ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
God bless you Mr kaula, I know u very well u teached me a french subject at zomba prison I am Robert
God is great zokanika ndiwathu zimatheka ndimulungu
God of wonders eeee 😢😢😢 indeed ure the lawyer 🙏🙏🙏🙏
Mr kaula my teacher for french,
Mulungu ndiwazatheka bwanj
24yrs ku nde munthu osalakwa..eeee this world😢😢
Kkkkk akuti onyonga ndi mzungu si munthu kkk koma
This reminds me the book "The political prisoner 3/ 75" by Samuel Mpasu... Ndendende
Chipani cha athu oyipa, mulungu azilemezeka
Mmm dziko lapansi😢😢😢
MCP nkhaza mzakalekale ndipo izi tikuziona lerozi sizachilendo ayi mzoyamwila
Misozi mmaso mwanga kwambiri chifukwa cha nkhani iyi . Mulumgu ndiwamoyodi ndithu .umboni wokhuza k ambiri I wish I could see this him face to face umboni wawo Uli ndi chipulumutso
Mmmm koma dziko ili, anthu ambiri ali ku ndende osalakwa.
Alhamdulillah Allah Akbar😢😢😢
Mulungu ndi wa mkulu Ulemu ndi matamando zipite kwa iye
Glory to God
Glory be to God
Zovesa chisoni mmmm😢😢😢
Inetu kuno kumangolila ngt ndibambo wanga
Àaa km yah
Mphavu ya Mulungu imagwira ntchito pa anthu achilungamo
Koma farm yawoyo ilipo?
Ati ndi nzungu simunthuyi😂😂😂😊
Nzung simuthu
Nkhani ndiyoona
Mulungu ndiye oweluza wolungama ngakhare mdima utakura kunja kumacha basi nthawi Zina mudaliso womwe mulungu watipasa ena sakondwera nawo ngakhare afumu ndi anthu ena anakhomelera koma mulungu anaziwa kare kt Munda ñdiwanu basi satana ukhare ndimanyazi
Hemusipi njoipadi ndithu😪
Nkuluyi mizimu ya kwawo inali yabwino Mulungu amadziwa kuti siolakwa
Omg 😭😭😭😭😭😭
Zokhuza zedi😢
Kusonyeza kuti ambiri amene ali kundende kuja ndithudi ngosalakwai😢😢😢
@bakili Muluzi tv
😢
Eeeeee koma dziko lapansi kuli nyansi za uchimo
19:22 eeeeeer komatu
Ndalira
very concerning story
Be kind
Koma sad.
Mulungu anali nao cholinga
Koma congelesi iii

Mulungu ndi wa mkulu
Ulemu ndi matamando zipite kwa iye