Koma awawa kuyankhula kot akafika pamalo minimum ndi 31years guilty conscious sikuwagwila komwe aliko?zimachita kuoneswlatu kut Biyeni samawafuna kuyankhula ngat mawa kulibe...sine wa ndale koma MCP ikudzipanga decompaign yokha..the economy is bad no wonder mayiko ena ukamacheza nawo anthu Ake amangoti Ku Malawi kosauka..shameeee dziko longokhalila ngongole silingatukuke zilingati mamuna okonda katapila
Akulu akulu Mary Chilima and all malawians of good will deserves better. Inuyo tangoganizani: 1 Ndege yopanda blackbox kumukweza VP wa dziko. 2.Ndege yopanda recorder, no any communication koma yanyamula Vp. 3.Ndege yokugwa 10am kusaka kukayamba 5pm, zoona izi?? 4.VP sanapezeke, koma kukaimisa kusakidwa kwake zoona?? Kodi zomwe zinachitikazi olo ali Chakwerayo olo mwana wake, akanakhutisudwa nd report ya German ija?????
Bakili muluzi tv is here ndipo zisakho zikawandikilamo chonde bwanawathu pofunika ma software otse ndima computer 🖥 azakhale m'manjamwanu muzizatiwuza mene zizizakhalira
Gotani Hara Chimene munamanga ndi Chimenechotu. Munamanga Kuti muphe Chilima ndipo munaphadi . M H S R I E P ✝️ ✝️✝️ VP SKC. Chakwera munthu Woyipa Chikangawa Party 👹⚒️🐊🐊🐊⚒️👹 Banja la mzako lili pa umasiye chifukwa cha Mtima wako wa Ng'ona. Unaphera CHILIMA Udindo. God will punish you Lazalo Well done Brother from BAKILI MULUZI TV Stay blessed 🙏 Stay safe ✊✊ Fight for the better Malawi ✊ ✊✊. God bless you Brother . Good work: Unforgettable moment : 10 June 2024 CHIKANGAWA MZUZU
Kkk monicachakwera alipo mankhwala akuti kumeneko kwakoko kozizirako kuzikoma..ukafunse azimai a kuchiradzulu distruct ndi thyolo ndi zomba district and mulanje and phalimbe districts and machinga and mangochi districts . akugulitsa ndipo a chikangawa wo sadzapitanso kwa Vera kantukule ndi mai yolamu..kenakio ungomupusitsa chikangawayo akhale bambo " Nanyo " kuti asamaphensi anzake kkkk uchitatu sieti mònica
Osamangoyankhula pa social media pano ngati ndife mbuli krausi chilima convinced us to get this manyaka and now it's our own time to change the goals of our children 💪💪💪💪
Manganya anamupeleka Chilima kuti aphedwe, anaulula kuti they were about to end aliance ku MCP then zinapangitsa kuti kasambala aphedwe ili trap yopha Chilima. Izizi ndili ndi umboni koma kuti ndiwasumile andimanga popeza ali m boma
Kwa ife amene timslowa pa TH-cam just to check if bakili muluzi tv has posted let's gather here
We here
Apoooo💥💥💥💥
1:29 1:29 1:48 1:48 1:52 😊😅a@@BobChibwana
Musamasowe koma a Braz, TH-cam is boring without kumvera BAKILI MULUZI TV.
Live boss Ife timava kukoma chifkwa inuy
BAKILI MULUZ TV FANS LET'S GATHER HERE ❤
God will revenge
Kupanda chilima agalu awa sitikanawa votera
Chakwera ngakhale atatumbwa motani adzafa basi ...or atamuonjezera zaka 1000000 adzaduduluzidwa pakhosi ...satana wachabechabe
Brother musamasowe chonchi tikudalila inu kutidziwitsa zomwe dziko lanthu likuyendera respect boss❤❤❤❤❤
Bakili Muluzi tv fans lets gather here
aaa Malawi tinapusa kwambili 🤦🙆🤦🙆🤣🤣🤣🤣🔥
Amene timati chakwera mchikangawa let's gather her
Muno masanje ayi ndipo likoma sitikugulitsa,, gulitsani central region mukapeze kokhala
Koma awawa kuyankhula kot akafika pamalo minimum ndi 31years guilty conscious sikuwagwila komwe aliko?zimachita kuoneswlatu kut Biyeni samawafuna kuyankhula ngat mawa kulibe...sine wa ndale koma MCP ikudzipanga decompaign yokha..the economy is bad no wonder mayiko ena ukamacheza nawo anthu Ake amangoti Ku Malawi kosauka..shameeee dziko longokhalila ngongole silingatukuke zilingati mamuna okonda katapila
kamajekete salephera kumutchula umva ka ma jeket 😅😅😅😅😅
😂
Chakwela ndamene adapha Chilima amalawi osapusitsika kumaona momwe palili pa ground, Chakwela ankamuzuza Chilima uja and ankati sakuimaso 2025.
Osafusaso umboni wina
Chakwela aimbidwe mlandu wa murder anapha chilima.
Ndimaona ngati Gotani Hara ali ndi nzeru koma ndi chibekete chodontha ngati a china kamajekete
😂😂😂😂😂😂😂
❤❤❤❤first comment here gather all as l love BAKILI TV
Ndipo live bigy tinakusowani ❤
Amalawi ndi anthu abwino osangomuwombela bwanji chakwelayu
Kom chikangawa forest
As malawi we always appreciate u bro u have open all the hidden things in Malawi
Inuyo ndi big bwana! Ulemu wanu!
umakwan bakili muluzi tv 📺 ❤❤❤❤
Akulu akulu Mary Chilima and all malawians of good will deserves better. Inuyo tangoganizani:
1 Ndege yopanda blackbox kumukweza VP wa dziko.
2.Ndege yopanda recorder, no any communication koma yanyamula Vp.
3.Ndege yokugwa 10am kusaka kukayamba 5pm, zoona izi??
4.VP sanapezeke, koma kukaimisa kusakidwa kwake zoona??
Kodi zomwe zinachitikazi olo ali Chakwerayo olo mwana wake, akanakhutisudwa nd report ya German ija?????
Answer is there 😢
Indotah yami ubuyile manje🎉 ngiyabonga sakuazah buthih😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😅😅😅😅
Mai malemu chilima mmmm waondatu amalawi let be together with mai mery chilima
All the time best Bakili Muluzi TV Boma lopanda Chilungamo ngati limeneli silinaonekepo aluza kale chisankho achoke
Welcome back bwana, timakunyadilani.
You are talented guy no matter now you're attacking politics and attack them bro truth shall never perish
Malawi kungonkgala ngat atidyesa mankhwala atulo abale satana akuyendela chakwera ndiwaphavu kwambili
God's watchmen Bakili Muluzi Tv
Mang'anyanso nde Kaya akuti Mulungu wadalitsa iiìiiiii. Koma abale 😅😅😅😅😅 Manganje kugudika nawo Amalawi musatengeke.
kung'alura osaopa iyayi,ife pambuyo pano
M'dima ungakule bwanji kumacha
Bakili muluzi tv is here ndipo zisakho zikawandikilamo chonde bwanawathu pofunika ma software otse ndima computer 🖥 azakhale m'manjamwanu muzizatiwuza mene zizizakhalira
Adolo awawa or atayamba campening kutasala one day yovotera. Titha kukuvoterani tose tikuonera this channel ❤❤
Am sure kuti plan ya ndege ija anthu ambiri a mcp amaziwa 😢but what I like mulungu anati every soul shall test dieth 😭 no matter what
Tinanzipha tokha ku votera. M. C. P. Tiyeni mifuti nafenso tikaphe akulu akulu a. M. M. P
Chipani chakupha cha mcp .kupha anthu 9 simasewela bakili muluzi ananena kale kuti ndichipani chagazi .amalawi gotani hara ananena kale kuti mcp yikuyenera kupitiriza kukhesa mwazi kuti yipitilire mpaka 2030.si uyu chilima wapelekedwa nsembe pamodzi ndi anthu 9.ofunika amalawi tisamale ndi mcp chipani chakupha chagazi
Bakili muluzi TH-cam channel is back to basic let's gather together!!
Ndale sikumphana kodi a MSP mudakhala bwanji kungongala ndi ntima wakumpha basi eish 😢😢😢😢
Kma anthu awawa samachilapa bwanji everytime misampha Yao ikungoulurika kma ndithu anthu opanda manyazi osasintha kti mwina nkutinamiza ndi tizitukuko kma eeee Mulungu tiomboleni nanga mafuta aja anakalandira ku Nsanje aja iii
Kkkk chibwana chimalanda mulungu anavomeleza zofuna za akumalawi posankha MCP anthu ngati sasamala ndikuthawila kwa mulengi wawo akhala m,mavuto oposa amenewa
Ngati sindinavele bakili muluzi tv sindimava bwino chonde musamasowe❤
Aaaa osamadabwa ngati akuchedwetsani dziwani kuti ochedwesayo ndiamene anapanga zimenezoyo
History is best teacher ❤
After longtime no lisen so am suffering toomuch. God bless you brother
Popeza Amalawi sitichedwa kuiwala tikavotele mcp so kachiwiri
Gotani Hara Chimene munamanga ndi Chimenechotu. Munamanga Kuti muphe Chilima ndipo munaphadi .
M H S R I E P ✝️ ✝️✝️
VP SKC.
Chakwera munthu Woyipa
Chikangawa Party 👹⚒️🐊🐊🐊⚒️👹 Banja la mzako lili pa umasiye chifukwa cha Mtima wako wa Ng'ona.
Unaphera CHILIMA Udindo.
God will punish you Lazalo
Well done Brother from BAKILI MULUZI TV
Stay blessed 🙏
Stay safe ✊✊
Fight for the better Malawi ✊ ✊✊.
God bless you Brother .
Good work: Unforgettable moment : 10 June 2024
CHIKANGAWA
MZUZU
Anthu oipa awa ndi amene anapha anthu ose aja anali mu ndege komanso anapha Mia
Zaka 31 galu iwe kukamwa ngati konyera bakha
Bwana munasowa 😢 musamasowe chonchi pilizi 😮
Akutitu musamale akutelo kamasaya Billy malata
Big man watulukira sopan
😂😂😂😂😂MG 2 ndi blesser😂😂😂
Ipondeni Fadah 💥🔥
Mhunu vakashata but Mwari ariko.
A zibabo🎉🎉🎉🎉🥰🥰🥰🥰
Ulemu wanu bro❤❤
Achimwene musamasowe
MCP chipani chamagazi
Mg2 yo kodi mmodzi yekha .!!? Vera kamtutukule.ndi Mary yolamu..kkkk kodìonicayo alibe nsanje ? Kumamudyera kudya kwake iyeyo ali pomwepo ? 😮😮😮😮😮
Brother Bakili Muluzi tv and Comrade ntanyiwa may almighty God continue to bless and protect you wherever you are ❤❤❤❤❤❤
2025 ikuchedwa kiufika kuti tichose Boma lopanda Chilungamo ndi chifundo Bakili Muluzi TV 🔥🔥
Brother wa Bakili muluzi TV. ifetu timakukondani kwambiri kotero ife tinali tikudandaula nditu ... Mulungu akudalidzeni nditu kwambiri..❤❤❤ the best history.
Adala inuyo musadzafe mudzango kusowa,eeh koma awonekela poyela chakwela, fiti yamuthu kubisa brack box ,mkumapatsa ndalama woumba,alibe zelu ,local Mozambique
If I buys bundle..it's bcz I love this channel...God protect you Bakili TV
CHAKWELA nd muthuu wakuphaa anamuphaa CHILIMAH ndpo anamuphera u dindo CHAKWELA ngwaa kuphaa ndthuu
Kkk monicachakwera alipo mankhwala akuti kumeneko kwakoko kozizirako kuzikoma..ukafunse azimai a kuchiradzulu distruct ndi thyolo ndi zomba district and mulanje and phalimbe districts and machinga and mangochi districts . akugulitsa ndipo a chikangawa wo sadzapitanso kwa Vera kantukule ndi mai yolamu..kenakio ungomupusitsa chikangawayo akhale bambo " Nanyo " kuti asamaphensi anzake kkkk uchitatu sieti mònica
The best TV only we have in Malawi BAKILI MULUZI TV keep up updated osawopa until chikangawa chibwele poyela
Thank you BMTV
Chipani cha MCP tikuchithetsa mdziko muno ndipo akanganya onse awa alowa ku ndende.
Keep this screenshot.
Ulemu wanu Big man.Manganya ndi Iscariot kumene.Adagulitsa ndi kupereka Chilima ndi Kasambala komanso miyoyo 8 ina ija.
Vuto ndife amalawi, timavela anthu omwe ali kudyelera dzikoli anthu ochepa okha omwe ali pafupi ndi president, iwe akudya money, akukhuta ,akumwa tea ,komanso akuyendela magalimoto apamwamba, koma ife osauka ,ovutika ,osowa ,anjala, ausiwa ndipo ndife ma millions ya anthu tikuvutika palibe chomwe boma mkutibela tikamalira ,boma likubweleka ndalama zochuluka mmaiko akunja mmalo mothandiza dziko ndi anthu omwe tikuvutika ndipomwe iwo akugawana okhaokha ife mkumapitilira kuvutika, koma tili buzy kumavelabe iwowo, zachisoni kwambiri pano akubwela ndi plan yobela zisankho mkumati tiyeselele kkkķkkkmk amalawi ndife ovetsadi chisoni, zomwe tikupangazi ndichimomodz bambo ndioledzela akagwila ganyu amaiwala kuti pakhomo pali njala yonse amakamwela mowa ,mai akagwila kut akagule ekha chakudya akupatsanso bamboyo kut akamwele mowa mkumalilabe pomwe tikuchita mwadala, kuvotelanso mcp . Ndipo kudzaliranso mtawina mcp palibwino adzangootcha dzikoli chifukwa tilibe mzelu, tikuvela chimwendo banda, tikuvela kunkuyu, tikuvela zikhale ng'oma anthu ochepa zoona akufuna tiwapatsebe mwai omatizuza chonchi.
Our history teacher, Mr Bakili Muluzi TV we always appreciate you for teaching us and always stand for your people Malawi big up Bakili Tv.
Awa ndiakutundu ....kulankhula ma live okha okha ....check n arrest but no where to be seen ....still releasing the fame.
Kapena kukoma kunatha..amangozizira .amai nonica chakwerawo kkkk.ndiye bola kufa .nanga ena azikudyera kudya kwako iweyo uli pomwepo...kumeneko.
Koma siboza ai president chakwera akuziwapo katu pa infa ya chilima ndine wakuzambia siboza ai yehovah mulungu wamakamu akuona tidikile kaya bwanji
May God forgive us....our willingness for change costed us what we couldn't afforr to lose.
Mukapeza wa MCP aliyense mupheni ndipo palibe mirandu iliyonse.
AMBUYE tichitiren chifundo dziko lathu 🙏😭😭😭😭😭
You always gather real facts before talking that's why am always trusting your source man. Keep up the good work
chilima adandimema kut votele chilombo aas😭😭😭😭😭 ndikadadziwa sakadayiona yang vot Koma mulungu yekha amuonetsa
Kwathu ndikulira kuilira mizimu yonse ija9,Ambuye aulura zobisikazo
Koma zobela zisankho 2025 nde muiwale ndipo ife sitingalole zachibwanazo munya muona anyapapi
Timakunyadiran mupitirize kumatipasa zosiyana siyana tiziziwa zochitika zamayiko azathuwa kuti kurinj
Timakunyadiran mupitirize kumatipasa zosiyana siyana tiziziwa zochitika zamayiko azathuwa kuti kurinj
Ladies have a heart, don't just utter your words b4 you think, remember time changes everything, fear the time mama
Osamangoyankhula pa social media pano ngati ndife mbuli krausi chilima convinced us to get this manyaka and now it's our own time to change the goals of our children 💪💪💪💪
Mtendere sitiupeza chifukwa ana aja sanali anthu wamba😢😢😢😢😢😢😢😢
Achilima ngwilizano unawaphetsa koma nthawi mkachitsiru chilungamo chizawoneka
Manganya anamupeleka Chilima kuti aphedwe, anaulula kuti they were about to end aliance ku MCP then zinapangitsa kuti kasambala aphedwe ili trap yopha Chilima. Izizi ndili ndi umboni koma kuti ndiwasumile andimanga popeza ali m boma
But why chilima😭😭😭adalakwanji mhsrip but God knows 😢😢
Tiyeni tingopanga za azanthu ku Kenya ,tiyambile pompano pa social media kupanga mademo keneko tikathele pamusewu , osakatengaso chilolezo
Pamalo 31 years, Really? Malawi is a democracy country, get it!!!!
Thanks for the update we have been waiting for this continue to give us the best analysis of what is happening around the world
Best TV bakili muluzi my Brother congratulations ❤
This people they must get under arrested in 2025 they made Malawians poorest than any country
Dziko ndilawathu dzaka 31 dzambwiyu 2025 mukuchoka mwatikwana agalu inu tikufuna umboni wa chilima
Zoonadi brother these are useless Government and they are criminals MCP ndi chipani chasatana
Ine chomwe akfuna anthu awawa sikuchiziwa 😢kodi ndlama zonse zomwe abazi akadyela kut God have in this country
Iwe kukhara mobisara mpaka liti wa bakili iwe chifukwa MCP m boma sichoka ase becare 😂😂😂😂😂
Eish zopasa mantha komaso zolilisa zomwe Inu amcp mudapanga koma nthawi nkachisiru tionana 2025