Atola nkhani akumalawi mafunso awo amafunsa ngati ndi alendo kumalawi kuno kaya amakhala mantha kaya ndikusantha ntchito I don't know eni akewo amati professional kkk
Analipo wina anthu sanamusinthe mu 31 years,people died, freedom was just a word and not action on the ground and the country was leaving in fear. Ngat amasintha mafumu mwini wake yekha Mulungu what more anthu. ?
CDED pen Russian president Putin to assist with the investigation. That man will help malawians to know the truth of that fatal accident. That man will never disappoint Africa
Exactly you are a real citizen of mawi continue fighting for our freedom
Thank you Mr NAMIWA we need people like you Osaopa Osafooka kms Osatopa 💪 nthawi zonse kuyima pachilungamo ( SKC💔)
I really love this my brother akuchita kuoneka kuti akuyankhula kuchoka pasi pa ntima
Very good Mr Namiwa tiimilireni chonde
Go ahead with what you are doing BRAVO CEDED
Ndizowo nbava yizi atiwuze zowona pasanathe mwezi wuno apo biiiiiii mademo a choke kusiteti hausiko kulowe a chili ngmo Kuno kumocanbiki
Bwana Namiwa ,, muzipemphera kosalekeza ,,,, Dzikoli layipa ,,, Chilima anafera chilungamo chomwecho
Mr namiwa mulunguakudalitseni
Amen ambuye azikudalitsani pazomwe mukuonesa
Bravo CEDEP ... awawa ayankhe sizomatipusitsa a Malawi ngati Ana awo. The thugs in this illicit act must be brought to book
Continue to rise Malawi 🇲🇼, namiwa it's our voices
Akulu akulu tiyeni timpange support Namiwa tisamusiye yekha munthu akutipula pa ground kut chilungamo chiyende ngati madzi tiyeni tipeleke support amalawi please. Akamuna akuyankhula mopanda mantha. Namiwa ndikatundu onyamulizana simunthu wamasewera ndipo safuna chibwana💪💪💪
Aaaaa ! Pamutu Panu pakuyenda bwino?
Number one point
Silvester Namiwa you are the best
Hope voice Mr keep good work
Komaso ndichifukwa Chan chakwera amayimisa kufufuza denge Kuti tiyambireso mawa chakwera chikangawa tiuze zoona ndi nkunkuyu nonse ndi phiri
Following gyz Running short of words
Strong words my brother we are with you wosawopa
Mzimu wa munthu ndiwovuta a Chakwela you have alot to answer, mwabisala mbatata msana wawonekela you can't ran away from this we all watching
U don't know what u want to say kkkk
Please go ahead with what you are doing for FIGHTING for POOR MALAWIANS we SALUTE YOU
Mwatiyimilira go ahead ma comrades
God bless Malawi please
Bravo you are only our hope limbikilani kutiimilira
Those questions Namiwa asked, are very valid, 700m from village, + why president said the plane was forced to return when it arrived in Mzuzu
😂😂😂 just wait u see l Hope u see still sleeping
@@StanleyDama vikupulikikwa yayi Ivo walemba
Go on 🙆♀️
You are one in a million ase
That's great tell them the truth
God protect you all the time bro
Chilumgamo chioneke,,Mr president defend your previous statement on
Ife tili pambuyo panu don't give up chilungamo chidziwike
Mwadya balalikani?
Comrade Namiwa your no one dude
Bravo CDED, may God guide & shield you guys for your fight for common Malawians
Watching from south Africa
Mr NAMIWA mulungu akutetezeleni ndipo MULUNGU akutsogoleleni muchilichonse mpaka tipambane munkhondo imeneyi
Go up namiwa
RIP my President SKC,
Ntima wanga sukuvomelabe..
💔💔💔
Ulemu wanu Big Namiwa...
Thanks mr namiwa for the trues❤❤❤
Atola nkhani akumalawi mafunso awo amafunsa ngati ndi alendo kumalawi kuno kaya amakhala mantha kaya ndikusantha ntchito I don't know eni akewo amati professional kkk
I agree with you plus chibanzi nso
Tiyamike kwambili nonse mukuimilila amalawi ❤❤❤❤❤ osafooka osatopa
Ukunena zoona namiwa
only today l can agree with yuo 👌💪💪💪
Even Chakwela him self is happy , bcoz as Malawians we knows only Audio's not action
Malawi everything anafeliya
Mr chikangawa alibe chisoni zisilu mcp boma patumbo paooo
Chakwera must go
Pena pake ine nduwona ngati we have too much democracy in this country, making it difficult for the country to be properly organized and progress
Tilinanu mr namiwa ulemuwanu
This is a fact
Mr namiwa alindiumunthu osamaikilakumbuyo nkhanizoyipa atolankhani awuchitsilu mafusomulibe
Zoona bwana
Mr Chakwala akufunika abwele poyela kudzayankha mafunso pa mtundu wa Amalawi.
Chifukwa akalephela kubwela poyela ndiye kuti simtsogoleri ofunika mudzoko la Malawi
Yes inudi mumamenyele ufulu
Atolamkhani akumalawi saziwa kufusa ay ndi Brian yenkha osat izi ay😂😂😂😂😂
The guy is intelligent and honest bravo!
Gwape samwamadzi galualipambuyo
Chakwera nyini yamake sangandiuze zochita amadya ndalama zanga mapwala angoononga misonkho
Zoonadi kulankhula modekha, mau amphamvu .
Komaso ife amalawi tidakali kulirabe
Chakwera amakonda kubunyula vuto 😢😢
Ulemu wanu anamiwa tikufuna xhilungamo pa imfa ya chilima
God will guide you Namia and you must be come a president wathu
Chakwera watitora kwambiri
Go on
Ndinu amene mmasokoneza anthu kusintha ma pulezidenti ngati Malaya apaso mkufuna kusinthaso eish amalawi mkaphuzira pena pache ndinu mama lakwa
Analipo wina anthu sanamusinthe mu 31 years,people died, freedom was just a word and not action on the ground and the country was leaving in fear. Ngat amasintha mafumu mwini wake yekha Mulungu what more anthu. ?
Ayi kusintha ma president sikwabwino koma chakwera ekha choke
Zoona izi Chakwera alepheradi
Powerful Mr namiwa
🔥🔥🔥🔥💪💪💪💪👍
God bless you bravo
Athuwa tikuwaselelela tingowathamangisa mu ziko muno
CDED pen Russian president Putin to assist with the investigation. That man will help malawians to know the truth of that fatal accident. That man will never disappoint Africa
apa madzi ada
the questions are relevant
Ndikuyamikileni kwambiri mukuyakhula fundo zabwino bwana koma vuto amcp ndi anthu wokuba kwambiri sangasinthe galu ndi galu sangasinthe kukhala munthu
Big man Mulungu akudaliseni akulu Malawi 🇲🇼 ilimba ngati tigwilana manja
Chilungamo chake bwana auzeni .thawi yakwana 😢
Anthu olimba mtima ngati Chilima aliponso eeeeeeeti😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢
The second question is so powerful and namiwa is failed to answer kkkkkk
Osawasiya tiyenawoni anthu okuba
Mulungu apitilize kukusamalani
President ndi nduna zake ndo valentino planned to kill the 8 pple achoke tatopa nawo anthu opanda nzeru, okuba, okupha
Until now, sindmakhulupilirabe kut anapita,,SKC
Powerful speech 👏👏👏
Mabungwe mukutani
Waiting for gear 2
Tikangoyatsa moto Manyumba mwawomo
Namiwa ndi m’banga
That's right
Motion, vote of no confidence
We need truth and reconciliation hearings.
Chakwera upha bwanji chilima ndi anthu ena chakwera nyini yamako😢😢
Boma ili tatopa nalo ndithu
Iwe ndiye munthu tiyeni kunsewu basi
Mukutiyimilira a namiwa go ahead.
Kkkkk zawathina amaona ngati anthu akhutila ndi bodza lawo lalipoti mr namiwa mumakwana ndi sitafu yanu athawatu apita ku chaina 😂😂
Chakwera really failed us akanakhala wanzeru was not supposed to go to China yes has questions to answer from plane report watitola kwambili
MCP ndiyakupha
Acded mmawoneka ngati muli siliyasi mukanakhala asiliyasi bwenzi mutayitanisa mademo okhuza imfa ya chilima
Mumakwanira bwana
Namiwa uremuwanu ozaopa 💯💯💥💥💥👍
Ukaziyamba ofunika kuzimaliza chifukwa ena akawonesedwe nthumba akazisiya ndiye ife osakawukafe tikamakusatan tikumafa changada any way keep it go
Tiyakhuledi ife amalawi
Atolakhan a dzodiyak ndakwiya nanu .mafuso anu mukukhala ngat sindinu amalawi 😣
👏🏾👏🏾👏🏾👏🏾👏🏾👌🏾