ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Why do they pretend to be drinking something from the cup?
Oohh yah😂😂
That's what I was wondering abale inu
Real wahala amwene kuzunzana
😂😂😂
😂😂😂 I don't understand bro
Makosana we love you so much but stop this thing chomawapasa anthu ma empty cups if Pali vuto la ndalama let me donate nyika for the artist zikomo
😂😂😂😂😂😂
Mu cup mulibe ngat nothing 😂😂😂😂
Prince 🤴 ndiwama senjekabi muchi sena
Abwera ngati coming
I love this channel 🤩🤩🤩
Ka v force ndi kobalalika kkkkkk ndakaona lero Kachepetse kubanda
Invest in good audio
Nde akumwa chani😂😂
Makosana Kodi ndi mtundu wanji wa mphepo mukuwamwetsa anyamatawo?
Why just bring empty cup osapasa zokumwa bwanji
Mumakapumotu mulibe nothing 🤣🤣🤣🤣
Kod maNyooo mu Cup muli chan😂😂I don't think muli kathu
At least Super Dip or Water munaikako tumbler, not drinking air like that,😏
Mukanaapasa mic
☺☺☺☺ ma disposable cups muchita kuoneka kut mulibe kanthu
Simadolo!
V force ndimfana ovutirapo ndamuona kkkkkkk kod kali std Chan kameneko 😂😂😂😂
Bola mu cup mo olo mukanangoyikamo madzi😂😂
Voice inali pasi yamafana than iweo host komaso empty cup Bora munakawapasa ka banks but I know kuti zithu zakwera mtengo🤣🤣🤣🤣nice makosana
You giving kids cups commonly known for saving alcoholic beverages?
Empty cups osangowasiya pasi bwanj🤣
Kodi mu tambulamo mumakhala chani? Hiboooo!!!
Zakumwazo ma gyz sizimatha mutambulalamo
Koma ndiyedi kkkkk
Nanji manejayo... Form form yake inayenda koma? Angawalangize anawa zotan?
Cardinal muli Chan mma tumbler mo
Aaaaa guys anawa olo chabwino munakayikamo madzi mu cup mo
There's nothing In the cups ...what's wrong with you people 😅😅😅😅
Mmakapumo mulibe kalikose... Whats the point?
V force akusilira cup🥤
Zachimidzi
this is too much ...makapu opanda kantu ndee chani. kusoowa dollar bwanji..it's better mungoyikamo madzi rather than kumwera mu kapu a empty
Why do they pretend to be drinking something from the cup?
Oohh yah😂😂
That's what I was wondering abale inu
Real wahala amwene kuzunzana
😂😂😂
😂😂😂 I don't understand bro
Makosana we love you so much but stop this thing chomawapasa anthu ma empty cups if Pali vuto la ndalama let me donate nyika for the artist zikomo
😂😂😂😂😂😂
Mu cup mulibe ngat nothing 😂😂😂😂
Prince 🤴 ndiwama senjekabi muchi sena
Abwera ngati coming
I love this channel 🤩🤩🤩
Ka v force ndi kobalalika kkkkkk ndakaona lero
Kachepetse kubanda
Invest in good audio
Nde akumwa chani😂😂
Makosana
Kodi ndi mtundu wanji wa mphepo mukuwamwetsa anyamatawo?