Nazombe's history is very difficult, but for a person who does not understand these things, you start to judge her as a prostitute, but He is not. I'm in the Nazombe season again, I've been rained on a lot and now I'm having a hard time.
Gaga u senior wako utenge bwino ukhala nawo mmavuto be careful 🤣🤣🤣🤣 Inuso a Davie, zione kukunkhululukirani ma blunder mbweee Mutaya omwetamwetatu a Davie kumuluza zione Proud of you guys Tipatseni number tivote basi You make my day gud
Mumde is a great actress,,!!!! Malawi got talent
Always lam leaning something from chef William, not just in the comedy only but also in reality zoone He is a chef
gaga asowe Kikikiki. Tonde more fire
Kkkkkkkk nadzombe ndi mbuzi yamunthu sakudziwa CHIMWE akufuna haaaaaaa ifesotu timamufuna m zione uja ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Koma kuli mahule okhaokha uku muthindaso ndiwinaso hule nazombeso hule koma nazombe wekhawe zione uja ndimamudziwa sakulolaso
Gaga iiiiiii🙌
Nazombe is ungrateful guy
The man behind mfumu is a guru...keep shinning
Mukumandinvetsa kukoma zedi from south Africa
Mude wangwilasobyenkha mamama 🎉🎉🎉🎉 snkhan iyi ikupita kwa boh guys waiting kuti xintha bwanj. Guys changu chonde
Mmativetsa kukoma
Kkkk zimveka aaaa ai mu2 sugwra bas nanu che davie tagwran pamoz kkkkkk
Ur the best
Gaga sawundila kkkkk
Kma ziveka icho chifuna iwe sichikidziwika kkkkk aaaa....
Muleke mwana Nd WA tonde
Agaga zinthu zavuta muziona kkkkk
I love make dola
Gaga saundila kkkkkkk😂😢
,azimveka 😂😂😂😂😂😂 koma iweyo🎉🎉🎉🎉
😂😂😂😂😂 Davie zamuvuta wabudula memo wake mapanga awili avumbwitsa ine ndikudikila gaga kuti kutsegoloku zizamuthrla bwanji
Kubeleka mwana ndikosavhuta koma kulela- Zimveka special
Anfumu William mumakwana ngati nfumuyeniyeni
Amfumu mumakwana mfumu yodekha bwino Kwambiri yaulemu wake ndipo mazimfumu midzimu adakakhala ngati amfumu William zikanakhala bwino komaso Atonde wadula pitiliza ndimasewero anu abwino choncho watching from South African
Zione wakwiya chuwa ❤❤❤
Mbambandeeeee comedy series , mumatha guys
NICE
Mude ndiwamaboza hiiiii yaah kkkk
More fire
AMFUMU AWILLLIAM AMAKWANILA 🎉🎉 NDIPO UFUMU UMAWAKHALA.
Davie kujijilika taonani izi
Amfumu vuto lawo ndi chani
Zokut anagumbo ali kuchipatala ukudziwa? Wamunamizira uja nkhalamba yachabechabe ija kkkkk
Zimveka 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂🎉😂😂😅
😂😂😂😂😂😂chiphwanya wavala chipewa cha mwana odwala chibayo
Nyamata wa Joni Ali pamavuto nditu
I luv u guys keep it up job well done ❤❤❤❤❤❤❤❤
Manganizo anga ali pa gaga n kuti kodi zimuthela bwanji
Koma nadzombe ndi tambwali eeee😂
Tiyeni tiwavotere anthuwa
Mbambande guys😂😂
Big up guys
Koma afumu pagaga pokhapa mupangepo kanthu nditu
Zione, panepo ndakumva ndithu.
Mbambande guys keep it up
Yonse 👍
Here waiting for Nagumbo's child😂
Guys you're making it 💪
makhadzi
Koma madola ndi azimveka amakhalana amadola akhuluruke basi
Avide zawavuta basi chagwa kwa dolo
Koma a William ndi fumu yodekha. Zimveka Ali mu madzi
Amfumu mukuichedwesa khani mukatheni gaga
Hiiii koma ziwone❤
Agaga kuzolowela kuba paka mukufuna mube ndi umfumu omwe 🗣🗣🗣agaga
27:37 gaga
tigawileni nambala yovotela
Best comedy tonde wadura
Nazombe's history is very difficult, but for a person who does not understand these things, you start to judge her as a prostitute, but He is not. I'm in the Nazombe season again, I've been rained on a lot and now I'm having a hard time.
Gaga u senior wako utenge bwino ukhala nawo mmavuto be careful 🤣🤣🤣🤣
Inuso a Davie, zione kukunkhululukirani ma blunder mbweee
Mutaya omwetamwetatu a Davie kumuluza zione
Proud of you guys
Tipatseni number tivote basi
You make my day gud
Now Tonde is the best ❤
Watching from antiokeya
Chibwez chivuta ichi
🔥🔥🔥🔥🔥
Moto unandi 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 mukutivesa kukoma
Amfumu osadanda.ndkapeza gaga .ndi menya ndekha 😂
Gaga sungamusiye pa ntchito Kut agwilizile Malo . Ntchitoyo yatha B's ..chizungu chake amati. Fired alone🤣🤣🤣🤣
Nazombe😂😂😂😂😂😂😂
❤❤❤guys MX tonde
makhadzi
Keep up mabwana ndimadona
KOMA ZIMVEKA NDI MACHINE 😂😊😅😮
Koma devie wabwela ndimoto
Nazombe yamulakwila bas😂😂😂😂
Mmakwana guys keep it up ❤❤
Amfumu ndi tonde ndipachibale?
Wonderful
coming back tonde wadula 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 afuna aziwalelela azawo Iwo kwawo ndikuswaa bas akakula avumbuluke Kuti ndiwake 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 koma anthu inuyo
guys inuyo mumakwana musadzasiye kutipasira zabwinozi
Kom misili mavuto sazakuthera
Nazombe
🙇♀️🙇♀️🙇♀️ next musayichedwetse nazombe ichi chakoma ich chakoma pusi anagwa chagada 😂😂😂😂
Kkkk Inde zione wamchita bwino kkkk
Big up🎉🎉🎉🎉
😂😂Koma nazombe . bas2 mkaz uja 🤣🤣
Ine ndiye ndafisira 😂 wandilolaso .ati chathapo bc
Well done my people 💯
Koma asachoke gaga
Usazamuyimbileso Zione 4n Dave ndiwe womanizer mmisili opandazida kkkkkk R.I.P fainess
Guyz mumatinvetsa kuzuna
Welcome Mumde missing
Zione and your sister mumatha
Am here for ndaziona
Koma guys ine nganga amamdiwaza kwambili❤❤❤❤
Zione pepani amuna ndichocho 😭😭
Koma gaga sazatheka
Tanditumizileni nambala yovoterayo pls ,anthu awa amatichosa mkhawa
*364#
D@@nkhalangomultimedia
Komatu pa gaga mukumuchedwetsa tikufuna zimuonekere kikikiikikiiki
Ndipo ndi zomwe ine ndikufuna
Mumatives kukoma guys ❤❤
Amfumu akuchedwetsa kuthamangitsa gaga
Amfumu mukuichedwesa khani mukatheni gaga
Nazombe 😂😂😂
Amfumu mukuichedwesa khani mukatheni gaga