ไม่สามารถเล่นวิดีโอนี้
ขออภัยในความไม่สะดวก

20 JUNE BOOON KALINDO 🫣🙌

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 18 มิ.ย. 2024

ความคิดเห็น • 19

  • @iamandypandy
    @iamandypandy 2 หลายเดือนก่อน +3

    Thank you Mr president

  • @Luxemaven8686
    @Luxemaven8686 2 หลายเดือนก่อน +1

    Keep up with your audios DC....You make my days. You always drop facts.

  • @Luxemaven8686
    @Luxemaven8686 2 หลายเดือนก่อน +1

    Bon Kalindo! You have gained a fan.

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo 2 หลายเดือนก่อน +2

    Ing'aluleni Mr DC, enanso tikapanga comment ngati choncho akumatitapa mkamwa, tsono adziwe kuti this not 1960 this 2024 auzeni

  • @MarvellousTech-kz6no
    @MarvellousTech-kz6no 2 หลายเดือนก่อน +2

    Abon kalindo , chaka cha mawa dzakhalen pampando wa upresident mudzalamulire dziko ,kuti ena adzakambeko zayinu kuti ndinu abwino,

  • @IshmaelJohn-iz1ej
    @IshmaelJohn-iz1ej 2 หลายเดือนก่อน

    Mumakwana uncle

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y 2 หลายเดือนก่อน

    Good Messnge Bon Kalindo Chakwela you mast go

  • @anthonynkhoma4265
    @anthonynkhoma4265 2 หลายเดือนก่อน +1

    Za ziii kufuna kutamika. Paja a dpp munazolowera kulowetsa ndale pa maliro. My vote for Chakwera

    • @Zelinakhisswell
      @Zelinakhisswell 2 หลายเดือนก่อน

      Palibe anapanga ndale pamaliro zakunyasani chifukwa CHOTI chakwera anakuwidwa nde zinakudinyani, mwaziotchera nokha CV mkupha kwanu anthu amangofuna ukudziwitsan kt saliso mbali yanu . Ndale amapanga achina chimwendo ku mpoto anthu alimuchisoni vp asanaikidwe komwe thank God anthu Akumpoto pano akuzindikira anawakanira kupanga msonkhan 😅

    • @YoungKhakhizo
      @YoungKhakhizo 2 หลายเดือนก่อน +1

      Pamtumbo pako iwe ndi MCP yakoyo

  • @Luxemaven8686
    @Luxemaven8686 2 หลายเดือนก่อน

    Koma ng'ona zimenezi decades later osasintha ufiti? Ndipo ku AG ndinapitakodi simukunama chisoni chinandigwila azigogo akuvutikila ndalama zawo. Mpaka angapo ndinawagaila transport yobwelela

  • @RaymondKaumba
    @RaymondKaumba 2 หลายเดือนก่อน

    Unali MP kwanu kwa Njeza
    Unapanga chani cha nzeru
    Pano uwoneke ngati uli ndi nzeru.
    Azanu anapeza zochitatu
    Inu milomo mbuu
    Palibenso chanzeru mukulankhula.

  • @fannyzimba149
    @fannyzimba149 2 หลายเดือนก่อน

    😭😭😭😭😭😭

  • @user-ux9ik4zr5x
    @user-ux9ik4zr5x 2 หลายเดือนก่อน

    Dobadoba wa Dpp,Can you look for something to do so that your Children can inherit when you die?

  • @user-pt8wb4vw6r
    @user-pt8wb4vw6r 2 หลายเดือนก่อน

    Popano iwe kalindo umayambana ndi autm tiziti ndiwe munthu wanzelu kalindo ndiwe opasula kukumana udindo chikhale chifukwa wosauka akava kunyozako ndiye kuti wathandiza zokusatilazo ndi achamba anzako ndiwe woopyad umapha anthu kunamila mcp chifiti ichi naweso uzafa zauchisilu kambwe galu zikutiwaws

    • @RhodneyBwa3
      @RhodneyBwa3 2 หลายเดือนก่อน +1

      Akutuma mn musiyeni ayankule

    • @Zelinakhisswell
      @Zelinakhisswell 2 หลายเดือนก่อน +1

      Tili mu democracy n everyone has got freedom of speech so leave kalindo alone , musamapake azanu zinthu zoti mwapanga nokha even mwana akudziwa kt MCP motsogozedwa ndi chakwera mwapha chilima ndi anthu ena 8

    • @stunahethibwi1112
      @stunahethibwi1112 2 หลายเดือนก่อน +1

      Ndiye opepelatu ndnuo man😂😂