Komanso ngati kuli kupindulira ,Amapindula ndi Chakwera ndi Kagameyo, komanso Chakwera anagulitsa anthu kale kale ,ndi chifukwa chake alibe nazo ntchito kufa kwa anthu ,zikufunika asilikali anthu amukanire Chakwera ,chifukwa anthu akumasiya ma banja awo ma dzuwa ,ndalama zimene amapereka kwa asilikali ndi ma cent chabe ,Chakwera ndi Kagame akudya ma bilion
Palibe ubwino wake pamene anthu akumwalira Ku banja lawo amphindulanji pa izizi Achakwera asatitenge ife ngati opepela iyayi Mbuzi ya munthu Chakwerayo mumuuze

Bro apa mwayankhula zomveka inenso zimandidabwitsa kuti chakwera ndi gagame akutipanga chiyani pamenepa
Komanso ngati kuli kupindulira ,Amapindula ndi Chakwera ndi Kagameyo, komanso Chakwera anagulitsa anthu kale kale ,ndi chifukwa chake alibe nazo ntchito kufa kwa anthu ,zikufunika asilikali anthu amukanire Chakwera ,chifukwa anthu akumasiya ma banja awo ma dzuwa ,ndalama zimene amapereka kwa asilikali ndi ma cent chabe ,Chakwera ndi Kagame akudya ma bilion
DRC Nkhondo nja kale kale chotumizira a silikali ndi chani? Utchuke iweyo Chakwera?
Mafutso abwino kwambili chifukwa asilikali athu amangogwilisidwa ndi ntchito opindula ndi omwe ali kusogolo
@@AbdulJohn-t7l amapezapo ma 20mita
Kodi ayamba kupita mulamuliro wachakwera? Nthawi yoseyi simumafunsa chifukwa chani? Born kalindo iweyo ndichitini chopanda kanthu. Ndimkakuvetsera koma mmmm utichedwetsa
Palibe ubwino wake pamene anthu akumwalira
Ku banja lawo amphindulanji pa izizi
Achakwera asatitenge ife ngati opepela iyayi
Mbuzi ya munthu Chakwerayo mumuuze
Ma million mesa
Ndipo no benefit at all kumangophesa anthu
Izizi azisiye ndipo palibe ubwino
Mafuso km opanda yankho😢