VICE PRESIDENT MICHAEL USI KUGAWA NDALAMA MU NSIKA WA BVUMBWE BOMA LA THYOLO

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 6 ก.ย. 2024

ความคิดเห็น • 61

  • @mwaiwaobanda2691
    @mwaiwaobanda2691 หลายเดือนก่อน +2

    Tijuferanji last part kkkkkkkkk

    • @Betty-fe9ql
      @Betty-fe9ql หลายเดือนก่อน

      Final episode 😂😂

  • @amoschataika7440
    @amoschataika7440 หลายเดือนก่อน +2

    Apolicewo azidya osamangozungulira nawo dzuwa lonse.

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 หลายเดือนก่อน +2

    Inu mukusekerera misonkho yanu ikuonongedwa iiiiiii

  • @EviChio
    @EviChio หลายเดือนก่อน +2

    Zaumbuli zenizeni

  • @esaMoha-dm4kj
    @esaMoha-dm4kj หลายเดือนก่อน +2

    Amanganya mwayyamba missalla kd bwanji sophano

  • @ThokoGomeza
    @ThokoGomeza หลายเดือนก่อน

    Asaiware kusunga ndalama zogulira chimanga chano chifika pa 80 pin

  • @MuhammadSamson-yz1kl
    @MuhammadSamson-yz1kl หลายเดือนก่อน

    Uyu amatuma chakwera akufuna ma vote apite ku central region aaa amanganya pitani ku mangochi mukagawe akakulandina mwantsangala koma no vote for chikangawa party

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 หลายเดือนก่อน

    Ndakhala ndikukumana ndi Michael Usi mundege atakwera kuja kolipira anthu olemera more than 5 times. Lero akunamiza anthu Mac-Hendie-son uyu.

  • @ishmaelchingwalu
    @ishmaelchingwalu หลายเดือนก่อน

    M'malo mongotenga ndalamazo ndikupereka ngongole kwa a business wo

  • @brainsmkumbwa6267
    @brainsmkumbwa6267 หลายเดือนก่อน

    Agawe ndalama olo asagawe koma chaka chamawa MCP ndi Chakwera akuchoka

  • @user-cd4df3vg4y
    @user-cd4df3vg4y หลายเดือนก่อน

    Misokho yathu mwatengera kumapangira kampeni pomwe zipatala makhwala mulibe athu opanda nzeru.

  • @georgemponda
    @georgemponda หลายเดือนก่อน

    Koma mphwanga Mangaa zausilutu ukupangazo wanva😂😂😂

  • @user-ih7li3im4s
    @user-ih7li3im4s หลายเดือนก่อน +2

    Zopusa izi

  • @masterchitabwino898
    @masterchitabwino898 หลายเดือนก่อน

    Ndinanena nthawi ina yake kuti atifuna azitigula tomato si izi

  • @paulnyondo7572
    @paulnyondo7572 หลายเดือนก่อน

    Koma awa i thing anayesa kuchairilatu .

  • @TiyanjaneKapalamula
    @TiyanjaneKapalamula หลายเดือนก่อน

    Ndalama mzake ma 1000 amatani kumangawa ma 5pin

  • @user-lp8wj3vq4x
    @user-lp8wj3vq4x หลายเดือนก่อน +1

    Kkkkklk.tikufelanji part ....
    Kkkkkk

  • @PaulvinMhango
    @PaulvinMhango หลายเดือนก่อน

    Mzimu wachilima ukuyendayenda pano apenga

  • @Jibsan-t2f
    @Jibsan-t2f หลายเดือนก่อน +1

    Zikusonyezeratu kti office ya vp.sikugwilitsidwaso ntchito. Mamganya mwaro molowa mu office nkupanga zao office. Akungoyendayenda chochi sizoona

    • @tamalangoma2765
      @tamalangoma2765 หลายเดือนก่อน

      Inutu ndinu abodza, ajawa mumawakonda aja akupanga chani?

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg หลายเดือนก่อน

    Chilima anapanga report ya ma reform kut dzikoli lisinthe, koma Chakwera ndi nduna zake anasankha kulikhalira kusafuna kut zikoli lisinthe. Lero akukhalira kuyenda, kodi maulendo amenewa akuononga ndalama zingat???? Kupusa kwathu tili busy kuombera m'manja zimenezo. Nduna zikuba sakuziyendera or kuzidzuzula koma ali busy kuyenda m'aboma shame on you Usi.

  • @CarloBasikolo
    @CarloBasikolo หลายเดือนก่อน

    Zoopsa anthu akusowa ndalama , mankhwala ayi zkm

  • @Eagle783
    @Eagle783 หลายเดือนก่อน

    Koma Manganya kuzunza asilikalitu uku aaaaaaaa 😅😅😅😅😅😅😅😅i think He is overexcited

  • @user-ul5hh3cz8z
    @user-ul5hh3cz8z หลายเดือนก่อน +1

    Zochitisa manyadzi kwambili kumalawi azeru asatuka zisilu

  • @ishmaelchingwalu
    @ishmaelchingwalu หลายเดือนก่อน

    Koma asilikali nde akunzunzika ndithu

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 หลายเดือนก่อน +1

    Inu chani chimenechi iiiii

  • @Qiraa.m
    @Qiraa.m หลายเดือนก่อน +1

    Wayamba zibwana mwanayu

  • @MaryNyirenda-nq3mh
    @MaryNyirenda-nq3mh หลายเดือนก่อน +1

    Ndalama zija abale inu 😢😢 misonkho ya Malawi

  • @DorrahBanda
    @DorrahBanda หลายเดือนก่อน

    Amanganya muli ndimphumatu mmmmmm

  • @user-vl8uw8mc3u
    @user-vl8uw8mc3u หลายเดือนก่อน

    Apenga misala awa panopa

  • @JuniorHala-vf9ov
    @JuniorHala-vf9ov หลายเดือนก่อน

    Kodi manganya ndizomwe ankafuna kut ma drama aja azikapangila ku boma asilikali busy kuyenda yanda zopanda future koma ziko lathu p

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 หลายเดือนก่อน

    Za ziiiii kusowa zochita eti zimenezi ndizitukuko zimene tizazikumbukira yitachika MCP 2025 😂😂😂

  • @GestardKamanga
    @GestardKamanga หลายเดือนก่อน

    Shem malawi

  • @DalitsoMatope
    @DalitsoMatope หลายเดือนก่อน +1

    Ukazipasa ulemu ngakhale ana amakupasa ulemu,,,,,manganya ndi chakwera amalawi vote yanu yakunyozeserani dziko lanu lero lasanduka dziko lokhala ngati chipatala cha Mental kuzomba

  • @ChisomoMsiska-oi2vg
    @ChisomoMsiska-oi2vg หลายเดือนก่อน

    Koma chakwera kusankha usi anaganiza kwambiri wasankha munthu wa nzeru enanu sanje chabe

  • @TaniaMphalumo
    @TaniaMphalumo หลายเดือนก่อน +1

    Ku mzimba mulutenge pa uli

  • @user-ul5hh3cz8z
    @user-ul5hh3cz8z หลายเดือนก่อน +1

    Anthu mwayamba kuwatenga dzisilu

  • @SaidiMilaji-dk8sr
    @SaidiMilaji-dk8sr หลายเดือนก่อน +1

    Kkkkk nzimu wa saulosi abale anthu apenganao 😂😂😂😂

  • @user-mb4tc2dx1p
    @user-mb4tc2dx1p หลายเดือนก่อน

    Koma sangakhale akujambula sewelo nkuluyu?😂

  • @Betty-fe9ql
    @Betty-fe9ql หลายเดือนก่อน

    Komatu 😂😂😂 ati mchani

  • @benjaminbanda-y3u
    @benjaminbanda-y3u หลายเดือนก่อน +1

    Is this a leader or a dramatist is this the way Malawi is going to runned by dramatically shame

  • @Sabina-hw4js
    @Sabina-hw4js หลายเดือนก่อน

    This is proper drama

  • @VictoriaWilliam-ms2ft
    @VictoriaWilliam-ms2ft หลายเดือนก่อน +1

    Manganya ndiye chani ichi?
    Ndalama akuti kumalawi kulibe Koma izi mukuzitenga kuti?

    • @TamikaKaponya
      @TamikaKaponya หลายเดือนก่อน

      Misonkho yathu yomwe iyi inu

  • @billeyjuma-phiri474
    @billeyjuma-phiri474 หลายเดือนก่อน

    Idyani ndi zanu

  • @JuniorHala-vf9ov
    @JuniorHala-vf9ov หลายเดือนก่อน

    Akufuna kuoneka wanzeru kwambili than chilima saziwa kut ku anthu odzindikila ngat ine akupepela kwambili bola tikufelanji uja ankapanga ndi boooon kalindo mwana oopsa kwambili

  • @allansili-rc9gc
    @allansili-rc9gc หลายเดือนก่อน +1

    Munthu wandale amatha kupanga chilichose kufuna kukopa anthu koma musayiware zana

  • @victorkachepa3515
    @victorkachepa3515 หลายเดือนก่อน +1

    Kkkkkkkk

  • @KettieJameson
    @KettieJameson หลายเดือนก่อน

    Is this really necessary?

  • @PatriciaTikhiwa
    @PatriciaTikhiwa หลายเดือนก่อน +1

    Abale manganya nde antaaaaa iye ati chan??

    • @sheila5812
      @sheila5812 หลายเดือนก่อน

      Handiziwa 😂😂

    • @PatriciaTikhiwa
      @PatriciaTikhiwa หลายเดือนก่อน

      @@sheila5812 kkkkk

  • @SimonJesimani
    @SimonJesimani หลายเดือนก่อน

    Zopanda tsogolo

  • @LonnieMdulamizu
    @LonnieMdulamizu หลายเดือนก่อน +1

    Koma azikwanisa?

  • @ChifundoChiwanda-ru3pg
    @ChifundoChiwanda-ru3pg หลายเดือนก่อน +1

    😂😂😂

  • @user-rs7vx6hc1k
    @user-rs7vx6hc1k หลายเดือนก่อน

    Za ziiiii zimene akupanga!

  • @ClydeNyasulu-tk6fj
    @ClydeNyasulu-tk6fj หลายเดือนก่อน +1

    😂😂😂😂iyi ndimisara sopano koma alindi phuma hmmmm koma tiona zinthu

  • @MadisonMagesi-t8f
    @MadisonMagesi-t8f หลายเดือนก่อน

    Zaugalu bas

  • @vicshyma5644
    @vicshyma5644 หลายเดือนก่อน

    Rubbish