LYTON MANGOCHI KUTIMIZA UTHENGA KWA CHAKWERA KOMANSO WAYAMIKILA BAKILI MULUZI TV AND MTANYIWA

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 16 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 32

  • @ChimwemweMathyola
    @ChimwemweMathyola วันที่ผ่านมา +1

    Mangochi ndiwe one ❤❤❤

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 วันที่ผ่านมา +3

    Zikomo big man ulemu wanu MCP yatikwana iyi

  • @chimzywyson2842
    @chimzywyson2842 วันที่ผ่านมา +1

    Amangochi osafookatu chifukwa pano nde muli ndi nzelu za bwino kwa mbili❤

  • @EmmanuelNgambi-y6h
    @EmmanuelNgambi-y6h วันที่ผ่านมา +1

    Mbambande 🔥

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu วันที่ผ่านมา +1

    Menya brother amvetse, Chakwera palibe chimene akuchita

  • @SelinaGamaliyere-q8v
    @SelinaGamaliyere-q8v วันที่ผ่านมา +2

    Chimwendobanda uzafangati galu

  • @FredKanyerere
    @FredKanyerere 18 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Comrade true.

  • @CharlesBande-yr1yb
    @CharlesBande-yr1yb วันที่ผ่านมา +3

    Chonde musanyengedwenso ndi ng'onazi chonde

  • @Elson-cf1gy
    @Elson-cf1gy วันที่ผ่านมา +2

    AMangochi takunya dilani m b tv tanyuwa A D C teyenawon zatikwana ng'ona zimenez

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 วันที่ผ่านมา +2

    Kodi za nsewu wa kumakanjila adzikawodza anthu aku BT chabwino ena anachokela komweko ku mangochi chipitile patenga nthawi amva chani amenewo nde mabodzwo ngati mufuna kunena za ku zomba pitani komweko mudzikalodza minsewuwo atsati muli ku mulanje kumanena za ku salima AAAA ANTHU SANGAKUMVELENI AYI UCHISILU WA MCP UYU ANTHU OLEPHELA AWA AKUDALILA KUBELA VOTE KUMATU KUDZACHEMA KU MALAWI CHIFUKWA ANTHU AMBILI SAKUFUNANI A MCP NDE MUSAMALE

  • @JamesLongwe-qz9fd
    @JamesLongwe-qz9fd วันที่ผ่านมา +1

    Apa ndiye mukuyimilira amalawi osati kumabakira boma loyipa la MCP

  • @DalitsoMatope
    @DalitsoMatope วันที่ผ่านมา +2

    Panotu tinzeru tikubwera

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole วันที่ผ่านมา

    🔥 fire lyton mangochi ❤❤

  • @emilynthite6545
    @emilynthite6545 วันที่ผ่านมา +1

    Mcp mulibemo utsoreri angakhare nduna zimene ndi mbuzi zokhazokha

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 วันที่ผ่านมา +1

    Mutu wayamba kugwila ntchito tsopano

  • @OsmanChisi
    @OsmanChisi วันที่ผ่านมา +1

    Koma lyton usapangeso zopusa Ngati umafuna zija Kuti utenge ndalama Ku MCP basotu

  • @MathiasJoseph-xv1hj
    @MathiasJoseph-xv1hj วันที่ผ่านมา +1

    Mangoch umachedwapat kulankhula ndikumeneku

  • @TomasDzifoole
    @TomasDzifoole วันที่ผ่านมา +1

    Apandiye bolani.

  • @EsetaGerate
    @EsetaGerate วันที่ผ่านมา +1

    ❤❤❤ mangochi 😂

  • @GestardKamanga-r7w
    @GestardKamanga-r7w วันที่ผ่านมา +1

    Pitilizani amangochi kutisegula kumaso takunyadilani

  • @CharlesGremu
    @CharlesGremu วันที่ผ่านมา +1

    Umatha

  • @maxwellchifupa1538
    @maxwellchifupa1538 วันที่ผ่านมา +1

    Hit the nail brother

  • @pierregondwe1096
    @pierregondwe1096 วันที่ผ่านมา

    Anapha track azimayiwa eeh

  • @MosesTangwe
    @MosesTangwe วันที่ผ่านมา +1

    Nsampha waning'a MCP munya muona

  • @ThivadoartistDyson
    @ThivadoartistDyson วันที่ผ่านมา +1

    Panopa amangochi tikukunyadilan

  • @WarriorKB-u3k
    @WarriorKB-u3k วันที่ผ่านมา

    A Lyton tili pambuyo panu osaopa malawi ndiwathu zoona anyamata amenewa ife timawakonda ndipo mlungu awapatse moyo wautali akutimenyela nkhondo zabwino kwambiri APM oyee! DPP oyee! Mumakwana sendela sister tili tonse 2025 DPP boma

  • @MulowokaBlessings
    @MulowokaBlessings วันที่ผ่านมา

    Mbuli yosaphunzira iwe palibe chomwe ukuziwapo tizithumwa tomweto munakakwima kwasing'anga anu aja mukunamatu inu

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs วันที่ผ่านมา

    Kwachematu

  • @stevenmwamadi3035
    @stevenmwamadi3035 วันที่ผ่านมา

    Mbuzi yamuthu nachimutu

  • @MulowokaBlessings
    @MulowokaBlessings วันที่ผ่านมา

    Ngati Pali chipani chaboza mumalawi ndi DPP chipani chinanamiza anthu kuti chisintha Malawi kukhala Singapore ,mbombera , zambili munalonjeza palibe chomwe munapangapo cholozeka ndimisonkho ya aMalawi

    • @SimbeyeSimbeye-z7l
      @SimbeyeSimbeye-z7l วันที่ผ่านมา

      Wasowa chonena iwe chikangawa😅😅😅

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 วันที่ผ่านมา

    Zowona mangochi umakwanira iweyo