ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Koma kuli kanthu kumeneko falai wabwera bwino.koma mwati Queen mpaka anadyana plain ndipadela kkkkkkk more fire mfumukazi ndi banja lawo chikondi chafikapo.together as one gling'ande kkkkkkk
Asaaaaa ntchito ndiyosayamba frayi takulandirani ndipo wayiyamba bwino chiberekero chipezeka bwanji nankha wa kumiting mfumu nkazi anayenda bwanji nankha padera zitha bwanji ndalama ya queen anayipereka ? Ine pheeeee kudikira pa 7 moto buuuu ❤
Kulukikiza kwabwino ndi mdyangu big up kan chibelekelo anachosa ndi ameneyi et 😂😂😂 nice proud of u gyz
Falayi akufanana ndi princess.
Amaliro ndi afiti, chiberekero abwwretse😂😂😂😂
Ka banja ra Mr sharp linagwira kkkkkkkkkk galingale wasinadi
Chibelekelo munatenga pena mulibe kkkkkk😅😅😅😅😅 nkhani yachibelekelo yavuta basi kkk
Inu mutipweteka ndi kuseka😅😊 Mr ShopRite ati cibelekelo ulinaco olo ulibe please continue good work am in Lusaka Zambia conde pitilizani
Koma queen wati apadera anagwira ma network 😂😂 ndiye mpaka sanavale anadya choncho koma queen usazafe uzangosowa❤❤
Princess ndie wanenepa2 eshi nc nc
Ulindi zaka zingat HOW OLD (apa ndabwerezapo kangapo kkkkkk)
Kkkkkk princess🔥🔥🔥🔥, good job guys
Thanks you
apapa Mdyangu ndi Mfumukazi zaphatikizana basi ndikuona maliro atatulukilanso mu mdyangu comedy🤣🤣🤣🤣
Ndzomwe ndikuona kkkk
Princess chitsulo nanunso mwalowa mu drama
Mumatiyimira guys here from zambia
Limenelo nde funso laziii, nanyoni my goon mama
Maliro ndiemwe anagulitsa chibelekero cha sindi 😂😂😂😂😂😂😂ndikuiona mdyangu v/s mfumu kazi mukuitha koma
Imfe sitikupeza tchito ataaaa chilomwe
Chibelekero cha sindi pelekani mzanu akhaleko ndimwana😂😂😂😂😂😂
Maliro ubwenza chiberekero cha Sindi ndithu😂more 🔥 Ngiring'ande
Maliro anagulisa chiberekero😂😂😂😂Km ndetu kkk ndekt mulelemba abwera so eti kkk😅😅 I can't wait next week 😊
Nkhaniyi plz musaisakanize ndiyaku mdyangu mutisokoneza
Komano Am not sure kuti nkhani ilumikizana bwanji kutengera kuti maliro was already mu Mdyangu ngati wakatapila
Maliro, sinditu akubwera kuchokera komwe kwa amdyangu azatenge chibelekero chake kkkkkk nayenso mulelemba akufunako mwana kwamdyanguku kkkkkkmukumazitengatu bwino guys srs
😂😂😂 Maliro wovuta, Cindy plus Mlelemba kkkkkkk kaya tiziona komwe zithele
Wellcome presence and Ellen
Mfumukazi siosewera naye😂i can't wait for the next episode❤
Farai wakuNamiwawa🤣🤣🤣🤣Princess more fayaaaa
Welcome princess this is gonna be fire
Mfumukazi kwagwesa abambo zoona kkk
Koma Farai amene ndie wabwera mwalatu
Kkkkkkk koma apa ndiye mukuzikwanitsadi zikukomatu ...
Very nice video
Princess sanabwere bwino 😅😅😅
kkkkkkkkk komatu kwavuta zedi kumeneko mukundivetsa kukoma zedi kuno ku Moçambique tete tsangano
So Sindi is coming to mfumukazi,well connection
Maliro,mapwepwete omangila trouser mkuzi🤣🤣🤣🤣
Apa nde zilibwino 😅
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣queen ati sanatchene
Mayi padela kufusa queen at anatchena kapena dzinazo nae queen at kidabwa dzinazo ndie dziti this s good combination ya mfukumdyangu comedy
Koma mai padela amatha act kwambiri ulemu wanu mai
Queen that too much mpakana yakwa 52 pin 😂😂😂😂
Kkkkkk
Falayi❤
kodi Chiphwanya adasiya kupanga nawo..?
Koma ndie mabwera moto kuti mbuu
Ndiye mayi padera mulipira ndalama ya chani 😂😂😂
Mfumu kazi umatha ❤❤
Plus devaluation 😂😂😂koma queen
Koma maliro 😂😂😂
😂😂😂😂😂
Ereni tinakusowa
Mr Maliro akuti azingoti Manze 😅😅
❤🎉
Koma manzee
Welcome back falayi😅😅😅😅😅😅
Fumukaz umakwana
Aaaa ai zanachene km queen🤣🤣🤣🤣🤣
Umakwana
Queen is nuclear weapons😂😅 Likiliki keep support Flora
❤❤❤❤
Comedy ili bwino zed koma vuto emwe amayika subtitles 🤣 eeee akayambile chizungu chomwe chikutuluka ndizomwe akuyakhula muthu zikumasiyana kwambili plz koposa musamayike subtitles yo
Farai she looks like Princess Chitsuro🤣🤣🤣
Komatu khwiniyu ndiye zamuyanja mu mdyangu kumpasa gawo ngat la achina Mercy mu mfumukazimunso nkukhala Mercy weniweni? Akut sanatchema🤪🤪🤪
December is yabooka time 😂
😂😂😂😂😂😂😂😂how old😂😂😂😂😂 koma Maliro kkkkkkkk
😂😂😂😂 komatu guys mumakwana ❤
❤
Manetwerk omwewo 😂😂
Sanatchene
😅😅😅😅😅
Falayi yemweo
Flora umativesa kukoma
Hooooooo ziliko midzi iwili yoyandikana bas
Uncle Manze 😂😂😂
kkkk kod osatchena ndi interest+devaluation eti?
Princess 🔥🔥🔥🔥
Kodi maliro nsapato yake anabwezeredwa?😂
😂😂😂😂😂😂Mfumudyangu😂
Guys mumatha heavy
apadera anatchena koyamba
Chavuta chibelekero
Aphalura Maliro, share yake sanalandire Maliro
Falayi i need your number very beautiful... Wamutha maliro😂😂😂

Maliro, sinditu akubwera kuchokera komwe kwa amdyangu azatenge chibelekero chake kkkkkk nayenso mulelemba akufunako mwana kwamdyanguku kkkkkk
mukumazitengatu bwino guys srs