ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Nepman udya mlongo wako uwona kupupuluma kwakoko😂😂😂 Amlelemba nanunso mupwetekana ndi mwana wa landlordFlora suya much respect you❤❤
flora I don't know what you think when you recruit characters... you pick the best I now feel why you took nepman onto stage kkkkk you are best director ma'am!! Maxwell still following
Umakwana napman
Kkkkkkk my favorite mr mlelemba iiiiii ayi ndithu iweyo anakonzatu usazafe uzangosowa 😂😂😂
Koma ndalama sichinthu wamba😂😂 prisica anamulusila nepman kungowona ndalama pomwepo kuyamba kusekelela
Mulelemba sazatheka 😂
Flora iweyo ndi dolo aise 😅😅😅
Kkkkk muluzi wokhawo ndiye umayimbidwa Mr chuma
Mlelemba si zinthu guys kkkkk😂😂😂😂 ati gitala waiwaza anointed water iziyimba mwauzim. Musazafe guy's😂😂😂😂😂
Nayeso shokoshoko.... uku nde kufula uchi masana uku wapalamula njuchi 😂😂
Limenya mtondo belita...kkkkk
Koma zili kwa mdyangu 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂. nepman afusila ssiter wake ukuuuuuuuuu yoooooooo
Queen wawona katundu wa mlamu
Waba gaiter kuno Mdyangu apite ku zbs aitanitxa ana Ake kkk umakwana frora
Ati Nepman wasuta boy thamanga😂😂😂😂😂😂😂
Mafill dephia kkk.. i like your sttyle brazzaaa
Nepman mdyangu umatha
kkkkkkkkkk MDYANGU COMEDY mumatha
Wawo thanks let me injoy it
Queen kwaonela alamwako 😂😂😂😂
A Pastor Mlelemba apasidwa Bible labwino kkkkkkkkkk. Umatha Mlelemba
Queen 😂😂😂
Mlelemba m'busa wabwanji iwe😂😂😂
kkk Nepman ndi one
Koma Nepman 😂😂
Nthawi isamathere pa Nepman
Wow ! the combination of Mulelemba and Nepman is so amazing , Mdyangu comedy please keep it up 👍👍👍
Kikkkkkkkk,zili chabe bwino
The devil is a liar kkkkk
Watching you from Matero in Lusaka Zambia
Talent at its best...you guys rock!
Abusa amulelemba mukweze muchoka pa Sargent to pope..... Muzitchedwa pastor, corpal, Sargent, commander, pope baison mulelemba
Nepman u r best on acting and also your music we are enjoying it here at south Africa
Week ino yachuluka phokoso mulibe zobeba
😂😂😂😂😂😂😂 i like you mulelemba
Nonse ndimakunyadirani guz🎉❤🎉❤
Mulelemba watutumuka
Eeeeh aindithu mulelemba ine chonena ndilibe 😅😂😂
Kkkk koma Jumani akuzionela bwanji 😂😅😊
😂😂😂 bring phwedo aswel
Gd advice Mr mulelemba kkk
Eyaa wa chindendelinde ndi ameneyu
Koma queen iiii
Piladefia wrote!😂
Komatu nepman nawe siuli buino ace 😂😂😂
Kom ching'aning'ani ana owapeza mpaka 8😂
Kkkk koma Mulelemba wathawaso
Anthu anga inu, Pali mlelemba sipanama😂😂😂😂😂
Kkkkkk Qen bwanji kuwonera aramu anu
Phwedo abwere please
nepman on fire
😅😅😅mulelemba ndi nepman aphana
nepman afuna akafikile kutchedwa adadiii 😂😂😂😂😂😂 wagenda katagendedwa kale 😂😂😂😂😂 nepman ft lelemba umenyedwatu ndi Mwana Wa mdyangu 😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Nepman atipha eee
Queen kuwaonera alamu Ako chidwi changa chiri pamenepo ndipitiridza coment yanga ndikazukira buuu lululuuuuu
Nice
😂😂😂😂 nyc
Nepman 😂😂😂
I love you mama Suya
Koma anthu achibwibwi ife eeeee ayi zikomo
😂😂😂😂😂mumatiyimilira guess
Ma verses onama okhaokha akut Joseph ananama
Nepman usalowe za eni ni k20000yako kkkkkkkkkk I see you from Lusaka Zambia😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅
Kkkk abusa athawitsa gitala 😂😂😂😂😂
Kkkkkkk mlelemba
Nepman & muleremba kutengesana sopano😂
Koma queen tsopano
Bambo Defia safusa anadya phula
Mafilidefia m'dyangu
Nepman usalowe za eni ni k20000 I'm watching you from Lusaka Zambia😅😅😅😅😅😅😅😅😅
Mulelemba please,, nkazi alindipathupi uyu'
Mpaka Nepman wapeza yolowera mkazi
😂2days packet ya sugar itha bwanji
Thako limenya ntondo belita😂😂😂
😂😂😂😂😂😂😂😂
Koma Mulelemba kkkk packet ya shuga
Koma Ma Guy Na Iyi Yokha Yapanga Usiku Wanga Kukhala Wabwino Kwambiri...... Flora Suya Mumatha Inuyo
Kkkkk Mlelemba...Nepman akanakupukuta lero😂😂😂😂
Kodi mulelemba ndi uja anayimba nyimbo ya chindendelinde kapena si uyu?
Yemweo
Inde ndiyemweyu mfumu matiki
Boy thamanga
❤
Nepu man akufuna kufungatila mazila?😅😅
Mleremba budget yavuta uyudi ndi January
😂😂😂😂😂😂 mlelemba
Mulelemba Nd nep kkkkkkNaye queen wadyesa Kwa mulamu wake kkkkk
Big ma NEP ma filadefia
Za nyatwaaa
CDM TOUR and TRAVEL 🧳
😂😂😂😂😂😂
Amubela gitter ndani? Nepman apha munthu uku😂😂😂😂
Defia game is over 😂😂😂😂
Kikkk,Mlelemba ndi Nepman musadzachoke mu drama limeneli pls.Mukubwela bwino kwambiri.
Boyii ithamanga 😂😂😂😂😂😂😂😂
Tabwera
Kkk ana amdyangu ayamba kubwera modzimodzi etii😅😅😅
😅😅😅 Kwini mumakwana mpaka kwawonela amula ake
Sandlabakatheni khomvokhovo kkkkk. Boi thamanga
Mlelemba man of God😂,, ulaliki wanu umandisisimusa😂😂
😂😂😂😂😂😂😂
Bodza basi😂😂😂😂😂
Zikomo kwambiri poyitumiza mwachangu lero. Timakukondani.
Queen zoona iweyo kwaonela alamwako kkkkk mumakwana guys
Nep akufuna atafune wa mimba😂😂😂😂
Nepman udya mlongo wako uwona kupupuluma kwakoko😂😂😂
Amlelemba nanunso mupwetekana ndi mwana wa landlord
Flora suya much respect you❤❤

Mulelemba Nd nep kkkkkk
Naye queen wadyesa Kwa mulamu wake kkkkk