Unduna wazamaphinzilo ku Tanzania wawuzidwa kuti ana a school ayambe kuphunzila malile asopano a lake nyasa,,pamenepa ndipamene Pali nkhani,, zatheka bwanji ngati Iwo sanapasidwe chilolezo ndi boma la malawi 😢 Zikwanje mmpariament chifukwa chiyani Kugulisa likoma mmmmmm nkhanizi ndizazikulu zofunika nduna nkhale president alankhulepo amalawi timvesese😢😢😢😢
Tilibe mbali ife, timangofuna ma views chabe. Muonele video imene itatuluka after 2hours, muone mmene taisambwazila DPP, kaya aku DPP sasiya kuonela ma video athu kaya
Izizi munthu sangodzuka nkuyankhula izi .. it's even about politics or zipani.... you'll be shocked how these pple will continue to destroy Malawi.... don't always be defensive zilizonse
I hered so end it's true oooooo where is MDF no aaaaa it's not true lake Malawi becoming lake Tanzania no they should not do so end if he is the commander no no
Payenera kuti munthu, kapena titi mMalawi akanena nkhani ya sensitive ngati yotereyi osapereka tangible evidence kumtundu was a Malawi, pakhale lamulo loti munthuyo azimuumiliza kuti anene zoterozo kwa atolankhani pa TV, Radio ndi mnyuzi pepala kuti alongosole nkhaniyo ndi kupereka umboni oti ndiyoona. Failing which s/he has to be arrested for committing a "disinformation crime".
Mukutsutsa dekhani muva posachedwapa simukuti mudikila atolakhani dekhani musathe mawu ,mukutsutsanu mumaonekeratu kt ndinu odana ndichilungamo
Fullish leader
Unduna wazamaphinzilo ku Tanzania wawuzidwa kuti ana a school ayambe kuphunzila malile asopano a lake nyasa,,pamenepa ndipamene Pali nkhani,, zatheka bwanji ngati Iwo sanapasidwe chilolezo ndi boma la malawi 😢
Zikwanje mmpariament chifukwa chiyani
Kugulisa likoma mmmmmm nkhanizi ndizazikulu zofunika nduna nkhale president alankhulepo amalawi timvesese😢😢😢😢
Amend amadziwa map a Malawi, including Lake Malawi sangavomereze izi. Tanzania alinso ndi kambali komwe ndi kawo uyambila kale kale
Amalawi chakwera tikumuopa kd tiyeni timuphe ameneyu
Tangonenipo za chilungamo mr bon kalindo kkkkkkk
Nyanja yapita ndalama zalowa mu thumba la chakwera
Anayambisa zimenezo ndi Mai joice Banda kugulisa nyanjayo
Boni kalindo zina umakonda kuwanamiza amalawi kulibe lake Malawi angagulise iwenso mtolankhani umanena zokondera Dpp
Tilibe mbali ife, timangofuna ma views chabe. Muonele video imene itatuluka after 2hours, muone mmene taisambwazila DPP, kaya aku DPP sasiya kuonela ma video athu kaya
@@bs-malawiiiiiii tisiya kumene kuonera kkkkkkk wow any way enjoy ur holiday God blc u
It's true part of our lake Malawi has gone to Tanzania
Kodi zinsinsi zambri zimavumbuluka ndi anthu onweo amadya nae Chakweray komas Mulungu akuvumbulusa znse poyera ndye ngt zil zoona zidziwika dziko lolenga Mulungu ili osachita nalo masewera
Mwana ooopsa kwambili
Izizi munthu sangodzuka nkuyankhula izi .. it's even about politics or zipani.... you'll be shocked how these pple will continue to destroy Malawi.... don't always be defensive zilizonse
Nkani iyi yabodza atolankhani akanazifunsa
Ndipo chakwera akuyenera achoke bc
Inu musamachedwe nd kuva atolankhani nd munthu ngt Inu nomwe amakhala kt awapatsa chimbazi kt asayankhule chilungamo
Osamangokana osamangovomera... wait the truth will always come n aliyense muzaona nokha...musathepo mawu...the truth will always come to pass
Zabodza kulu
I hered so end it's true oooooo where is MDF no aaaaa it's not true lake Malawi becoming lake Tanzania no they should not do so end if he is the commander no no
Zovuta
Nyanja nkhani yake ndiyakale kale sikuti MCP yagulisa ayi
Zikuchitika mu ulamuliro wandan
Mulungu ndye mboni yazonse mukudziwan ndye sekani pachimbuzi panop mumafun adxikutaman ndani mumadxitenga ngt phweya tikupumau mwatipasa inuyo bwanji gulisan osandiiwalas kundgulisa ine Mulungu akudaliseni komwe muliko pamodz ndi famiry yanu enjoy ur holiday be calm and relax
Wachamba uyu
Ndiwe wamkulu asamakupusitse
Za ma drama ife ayi
Be serious
Payenera kuti munthu, kapena titi mMalawi akanena nkhani ya sensitive ngati yotereyi osapereka tangible evidence kumtundu was a Malawi, pakhale lamulo loti munthuyo azimuumiliza kuti anene zoterozo kwa atolankhani pa TV, Radio ndi mnyuzi pepala kuti alongosole nkhaniyo ndi kupereka umboni oti ndiyoona. Failing which s/he has to be arrested for committing a "disinformation crime".
Ndipo ndizoona
Mmm kod zikoli likupita kt ambuye yesu bwerani muweluze