ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Glory be to the most high GOD ❤❤❤
This is so powerful song wawooo ...glory to the almighty father ...I have played this song 7times ...AMEN AND AMEN
Ooih yes
We glorify God for the grace which upon Daughter of Zion. This is one of the powerful songs. Amen Amen
Yes Lord, your no 1 palibe ofanana nanu baba ulemu,matamando kukwezedwa konse ,kwayenera inu🙏🙏
Eeee this song is very powerful glory to the most high God, the owner of everything, king of kings and lord of lords 🙏🔥
Amen
Q
Mwayenela kulandila ulemu ndi matambo,,bondo lililonse layenela kugwadila inu baba,,, powerful song
Mai mumaimba, koma nyimbo iyi mmmmm 🙏🙏🙏 Ambuye apitirize kukugwiritsani ntchito!!! Tikulemekeza Yehova osati chifukwa cha zimene tiri nazo ayi koma CHIFUKWA CHA M'MENE IYE ALIRI!!!
Am blessed with the songs. ... Munyimbo muli mphamvu yopoosa kwambili
❤🎉🎉🎉powerful 😢alandiledi ulemu ndi matamando God bless u cct
Ooh yes chifukwa. Mene mulili landilan ulemu ndithu 🎉
Almighty Lord your an equal There is nothing we can compare with you
Musadzasinthe Mama. Yehova wayeneradi Ulemu ndi matamando chifukwa Cha mmene Alili. Nyimbo yokoma kwambiri kwa ma Worshippers onse. Indiphe ndi sitepe ine kuno ,on repeat . Ooooooo Yesu landirani Ulemu Woyera wankulu wa Israel, opanga njira popanda njira, Alefa ndi Omega , Thandizo lopezekeratu, Moto Onyeketsa,Tate Osakwiya msanga. Tate wa Amasiye onse . Dzina lanu Lili pamwamba pa Maina onse. Otimenyera nkhondo, otiweruzira milandu yathu. Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah HallUpelujah Hallelujah 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🥁🎷🎵🎶🎺🎤🎻🎸🎧🎹🎧🎹🎻🎸🎷🎵🎶🎶🎶🎶🎶🎶🎤🎺🥁
Amen amen amen
Amen Amen Amen
Amen 🔥
Oh yes Hallelujah ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤I'm in love with this song
Amen daughter of Zion, Mulungu akuuze malire anu , mupitilize kutitsitsimusa ndi nyimbo zanu zabwino zopereka chiyembekezo🙏
Amen amen
What a powerful ministration remain blessed
Ameeeeeeen!❤❤❤❤❤
Allelluya, Ambuye tikulemekeza, tikulambirani, pakuti ndinu woyenera ulemu kulibe wofanana nanuUlemerero wanu ndi wosasanthulikaHa!! Yehova dzina lanu liposadi nanga Kumwamba ndi dziko lonse lapansiNthawi yakwana kuti wolambira inu akulambireni mu Mzimu ndi muchoonadiNdi mitima yokondwera, ndi yoyamika tiyimba kukulemekezani, Woyera inu🙌🙌
Amen!!!
Glory to God
This song is so powerful and ndikulimbikitsikan ndi nyengo yomwe ife tukumanananO❤
Nice mama mumantha ❤❤❤❤❤❤❤❤
Amen Amen Ambuye alemekezeke koposa kwabasi kamba kamphaso ya moyooo kunooo
Nyimbo zoti ukamamvera thupi lonse nyesi kuzoza kwanyimbo AMEN
❤❤Amen , great messenge
Glory ...chifukwa Cha mmene mulili landilani matamando Yehovah
❤❤❤❤❤❤❤landila matamando Jehovah WOSAKWIYA sanga wosamala wosamala thawi zonse
Love you mama❤️
Nice songs momie❤❤❤❤
Hozaaaaaaaa 🔥🔥🔥🔥🔥🔥 ayayaya God receive the glory , Mami I love u
Nyimbo yabwino kwambiri ❤❤
Powerful
🎉🎉🎉 Becoz of your nature receive all praises🔥🔥
God
Amen ❤🔥
Moto wonyekesa🙌🙌🙌🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥Landilani matamato dzinalanuliri pamwamba pamayina wose.Amen
Ambuye mulemekezeke nthawi zonse.
Thank you Jesus❤
Alleluya zoonadi mulandile matamando yehova
Mamie, I love u so much. Glory be to God
Ooh yes,, powerful 🎉
Ikanamvekanso mwamphamvu kwambiri mukanaimba ndi Thom Kachimanga Kapenga Joseph Chirwa.
Oooh yes ❤❤❤❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉groly groly groly
We love you daughter of Zion God bless you
Landiranidi matamando inu father of fatherless mukungoyeneradi inu wondichotsa mmatope nkundiika pa thandwe .cmunafunse munthu pondidalitsa ooh hallelujah ❤🎉
Mulungu azikudalitsani kwambiri a Mai inu😭😭😭
Akungoyenera Matamando palibe wofanana naye🔥🔥🔥
Chifukwa cha mmene muliri Yahweh.. Landilani matamando
Eish landilani matamando Yesu .
Amen amen zilibwino kwabasi ife tili busy kuvina kosalekeza
Chifukwa cha m'mene muliri Yehova❤❤❤❤
Amen and Amen
Zoonadi landilani matamando chifukwa cha zabwino zokoma zimene mukumandichitira yaweh🎉🎉❤
🎉🎉🎉🎉🔥🔥🔥
Oooh Yes🎉🎉 Hallelujah ❤❤💃💃💃💃
So amazing
Landilani matamando ❤❤❤❤❤❤
Beautiful song
Mandidalitsa mama mnyimbo zanu muli za mphamvu
Ooooooh yes keep it up
Amen so powerful
Amen mulandire matanda yahweh
Hallelujah powerful
Amen 🎉
Amen Amen
Amen❤
Oh yes chifukwa chammene mulili baba I dont know why am singing this song with tears 😢 Jesus
Glory up God
❤❤❤❤Amen
Mai mumandidalitsa kwambiri ndi nyimbo zanu
Hallelujah
Halleluyah 🎉🎉🎉
❤❤❤
Oooooh yes landirani matamando🧎🙏
Ambuye chifukwa cha mene mulili palibe wina inu mukule ife tichepe
❤
Zoona la ndirani Matamando Yehova chifukwa cha mmeene
Amen. Mama keep prays and worshiping the true GOD
Matamando akukuyenerani baba
muli kudzodza munyimbo iyi
Chifukwa Cha mmene mulili......
𝕟𝕕𝕚𝕡𝕠 𝕒𝕜𝕦𝕪𝕖𝕟𝕖𝕣𝕒 𝕜𝕦𝕝𝕒𝕟𝕕𝕚𝕣𝕒 𝕦𝕝𝕖𝕞𝕦 𝕪𝕒𝕙𝕨𝕖 ❤❤
Glory be to the most high GOD ❤❤❤
This is so powerful song wawooo ...glory to the almighty father ...I have played this song 7times ...AMEN AND AMEN
Ooih yes
We glorify God for the grace which upon Daughter of Zion.
This is one of the powerful songs. Amen Amen
Yes Lord, your no 1 palibe ofanana nanu baba ulemu,matamando kukwezedwa konse ,kwayenera inu🙏🙏
Eeee this song is very powerful glory to the most high God, the owner of everything, king of kings and lord of lords 🙏🔥
Amen
Q
Mwayenela kulandila ulemu ndi matambo,,bondo lililonse layenela kugwadila inu baba,,, powerful song
Mai mumaimba, koma nyimbo iyi mmmmm 🙏🙏🙏 Ambuye apitirize kukugwiritsani ntchito!!! Tikulemekeza Yehova osati chifukwa cha zimene tiri nazo ayi koma CHIFUKWA CHA M'MENE IYE ALIRI!!!
Am blessed with the songs. ... Munyimbo muli mphamvu yopoosa kwambili
❤🎉🎉🎉powerful 😢alandiledi ulemu ndi matamando God bless u cct
Ooh yes chifukwa. Mene mulili landilan ulemu ndithu 🎉
Almighty Lord your an equal
There is nothing we can compare with you
Musadzasinthe Mama. Yehova wayeneradi Ulemu ndi matamando chifukwa Cha mmene Alili. Nyimbo yokoma kwambiri kwa ma Worshippers onse. Indiphe ndi sitepe ine kuno ,on repeat . Ooooooo Yesu landirani Ulemu Woyera wankulu wa Israel, opanga njira popanda njira, Alefa ndi Omega , Thandizo lopezekeratu, Moto Onyeketsa,Tate Osakwiya msanga. Tate wa Amasiye onse . Dzina lanu Lili pamwamba pa Maina onse. Otimenyera nkhondo, otiweruzira milandu yathu. Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah Hallelujah HallUpelujah Hallelujah 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🥁🎷🎵🎶🎺🎤🎻🎸🎧🎹🎧🎹🎻🎸🎷🎵🎶🎶🎶🎶🎶🎶🎤🎺🥁
Amen amen amen
Amen Amen Amen
Amen 🔥
Oh yes Hallelujah ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤I'm in love with this song
Amen daughter of Zion, Mulungu akuuze malire anu , mupitilize kutitsitsimusa ndi nyimbo zanu zabwino zopereka chiyembekezo🙏
Amen amen
Amen
What a powerful ministration remain blessed
Ameeeeeeen!❤❤❤❤❤
Allelluya, Ambuye tikulemekeza, tikulambirani, pakuti ndinu woyenera ulemu kulibe wofanana nanu
Ulemerero wanu ndi wosasanthulika
Ha!! Yehova dzina lanu liposadi nanga Kumwamba ndi dziko lonse lapansi
Nthawi yakwana kuti wolambira inu akulambireni mu Mzimu ndi muchoonadi
Ndi mitima yokondwera, ndi yoyamika tiyimba kukulemekezani, Woyera inu🙌🙌
Amen!!!
Glory to God
This song is so powerful and ndikulimbikitsikan ndi nyengo yomwe ife tukumanananO❤
Nice mama mumantha ❤❤❤❤❤❤❤❤
Amen Amen Ambuye alemekezeke koposa kwabasi kamba kamphaso ya moyooo kunooo
Nyimbo zoti ukamamvera thupi lonse nyesi kuzoza kwanyimbo AMEN
❤❤Amen , great messenge
Glory ...chifukwa Cha mmene mulili landilani matamando Yehovah
❤❤❤❤❤❤❤landila matamando Jehovah WOSAKWIYA sanga wosamala wosamala thawi zonse
Love you mama❤️
Nice songs momie❤❤❤❤
Hozaaaaaaaa 🔥🔥🔥🔥🔥🔥 ayayaya God receive the glory , Mami I love u
Amen
Nyimbo yabwino kwambiri ❤❤
Powerful
🎉🎉🎉 Becoz of your nature receive all praises🔥🔥
God
Amen ❤🔥
Moto wonyekesa🙌🙌🙌🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Landilani matamato dzinalanuliri pamwamba pamayina wose.Amen