapena kuchotsedwa pa udindo

  • @ShabilKamwendo
    @ShabilKamwendo 3 วันที่ผ่านมา +1

    Kodi chakwela zako uja anakulakwila chani ? Ku court kosekuja zoona kumupha munthu chifukwa cha ngwilizano yosithana term.

  • @PHILLIPMmwenye
    @PHILLIPMmwenye 3 วันที่ผ่านมา

    Chakwela munthu oipa kukampitisa saulosi chilima iwenso umusata sure

  • @stevenmwamadi3035
    @stevenmwamadi3035 3 วันที่ผ่านมา

    Chakwera unamupha nzako uja chifukwa chani koma iweyo chakwera mulungu Ali nawe mpaka umusata nzakoyo muthu iweyo chakwera ndi muthu oyipa unamupha nzeru nzako chifukwa cha mando thawi ndi nyengo ikwana kuti iweyo zako zida pompano