Maina anthu omwe anakhuzidwa pa imfa ya Chilima ndi anthu ena 9. Apa Ayaluka 🤔

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 15 ก.ย. 2024

ความคิดเห็น • 89

  • @PhiripChinkango-k5p
    @PhiripChinkango-k5p วันที่ผ่านมา +1

    Comrade ntanyiwa keep it fire burning brother God gives you wisdom and rong live

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b 9 วันที่ผ่านมา +11

    Mudzayenda ndi matemberero moyo wanu wonse mudzasowa mtendere moyo wanu wonse munapha mizimu ya anthu osalakwa muthawi ya Mulungu mwini wake isanakwane zoopsa kwabasi

  • @MitochiClinton
    @MitochiClinton 8 วันที่ผ่านมา +4

    Mpaka Micheal usi ,kondwani nakhumwa,dausi komanso anthu mulibe chifundo abusa achakwera zoona

  • @KennethMoses-dq9hz
    @KennethMoses-dq9hz 7 วันที่ผ่านมา +4

    There is no secret under the sun

  • @HawaHussein-d4l
    @HawaHussein-d4l 10 วันที่ผ่านมา +9

    Comrade mtanyiwa more faya

    • @EliasBout
      @EliasBout 8 วันที่ผ่านมา

      🎉🎉

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 7 วันที่ผ่านมา +2

    Koma anthu a MCP munabadwa pa nyini zotembeleredwa sure manganya nkholo yamako sure😢😢😢😢

  • @esaMoha-dm4kj
    @esaMoha-dm4kj 10 วันที่ผ่านมา +2

    Ayaluseni mtanyiwwa osawopha bakili muluzi TV Ayaluseni onse please tiutseni soona shonde

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b 9 วันที่ผ่านมา +3

    Palibe angafanane ndi Mulungu, mwayaluka

  • @ShaidaJackson
    @ShaidaJackson 8 วันที่ผ่านมา +3

    Mulungu awalange pansi pomwepano tikuona

  • @PatrickMbenje
    @PatrickMbenje 10 วันที่ผ่านมา +2

    Mulungu achite nawo anthu Amenewa ndipo mizimu ya anthu onse ibwele pa mitu pake Chikangawa ndi onse okhuzidwawa.

  • @ShinelShishi-ib8rw
    @ShinelShishi-ib8rw 10 วันที่ผ่านมา +2

    Ayalike amalawi tatopa chilungamo chioneke

  • @TrizaMandawala
    @TrizaMandawala วันที่ผ่านมา

    Kwaine chinena ndilibe taona imfa ndizoona km imfa yaamzathuwa ndiyomvesa chisoni ndipo ndiyowawa ndipemphero ndi pembedzero langa ndipo Mulungu amanvera kulira kwa ana ake kwaonse okhuzidwa popanga zimenezi Ambuye kumwambako amukanthe ndipo moto uoneke pansi pompano Mulungu wathu ndiwakutha ndipo izi khulupikirani zioneka kusogolo mizimu ya anthu 9 eshiiiiiiiii😢

  • @MathewsMpanga
    @MathewsMpanga 4 วันที่ผ่านมา

    Our God was there before, during and after the accident.
    He is a good God.
    If it's true, God's punishment is on their necks.

  • @BarwickSalanje
    @BarwickSalanje 11 วันที่ผ่านมา +4

    Uuuuu koma zinthu zake mpaka joyce banda

  • @user-je8jm5uy1q
    @user-je8jm5uy1q 4 วันที่ผ่านมา

    Yudasi weni weni ndi manganya amene wapeleka Chilima

  • @happychavula4469
    @happychavula4469 7 วันที่ผ่านมา +2

    Kondi ngati yinali ngozi nanga chilima suti yomwe anavala yinapitakochi mmmmmmm

  • @SteveSpeack-u2s
    @SteveSpeack-u2s 7 วันที่ผ่านมา +1

    Paka kalista mutharikaso

  • @KhumboChirwa-z2u
    @KhumboChirwa-z2u 5 วันที่ผ่านมา

    No sense why is it that there's so much hate in Malawi, amongst different tribes, zitha liti kodi.?

  • @KhumboChirwa-z2u
    @KhumboChirwa-z2u 5 วันที่ผ่านมา

    Nyasi zokha zokha

  • @ImmanuelndagomaKondowe-n1v
    @ImmanuelndagomaKondowe-n1v 4 วันที่ผ่านมา

    Anangovala ngati ma prisoner koma sanali ma prisoner eti?,amakathyola ndege ija,wanenadi paja kuti kukhala m'busa sikupusa

  • @DavidJohn-g8o
    @DavidJohn-g8o 6 วันที่ผ่านมา

    Thanks Limpopo fm for give us truth information about the death of chilima n 8 others,chikangawa(chanyera)and his team must go to herlo tatopa naye chakwera n his ng'ona party 😢😢

  • @TamalaMwamlima-gk5im
    @TamalaMwamlima-gk5im 7 วันที่ผ่านมา +1

    Kupha gulu lonselo anyani inu mizimu yanu isautsike mtendere udzakusowani mpaka kalekale

  • @YaqoobStandwell
    @YaqoobStandwell 10 วันที่ผ่านมา +1

    Akuziwa ose mcp kut ndizoonadi mmmmmm kukhala ena kungotula udindo pasi bas amene akupasidwa ndalama kut azibisa chilungamo azingozivutisa because Malawi wina aliyese or mwana akuziwa kut mcp sichipan ay

  • @S-rr1eu
    @S-rr1eu 7 วันที่ผ่านมา

    Mfiti zimenezi,,, zizakathera ku ndende 2025😢

  • @AlexChilombo-x2m
    @AlexChilombo-x2m 6 วันที่ผ่านมา

    Mulungu ndi amene akuziwa zonse zimene zinachitika kumuchotsa munthu nzawo chifukwa cha udindo wa dziko lapansi zokutha zotsala

  • @VaidaSidreck
    @VaidaSidreck 5 วันที่ผ่านมา

    Mulungu alangen notes afit

  • @MBwanali-x8z
    @MBwanali-x8z 10 วันที่ผ่านมา +3

    Palibe chisisi pansi pa thambo
    Zoopsa Mulungu azaweruzadi 25:42

  • @WAXBDJANGOSMOK
    @WAXBDJANGOSMOK 7 วันที่ผ่านมา

    eee koma able mulungu akudalitseni tembenukani mitima kma Chakwela Ulibe chisomo🇲🇿🇲🇿🇲🇿

  • @user-eq8hr8li8h
    @user-eq8hr8li8h 7 วันที่ผ่านมา

    Kodi kupha chilima zikugwirizana ndi DPP wasowa mfundo suzavota wekhetu azavote ndi amalawi ndipo azdzasankha okha amalawi

  • @user-gm9xj1wc2m
    @user-gm9xj1wc2m 10 วันที่ผ่านมา +4

    Ok nyc job vuto km mumapanga zobhowa bwanji samaulura asanamfe nd mumachedwa kufotokoza straight point bwanji ..???????????😢😢😢😢😢😢😅😅😅😅😅😅

  • @JimmyIsaac-xd4ef
    @JimmyIsaac-xd4ef 10 วันที่ผ่านมา +1

    MCP ndi chipani chakupha basi

  • @MwayiMponda
    @MwayiMponda 6 วันที่ผ่านมา

    Yahweh akungoyang'ana eishiiiii

  • @JessicaKatugwe
    @JessicaKatugwe 5 วันที่ผ่านมา

    adzakulangani mulungu anthu inu mmmm😊

  • @user-sm8gx4vf1v
    @user-sm8gx4vf1v 7 วันที่ผ่านมา

    Mcp yakoyo ndiwe galu udzavota wekha ndiweso chitsilu ukusapota mcp galu

  • @watsonmhango8794
    @watsonmhango8794 10 วันที่ผ่านมา

    More fire Mtanyiwa umayitha 😅😅😅😅😅

  • @petrooverton6643
    @petrooverton6643 10 วันที่ผ่านมา

    naweso ulini matha maina osewa sangagwile shito imozi ukuopa kuwatnchula athu anai waachula kale koma ukuonezela ena kutu eti tiziti akuganiziridwa enao ngati akuchulidwa amagwila tnchito motumidwa ndi abwana mosaziwa kuti chikuchitika ndi chani

  • @DanielSimwela
    @DanielSimwela 10 วันที่ผ่านมา

    Zikumveka nditu comrade. Koma kanyimbo aka ka takuikani pa muyezo tigailen

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire 5 วันที่ผ่านมา

    Munthu ndoipa abare mmmmh kulimba mtima chonchi

  • @esaMoha-dm4kj
    @esaMoha-dm4kj 10 วันที่ผ่านมา

    Shinkangawaw amwalila ndi BP before 2025 tisanavinke pompano

  • @JuniorMkumba
    @JuniorMkumba 5 วันที่ผ่านมา

    OK nkhanga zaona

  • @LumbaniPolowani
    @LumbaniPolowani 7 วันที่ผ่านมา

    Wazigwetsa yekha sife ayi koma mufune musafune sawinabe olo mubele mavoti,Dpp anapha chabwino koma inu mwaonjeza kupha anthu ngat nkhuku choncho bwanjo?mpaka 9pple??? Mizimu yawo ikukatheni ndithu

    • @jameschiwanga
      @jameschiwanga 6 วันที่ผ่านมา

      Osayiwala Kut DPP inampha anthu 25 Ku mzuzu and not only that but also ma lubino ose Aja munampha aja

  • @KennedyDaudi-c2k
    @KennedyDaudi-c2k 5 วันที่ผ่านมา

    eeeeeee zovuta kwambiri

  • @StewartGoma
    @StewartGoma 7 วันที่ผ่านมา +1

    Really a Joyce Banda infront of the people u act good when the sun set u changed colours
    That's why u were saying that politics u do at night shame on u all

  • @VaidaSidreck
    @VaidaSidreck 5 วันที่ผ่านมา

    Akulangen afit ngati chinyama zanu

  • @LifaMalakamuMazibuko-h2m
    @LifaMalakamuMazibuko-h2m 7 วันที่ผ่านมา

    Akulu akulu apa ndinthawi sopano ya mademo basi😊

  • @GeraldBMaster
    @GeraldBMaster 7 วันที่ผ่านมา

    Mulungu achitepo kanthu😢

  • @user-ll3qi5im7x
    @user-ll3qi5im7x 6 วันที่ผ่านมา

    Manganya umuziww yesu😢

  • @SuleimanRabsonMkhunga
    @SuleimanRabsonMkhunga 11 วันที่ผ่านมา +1

    Eeee zovuta

  • @priscillamangata4023
    @priscillamangata4023 10 วันที่ผ่านมา

    Namkumwa anakulakwilani Chani chilima

  • @GenialaChalera
    @GenialaChalera 7 วันที่ผ่านมา +1

    Ngati mukufuna kumugwetsa chakwera fundo zake sizimenenezi mwanama ifeyo tikudziwa dpp idapha anthu ambiri ndipo sizitheka kumugwetsa

  • @EDSONNAKULENGA
    @EDSONNAKULENGA 8 วันที่ผ่านมา

    Tikupepelazimuwachilima ukusauseninose ndipo nanusomuzipanoka choipachikusatani ahebili 12:29 ikulodoleni

  • @EDSONNAKULENGA
    @EDSONNAKULENGA 8 วันที่ผ่านมา

    Komamulungu awakwapula kwabili masalimo 1o9:1

  • @thomaswyson-e2q
    @thomaswyson-e2q 10 วันที่ผ่านมา

    Amfit amenewa atimalizad

  • @MaxwellMbesa
    @MaxwellMbesa 7 วันที่ผ่านมา

    Munaoha thupi lokha mizimu ilipo musowa mtendele

  • @Richardbanda-hg6pt
    @Richardbanda-hg6pt 8 วันที่ผ่านมา

    No secret underground

  • @EllinaBitto
    @EllinaBitto 10 วันที่ผ่านมา

    Mmmmmm😭😭😭😭😭😭😭amakaphadi mfumu gullu lonseli😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭

  • @StaphordNangumi
    @StaphordNangumi 7 วันที่ผ่านมา

    Ziko ndi anthu ake

  • @user-gm9xj1wc2m
    @user-gm9xj1wc2m 10 วันที่ผ่านมา

    Pakana Dausi

  • @florenceMhone
    @florenceMhone 5 วันที่ผ่านมา

    😅

  • @AbdullsharifuJasiteni
    @AbdullsharifuJasiteni 8 วันที่ผ่านมา +1

    Achakwela ndikunthu opantha chinson 😭😭😭😭😭

  • @ruthkundwe7448
    @ruthkundwe7448 7 วันที่ผ่านมา

    🙆🙆🙆🙆

  • @ChimwemweKondowe-nj4lx
    @ChimwemweKondowe-nj4lx 8 วันที่ผ่านมา

    Jay Kawere uli ndi vuto. You like posting other people's videos.
    Kodi iweyo can't you start up your own carrier than posting other people's videos?

  • @EbaBaera
    @EbaBaera 8 วันที่ผ่านมา

    History is a best teacher

  • @SydneyAbsalomkamangah
    @SydneyAbsalomkamangah 5 วันที่ผ่านมา

    MCP inapha an2
    Tinkangomva tili ana
    UDF inapha tikuona
    Lero Kachikena MCP
    Malawi wakupha mbiri ya2

  • @GodfreyMzembe-b3n
    @GodfreyMzembe-b3n 11 วันที่ผ่านมา +1

    😂😂😂😂😂

  • @NoorRasheed-re5vh
    @NoorRasheed-re5vh 6 วันที่ผ่านมา

    Sizingangatheke zimenezo osewa sangakhale odana ndi chilima ,maganizo ako ndiosochela , akhalabwanji Nankhumwa VP ngati adalinawo mu ngwilizano watonse zizikunveka ndiwe wabodza.

  • @AustinKhonje
    @AustinKhonje 10 วันที่ผ่านมา

    Eeeeee koma ziliko

  • @HajjAmadu-e1u
    @HajjAmadu-e1u 10 วันที่ผ่านมา +1

    Koma anthu ndoipa ee

  • @captainmdima1102
    @captainmdima1102 7 วันที่ผ่านมา

    Aaaa izi tingamizane mulungu ndamene akuziwa zonse

  • @Slyvester-zs6ww
    @Slyvester-zs6ww 7 วันที่ผ่านมา

    Wabodza uyu akungofuna kuipitsa mbiri ya anthu. Akut kukoza njila yoti DPP idutsepo aaaa manyazi ulibe galu iwe.
    Munthu wanyibvi mutu iwe udzagwidwabe osaoneka ndi MULUNGU paja zimenezi osayiwala. And udzayankha milandu yochuluka ya anthu ukuwayipitsila mbiriwa.

  • @Slyvester-zs6ww
    @Slyvester-zs6ww 7 วันที่ผ่านมา

    Ndinu achitsilu Ku MALAWI kuno wayamba kufa ndi Chilima? Tsitsilu kwabas inu anthu osafuna chitukuko kuzolowela kulandila basi.
    Boma la Chakwela ndiloyanja anthu okhawo amagwira ntchito ndimanja Ake.
    Osati alesi akubwela.
    And mukachita masewela tigawana dzikoli. Munya akumwela mudazolowela kulandila.
    Tigawane basi.

    • @LifaMalakamuMazibuko-h2m
      @LifaMalakamuMazibuko-h2m 7 วันที่ผ่านมา

      Unalinawo limodzi ubwinowake ndukuziwa iwe

    • @BettieKamija
      @BettieKamija 7 วันที่ผ่านมา

      Loyanja iwe ndi akwanu. Mukubera limodzi

    • @GregoryMatambo-m6y
      @GregoryMatambo-m6y 5 วันที่ผ่านมา

      Koma a Malawi ndife zitsiru kumamvera zabodzazi klkkk kupusitsidwa ndi mbuzi ngati iyi aaaaaa kumbwambwana

  • @samdiverson9733
    @samdiverson9733 7 วันที่ผ่านมา

    Just go straight to the point bro mtanyuwa

  • @Slyvester-zs6ww
    @Slyvester-zs6ww 7 วันที่ผ่านมา

    Ndipo ndaona ifa ine mukanene yachilima.
    Adafako bambo anga mukanene chilima ndaniso.