ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Ras Chikomen plus Denis Mahata 🎉🎉🎉
Kulankhula mwanzuru Mr chikomeni...umatha heavy kulankhula🎉🎉
Respect honorable from liwonde fire rose again
My candidate has come. You have my vote
You have my vote.
2025 Bomaaaaaa!!!!!
Tha's good rasta chikomeni u can go start house
The choosen one ,
More 🔥🔥🔥 Raster chikomeni let's go to chakwela house
Bola kuononga data kumvera a Chikomeni Chirwa osati Beni Longwe kulankhura moziluma luma kulephera kutambasula bwino bwino,kulankhura mwacheu cheu ngati akuopa kubooledwa maso
Yeh yeh rastaman🤛
Ganja Government is coming pa 16 September pompa
Mfundo kuposa ochakwera😂
Chikomeni my vote 😂😂😂
2025 bomaa🔥
Mahata apange alliance ndi chikomeni
Apule wanthuwanthu uyu pa 16september
That's good
Kuyendetsa boma sikulima chamba...politics is a serious business...Koma school ilimo?
😂😂😂 chamba Chija osazaphweketsa kkkk
Kumalawi kuli zithu😂😂😅😮
Nanunso bwenzi mutayamba kugawa cannabis 😆😆😆🤪
Viva Chikomeni 2🔥25 boma!!!
He brilliant guy
Zachamba basi.zaganja muno malawi ayi
Awatu kulipo kudzatikakamiza kuti tonse tidzidya zomera 😂😁😂
@@abdulsalammkwepu3321 hahahaha komaditu
Bolani chikomeni not usi
Shikomen ndioganisa kwambiri
Koma uyu akanakhara kaye mp bwezi ku parliament kukubeba kwambili
Mzelu kuposa chimwendo Banda, Jessie Kabwila
CDM YOUR RELIABLE CAR DEALER
Mumakwana apure
Komatu munthuyu ndiwadzelu kwambili shikomen
Si kape
Inu tiyen tidzingosuta chambachi bas osati ndale
Ada awa ndi a nzeru
Koma amalawi amene anatilosayo ai zikomo Koma kwayineyo mwauyuyu ine mulibemo ndtu
Jah Rast 😂 don't smoke too much just drink water 😅
😂😂😂😂 Sitikufuna asogoleri oziwa kulankhura tikufuna asogoleri odziwa kuchita chikomeni chimanga mukugawa kuti and bwanji mukuonda mwadya kwambili kanabasi😂
Kkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkKoma timva zinthu
Uyuyuy ndiwabodz Ngat tamusankha msogoler ndiy sakuchit zomwe amalaonjez ukuganiz kt Anthu amusankhayo angokhal chet kudikir nthaw yakampen ? Komanso chot udziwe nchakut mtsogoler amalandir ulem ngat iyeyo akuchit zabwino kwa Anthuo
Umakwana rast chikomeni 2025 BOMA
Fumu yafika tsopano
Fodya
ngati munthu sakuchita bwino ayenela kunyozedwa osamasekelela zinthu zikamapotoka muzampha nazo ana dziko chifukwa cha sogoleli wakuba
Ganja government woyeeee 😂😂😂
Selassie i
Tingopitiliza kubema vwamba amwene
Ndikubotera rasi lneyo tizizasuta rimodzi
😂ndipo tizizabanda momasuka
Kkkkkkkkkkkk
Ras Chikomen plus Denis Mahata 🎉🎉🎉
Kulankhula mwanzuru Mr chikomeni...umatha heavy kulankhula🎉🎉
Respect honorable from liwonde fire rose again
My candidate has come. You have my vote
You have my vote.
2025 Bomaaaaaa!!!!!
Tha's good rasta chikomeni u can go start house
The choosen one ,
More 🔥🔥🔥 Raster chikomeni let's go to chakwela house
Bola kuononga data kumvera a Chikomeni Chirwa osati Beni Longwe kulankhura moziluma luma kulephera kutambasula bwino bwino,kulankhura mwacheu cheu ngati akuopa kubooledwa maso
Yeh yeh rastaman🤛
Ganja Government is coming pa 16 September pompa
Mfundo kuposa ochakwera😂
Chikomeni my vote 😂😂😂
2025 bomaa🔥
Mahata apange alliance ndi chikomeni
Apule wanthuwanthu uyu pa 16september
That's good
Kuyendetsa boma sikulima chamba...politics is a serious business...Koma school ilimo?
😂😂😂 chamba Chija osazaphweketsa kkkk
Kumalawi kuli zithu😂😂😅😮
Nanunso bwenzi mutayamba kugawa cannabis 😆😆😆🤪
Viva Chikomeni 2🔥25 boma!!!
He brilliant guy
Zachamba basi.zaganja muno malawi ayi
Awatu kulipo kudzatikakamiza kuti tonse tidzidya zomera 😂😁😂
@@abdulsalammkwepu3321 hahahaha komaditu
Bolani chikomeni not usi
Shikomen ndioganisa kwambiri
Koma uyu akanakhara kaye mp bwezi ku parliament kukubeba kwambili
Mzelu kuposa chimwendo Banda, Jessie Kabwila
CDM YOUR RELIABLE CAR DEALER
Mumakwana apure
Komatu munthuyu ndiwadzelu kwambili shikomen
Si kape
Inu tiyen tidzingosuta chambachi bas osati ndale
Ada awa ndi a nzeru
Koma amalawi amene anatilosayo ai zikomo Koma kwayineyo mwauyuyu ine mulibemo ndtu
Jah Rast 😂 don't smoke too much just drink water 😅
😂😂😂😂 Sitikufuna asogoleri oziwa kulankhura tikufuna asogoleri odziwa kuchita chikomeni chimanga mukugawa kuti and bwanji mukuonda mwadya kwambili kanabasi😂
Kkkkkkkkkk kkkkkkkkkkk
Koma timva zinthu
Uyuyuy ndiwabodz
Ngat tamusankha msogoler ndiy sakuchit zomwe amalaonjez ukuganiz kt Anthu amusankhayo angokhal chet kudikir nthaw yakampen ?
Komanso chot udziwe nchakut mtsogoler amalandir ulem ngat iyeyo akuchit zabwino kwa Anthuo