Momwe akuyankhulira uyu atha kusakidwa ndi boma paja sakumachedwa kutseka anthu pakamwa

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 17 ก.ย. 2024

ความคิดเห็น • 4

  • @funnynyirendafunny7888
    @funnynyirendafunny7888 3 วันที่ผ่านมา

    Zowona zake 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 usi be careful ziwa bola umziwe chomene ukupanga. Ukanaziwa ukana menyana ndinkhondo ya Malawi mmene akulilira . Ziwa zimezo

  • @gracem-y8p
    @gracem-y8p 5 วันที่ผ่านมา

    Zazii

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 3 วันที่ผ่านมา

    USI SAMALA POSACHEDWA UTHA KOLONDOLA CHILIMA UJA UNAMPEREKA KWA CHAKWERA

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 3 วันที่ผ่านมา

    BULISHILI SANAFOTOKOZE MWACHINDUNJI AI WAMUZUNGULILA CHAKWERA KAFOTHOKOZEREDWE KAZIMENE CHAKWERA WAKUMANA NAZO NKHANI IKUKHUDZA CHAKWERA MUKAVETSETSA BWINO BWINO KWINAKO IKUWONETSA KUTI CHAKWERA ALI PAVUTO LALIKULU CHIFUKWA WAZEZA ANTHU NDIPO ANTHU SALEKA KUGENDA CHAKWERA NDI USI ANTHU AWILI AWA ALIPAVUTO NDI AMALAWIAN ASANALE