ไม่สามารถเล่นวิดีโอนี้
ขออภัยในความไม่สะดวก
Cruise 5 with Lucius Banda
ฝัง
- เผยแพร่เมื่อ 6 มี.ค. 2018
- Malawi’s most celebrated and versatile musicians and politician Lucius Banda talks about his highs and lows of his musical career, his time in prison and his political ambitions. He talks about how he thinks he is the better man to lead the UDF and how he believes the current leadership of Atupele Muluzi is not inspiring. He does not hide that he has presidential ambitions and that he is confident he will rule Malawi one day.
Lucius Banda mnayamba kukonda nyimbo zake ndili mwana ,wapita msanga ambuye landilani mzimu wake😢😢😢😢😢😢
Lucius banda your such a great and courageous man. I see bright future in ur leadership my God place his hands on ur plans.
koma abale ngati padziko lino pali anthu amene amatsatila maimbidwe anu komanso kukonda luso lanu, ndine kuno kuzambia moti ndimalakalaka kuti ndikakuoneni maso ndi maso. pemphelo langa ndilakuti mulungu akonze njila kuti mwake muno tikaonane basi nice interview thank you.
Mr Banda u really from where people stays, thats why we suport u
No one and no body will change Malawi but let the will of God be, and I wish him good luck for his dreams to be fulfilled.
I respect Lucius Banda as the best musician in Malawi.
you all prolly dont give a damn but does anyone know of a tool to log back into an instagram account?
I was dumb forgot the login password. I would appreciate any assistance you can give me!
@Zaid Lionel Instablaster :)
Yes lulu his future of music
Nice interview you really do your research on questions you ask very interesting.. keep it up.
Rest in peace legend
Timamvera ochuluka program iyi please tamalankhulani chichewa
Lucius great musician
God is good, timakunyadilani bwana Lucius.
My future leader I hope so
Am always encouraged ndikamanvera interview ya Soldier Lucius Banda
Alexander Ntawanga amangoyankhula mtima uli zii
Ndikuuzani Chemwali adakakhala kuti mwina alipo anthu angapo ngati amenewa mwina bwezi zinthu zitasinthako
Alexander Ntawanga zoonadi
Rest in peace sir soldier Lucius Banda
Mr solder i like you
Kunena zoona, bwana speech yanu ikundipasa chidwi. koma chomwe ndinachiona ndichakuti asogoleli amayambabwino. Koma vuto ndi pressure yochoka kwa anthu. Pena aja amati ma advisor. Kodi inu simuzakhala ndi ma advisors? Will you stand? This pressure sometimes comes from party members. Will you not listen to them? Will you stand for final conclusion in evething? Should we trust you? Finally l say, keep fighting. It seems.....
That's nice chart koma chonde muzilora kuti tiziika ku offline please
I can see tsogolo in this man
Thats true Lucius Banda .
Soja the Legend!
Paja mukumati khoswe sangakhale mfumu ya mbewa eti? I think Lucias and manganya can change MALAWI positively
U think so...?? Ok...
our generation president
My pleasure Mr chakhaza
Mumatiimilira soldier
Palibe zotukwana apa kungonena kuti yankhulani chichewa aliyense ali ndi manyi,umunthu ndiofunika abale.
Nde anali wamzeru😢
Big boss
ndizowonadi nkhani zilibwino ndipo timakunyadilani komano muzitha kumayika Ku offline tizitha kumaonelanso pena tikakhala opanda WiFi
We're crying about death of lusius banda we was too much loving him until now I can say R.I P
Bwana lucius nyimbo ya nthawi mmmmmmmm munandimbira bwino kwambiri
zakukhosi mmm adapha
Ulibo
mumakwana olemekekeza
Amwene a Chakhaza muli booooo.
Mateus Frezala mulipo yeti?
Sleeping cat never catches a rat
Have u ever smoked weed?Lol. What a hard questions
Koma amwene a Chakhaza mafunso amene mumapereka kwa alendo anu mu cruise5, eeeeheee, mulibe mantha???!!
Please Mr chakhaza anthu ngati awa muziyika mchichewa akuimirira anthu a kumudzi ndye English yo mmmmm
Amenewa tinacheza nao mChichewa ndi chizungu chomwe bwana.
+Joab Frank Chakhaza chakhaza pls is it possible to send me cell number for Mr Napoleon Dzombe on WhatsApp?mine iz 073 164 8232 plz
+Joab Frank Chakhaza I know it's wrong parking but plz
Its not only chewa 24:45 people that watch cruise 5 so its fair enough to use English and chewa😊
Manyianu bwanji mukuyankhula English pamaso amalawi
Kkkk
Control ur tongue
Mmmm koma chakhaza yoh ulibe mantha pofusa mafunso yoh