Ulaliki pa Maso pa President Chakwera. Azibusa atha mantha, Angosata chilungamo

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 23 ส.ค. 2024

ความคิดเห็น • 22

  • @IanAllstal
    @IanAllstal หลายเดือนก่อน +2

    Pachilungamo palibe Mantha 💪💪💪 kufera mbendela iyiiih 👉👉🇲🇼🇲🇼🇲🇼

  • @peternashyo9850
    @peternashyo9850 หลายเดือนก่อน +2

    Powerful preaching

  • @ngolekakondwani
    @ngolekakondwani หลายเดือนก่อน +2

    Nthawi yabwino ndiyomweyi kulapa ndikusiya zonyasa..Mulungu atitsekule maso ndi makutu kuti tione nyengo tili.

  • @user-jn9tz3li3v
    @user-jn9tz3li3v หลายเดือนก่อน +3

    Abusa opanda banzi mukamwa amenewa

  • @ElizabethMaononga
    @ElizabethMaononga หลายเดือนก่อน +1

    Palakwika chani apa.uthenga ndi uthenga ukupita kwa aliyense.koma lmasulirani mukuona ngati ngwa a Chakwera uthengawu.Mumudziwe Yesu ithink.Uthenga wa mu bible umapita kwa anthufe.osati uyo kapena uyu koma kwa ife anthu .chotero mmafunika maso auzimu kuti muzindikure.Chakwera mukulimbana nayeyu muchedwa naye. Zake zilibwino ohoooo.

  • @user-jn9tz3li3v
    @user-jn9tz3li3v หลายเดือนก่อน +1

    Chakwela makutu giwogontha mukungotaya nthawi yanu mukuganiza kuti angasinthe ndikumuthawa amene panopa ndi bwenzi lake lapamtima Satana.

    • @tamalangoma2765
      @tamalangoma2765 หลายเดือนก่อน

      Amalalikira iweyo ndi dziwanda zakozo, umudziwe yes.

  • @priscillachola1006
    @priscillachola1006 หลายเดือนก่อน

    What a word!
    What a bold messenger

  • @tamalangoma2765
    @tamalangoma2765 หลายเดือนก่อน

    I agree with you 100% my sister

  • @williamsjonazie5764
    @williamsjonazie5764 หลายเดือนก่อน

    Kuziyamba zoti siungazimalize

  • @RobertGoliat-gt2qh
    @RobertGoliat-gt2qh หลายเดือนก่อน

    Powerful preacher

  • @ellensambo6323
    @ellensambo6323 หลายเดือนก่อน

    Powerful Amen

  • @chimwemwenkute3839
    @chimwemwenkute3839 หลายเดือนก่อน

    May God be praised

  • @alfredmphande4930
    @alfredmphande4930 หลายเดือนก่อน

    Utùmki wamphamvu ❤

  • @user-yc3ik9dq3x
    @user-yc3ik9dq3x หลายเดือนก่อน

    Very powerful 🙏🏽

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 หลายเดือนก่อน

    Abusa alalika bwino akumva wamva otsamva akwiya mutima

  • @user-ik5sz8hc6f
    @user-ik5sz8hc6f หลายเดือนก่อน

    Uthenga wa mulungu ukafikile onse dziko lapansi.

  • @chrismando224
    @chrismando224 หลายเดือนก่อน

    Uthenga kunva mkumanva osasiya Kuba ndi kupha anthu osarakwa

  • @gracemkandawire8769
    @gracemkandawire8769 หลายเดือนก่อน

    Abusa zikomo,,koma anva awa

  • @user-uq6ph3ox2u
    @user-uq6ph3ox2u หลายเดือนก่อน

    Mkanadziwa simkanapitako 😅

  • @user-ik5sz8hc6f
    @user-ik5sz8hc6f หลายเดือนก่อน

    Ena mwaomverawo alephela

  • @kennedybanda
    @kennedybanda หลายเดือนก่อน

    Hell is real