Excellent Chawezi. You talked well on stewardship. Zikakhala za MCP ena nkumati misonkho ya anthu, koma zikakhala za DPP aziti lozani zanu, koma yili misonkhoso ya a Malawi.Kodi pali chilungamo pamenepo? Nsanje yachuluka anzathuwa.
I just like his presentation, we need such kind of journalists as a country, osati ma journalists a lazy just getting unverified information from the social media & Wikipedia.
He hits the nail at a right angle, moti tipemphenso apa a Chawezi kuti timenyereni nkhondo boma lisanatulukemo lipereke ndallama kwa nzika zawo anagwira ntchito 30 years ago, anthu 1019 akuwalipira time one M instead of paying them once and for all, ndi a gogo pano can't even send the children to complete education and yet ndalama ziliku treasury ready for Campaign and the money has already approved by Dr Chakwera koma treasury and opc people hold the money till today. Why ???
I like the way chawezi explains most economic issues.. Chawezi, take my hut off... You are great.. but then why are those in government not able to come and explain these types of technical issues by themselves and clear most misconceptions? It would have been exceptional if you and Moses kunkuyu were working hand in hand.. Asamangotinaziza awa a DPP.. Especially" Namalomba"
Excellent Chawezi. You talked well on stewardship. Zikakhala za MCP ena nkumati misonkho ya anthu, koma zikakhala za DPP aziti lozani zanu, koma yili misonkhoso ya a Malawi.Kodi pali chilungamo pamenepo? Nsanje yachuluka anzathuwa.
I just like his presentation, we need such kind of journalists as a country, osati ma journalists a lazy just getting unverified information from the social media & Wikipedia.
He hits the nail at a right angle, moti tipemphenso apa a Chawezi kuti timenyereni nkhondo boma lisanatulukemo lipereke ndallama kwa nzika zawo anagwira ntchito 30 years ago, anthu 1019 akuwalipira time one M instead of paying them once and for all, ndi a gogo pano can't even send the children to complete education and yet ndalama ziliku treasury ready for Campaign and the money has already approved by Dr Chakwera koma treasury and opc people hold the money till today. Why ???
I like the way chawezi explains most economic issues.. Chawezi, take my hut off... You are great.. but then why are those in government not able to come and explain these types of technical issues by themselves and clear most misconceptions?
It would have been exceptional if you and Moses kunkuyu were working hand in hand..
Asamangotinaziza awa a DPP..
Especially" Namalomba"
Much understanding
Ndimaona ngati uli ndi nzeru Chawez wadya banzi za ziiiiiiiii
Akusaka u mp
Chawezi is the best ever and school is good
Palibe za school apa mukazaimvetsetsa economy ya dziko muzaziwa kuti kuti uyu amangolongolola apa
Chawezi without looking at him with political eye...he knows this.
We need such kind of journalists who present their arguments with facts & evidential recommendations
Eversince Chawezi has never criticized MCP government. But I don't blame him government always change.
Chawezi ayi ndiwe wazeru you can explain ndipo ndakumvesa
Chawez ndiwe wa mcp
Kkkkk chaweza umakwana iweyo 🫡🫡🫡🫡 ena adaiwala kuti dan lu amaloza zachipani kapena zaboma 😂😂😂😂😂😂
Yowoyani Banda ,nkhumupulikilani kuno ku Robins Island Cape Town
Chawezi ndi mashine
Devaluation amapangitsa ndi ndani, kuikira kumbuyo zachabe
Km awawa amawonetsa mbali ndipake enafe sitikonda zomwe akunena
Ndiye akunena zabodza?
Chawezi ndi spokesperson wa MCP.
But Dausi Chawezi laba bafundile se s' kolweni siyazwa kakhulu ,
Sindikudziwa ngati utazalankhule chomcho after 2025 ndi boma laku lakuphali
CHAWEZI MABODZA😂😂😂😂
Koma chawezi ndidoro
Odana chakwera ndi mfiti.ozolowera ma bodza.
Chilungamo chimapwekeka auze Chawezi
AIP subsidies koma munthuwe 33% of your budget ukutenga ngongole. Freedom will never come to a debt government
Awa ayibereka mcp ndi shawel
Chaewzi banda is educated savage. He 100% show that he is mcp representative.. hes making this nice shows to look bad..
Zulukomela mbali imodzi Koma.
Chimene chikugwetsa kwacha tiuuzesoni mwina mkudziwa zeni zeni.
Ine Bwande pano sandikomelanso
Apa palibepo Bwande, uyu Sandram.
Akuluwa nga mcp...ndpo i dont understand kt bwnj prgrm yanuyi muzkapanga ma MBC...get out chawez
Kodi inu amibawa bwanji mumakonda Kumamuika chawezi yekha bwanji?
Munthu uyu definitely Ali ku MCP inuyo,vomerezan kt boma ili langongola ndalama zochuluka,ndipo muzane sitikuyifuna ife MCP achoke
Akulu awa akuwoneka ngat ndiwamzeru km ndi mbuli kwambiri,
Machende ake chawezi
Inunso ofunina muunguze za ndege ya Chilima
Chawedzi always Government side..he never be balance...try to be balance or bring two analyst
Zoona
Chawezi ndiwe chaboza boma lakongola chomene ili iwe Ute waka ukurya nawo
Total lie now debt has risen from 5 trillion to 16 trillion. This is 300% increase.kodi kwachayo yapangidwa devalue ndi 300%
.Malawian dont like this man
Don't say Malawians, say you don't like this man.
As long as MCP still there Malawi will continue being poor 😂😂😂
You are a great liar
Sukuona mmidzi zomwe zikuchitika athu pano limbika akusangalala