DAN LU - CHAKWERA (NEW SONG NOW OUT) NYIMBO YOYAMIKIRA ULAMULIRO WA PRESIDENT DR LAZARUS CHAKWERA

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 20 ก.ย. 2024

ความคิดเห็น • 204

  • @CharlesGremu
    @CharlesGremu 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +5

    Awa last week ija amalira kuti anthu sakukonda nyimbo zawo akuluwa alibe gud guidance and akupha carier

  • @WillyTembo-hq4fe
    @WillyTembo-hq4fe 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +5

    Shaaa koma wapala heavy kapeyu though money exchanged hands koma nde wapala wathera pomwepa.

  • @JohnKenty
    @JohnKenty 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +6

    Dpp my vote 💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙

  • @JessicaManda-zm1ug
    @JessicaManda-zm1ug 54 นาทีที่ผ่านมา +1

    Akuwapusisa achikangawa uyu mumuwonaa azatulukaso kuzapita komwe kul ndalama.
    Dpp my vote 🗳❤🎉🎉🎉🎉

  • @williammenard48
    @williammenard48 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +4

    Rest in internal perfect peace Grace Chinga 😢😢😢😢
    Munatisiyila mau, I just want to say zomwe munatiuza zija zikuchitika mom once again rest in peace 😢😢😢😢😢😢

  • @arafatMtyala-bo8ev
    @arafatMtyala-bo8ev 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +5

    Dan lu wapala ndinyimbo iyi, lozani zanu ndiye nyimbo broh

  • @mikebernabechimundi3472
    @mikebernabechimundi3472 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +5

    Manyaka, phala la nyimbo,

  • @DavidManyela
    @DavidManyela 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +4

    Lozani zanu is the best song osati manyaka iyi

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Dan Lu, Nkasa Ndi anthu oti sanapite ku school amadyela mukuimba chonchi, Akufuna azithandiza mabanja awo kangachepe angapeze ndeosawaloza zala koma pachilungamo chakwela waononga dzikoli,
    Chakwela amabisalila kuti ndi m busa koma amamupanga chilima zija ndinkhaza komanso Ufiti.

  • @GeraldMkwewu-gd5eb
    @GeraldMkwewu-gd5eb 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Dan Lu skeffa ndi agalu muziona 2025 sipatali gyz ndi chakwera chikangawa wanuyo paeazy

  • @RemitterFlik1130
    @RemitterFlik1130 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ntayeni uyo bola anatisila nyimbo za boh ku dpp galu akagwele ameneyo nde amvatu nyunyunyu mene kwa khomela pa katoto akunamatu ameneyo dpp my vote

  • @HestingsZiba-d6k
    @HestingsZiba-d6k 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Apm my vote😊

  • @LindaBanda-cg1hv
    @LindaBanda-cg1hv 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +3

    After Jetu atawapambana aganiza zolowa ku ndale 😢😢

    • @AiwaMedia-sh6vx
      @AiwaMedia-sh6vx 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Kkkkkkkk apa wanya nayo, zake zada basi

  • @stevendemanje
    @stevendemanje 42 นาทีที่ผ่านมา

    Dan apa ndiye ayi.... Nyimbo zomwe mudaimba posapota DPP ndikawawa ndipo dziwani kut ndizomwe agwilitse ntchito pa kampeni osat iyi ayi...

  • @GospelSoldiers-sr7np
    @GospelSoldiers-sr7np 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Mukuziyalusiranji akulu, Malawi wa lero Simachakatu ay anthu anasukusula palibe angawanamize😂😂😂😂

  • @robenmatchilinga604
    @robenmatchilinga604 37 นาทีที่ผ่านมา

    Dan lu sanalakwisee iyeyu akangochemerera chipani chimaluza 😂😂 osadanda adadi boma 2025moto kut buu 🔥🔥🔥 DPP my vote

  • @Witchdoctor334
    @Witchdoctor334 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Ine nd mmozi ndmamukonda kapeyu zomwe wachita apa patumbo pake

  • @TaweniChavulaKamwendo
    @TaweniChavulaKamwendo 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Mxiiii nde bola lozan zanu iyi ndiyo cha 🏃🏃🏃🏃🏃🏃

  • @GeraldKaputa
    @GeraldKaputa 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Kudyetsa anthu chitedze feteleza Mk100.000 chikangawa mbola ya nyimbo!

    • @AiwaMedia-sh6vx
      @AiwaMedia-sh6vx 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      MANYI amunthu

  • @FrancisChitsulo-f2d
    @FrancisChitsulo-f2d 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ndipo Dan lu sikuti siiwe oimba ayi mwina sukudziwa

  • @CosterMustafa-m6h
    @CosterMustafa-m6h 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Mmm zaziii muzangofela zayeni inu 😢😢changa chisoni chabe pot ndi artist wathu

  • @joyahmedjoma4615
    @joyahmedjoma4615 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Lozani zanu ife tione imeneinja number one 🎉🎉🎉kma iyi zilo pa 10 😂😂😂😂😂ubwedza ndalama iwe chikangawa akabwerako ku America 🇺🇸 silibwino ata 😂😂😂😂

  • @MwezoMuhajiryakidu
    @MwezoMuhajiryakidu ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndiwe galu palibe chimene chikuveka apa APM my vote

  • @stevovosalimu5443
    @stevovosalimu5443 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ukayambileso aise apa nde palibe wagodya ndalama 😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @JafaliAjusa-zg2xi
    @JafaliAjusa-zg2xi 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    I stopped listening to his music a long time ago when I heard about him About chakwela

  • @mcsellahntv6896
    @mcsellahntv6896 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chikangawa party Chikapita chaka chamawa chino, uzangoyang'ana nsana wa njira ya ku South Africa uzikagwira maganyu, Chifukwa ndiye ife tizakuphiphita ndikukuphwasulila ting'oma takoto.

  • @AuphieBannet
    @AuphieBannet 31 นาทีที่ผ่านมา

    Ayimbileni basi koma simukuwinanso taaa,
    Ayimba oooooonse kaloweni kwa chikangawako,koma 2025 muli kunja

  • @KennieMwacho-r9z
    @KennieMwacho-r9z ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Braza mwapala lozani ija munapha💙💙💙💙💙💙 ....ayi adyeleni ndalamazo pot APM ananena kut kukana ndalama nkovuta ...tiyeni tilandire vote yanu ili komwe mwachoka uja😂😂

  • @johnaman5791
    @johnaman5791 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    APM my vote

  • @jameschibisa1433
    @jameschibisa1433 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndichifukwa chake pa ndalama paja Pali anthu akufa awa after awafinya pakhosi ati atembenuka munali ndani a Dan lu apa ndiye mwangoononga mbiri iwe n'galu

  • @ShadreckHassibu
    @ShadreckHassibu 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ineyo si sapota wa aliyense koma akulu awa alira sadati ndithu a Dan Lu mwachidule angovomereza kuti nsuzi watha awa

    • @Twayaibrahim
      @Twayaibrahim ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Sure ndipo awawa ndachitsilu samayeneraso kumayakhula zamwano anakangokhala chete osat kumalubwalubwa zaziii

  • @TrinityMaloko
    @TrinityMaloko ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Dan luu ungofuna akupase ndalama bas ukatero utuluke bisines imeneyo aaa koma ikudula

  • @JohnNdala-tv7gm
    @JohnNdala-tv7gm 36 นาทีที่ผ่านมา

    Iye amati marilo akatuluka nyumba sabewelela nyumba iye kumeneko wapitako ndiye maliliwo chifukwa anamwalila kalekale mu 1994 abella bwanji tingot wonse amene akulamulapanowo ndianthu akupha skufuna azingopha anthu osalakwa

  • @RajiChapollah
    @RajiChapollah 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Dan lu mwana wanga Dan lu mwana wanga Chan ichi olomanyaz pakamwapo kd mwachita kupangila record PA 4ni kapena Sana ibalace

  • @isaaczuze
    @isaaczuze ชั่วโมงที่ผ่านมา

    My vote is for Apm osati chisilu tili nacho lelo chopanda maplan
    .....chisilu cha munthu .....ineyo ndiye chakwera toto ngakhale anthu atatha mu ziko

  • @AnizMotti
    @AnizMotti 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Munthuyi ndi zobadi bwanji kkkkk maluzi amuswa heavy😂😂

  • @TracyBanda-i2g
    @TracyBanda-i2g 18 นาทีที่ผ่านมา

    Adan Luu mwakwera yokuphwa matayala iiiiiiu palibet chikomapo kuposa tsonyani ZANU IJA ife tione .

  • @JobeAntonio
    @JobeAntonio 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    DPP MY VOTE ❤❤
    DAN LU WADYERA PASANA PAKO NDITHU NDI CHIKANGAWA PARTY YAKOYO ZOPUSA

  • @EmmanuelMponda-ig9bm
    @EmmanuelMponda-ig9bm 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    UTM MY VOTE ❤

  • @PanganiW.Bilali
    @PanganiW.Bilali 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Tomorrow is a hope not a promise....
    Oppressed will decide

  • @DanMhone-iw6xg
    @DanMhone-iw6xg ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Choka apa iwe mwana wovesa chisoni iwe anthu akwanu akuvutika kwa baluku uko iye ulipano kutambasula kuchikamwa kwako konunkhako mwana ovesa chisoni mulungu akuyendele mwapadela dela ukufunika yesu iwe moti asukuwona mavuto ali muno

  • @EmmaEmma-q4u
    @EmmaEmma-q4u 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Kunena molondoloza ndekuti Peter salinawo kumidimaku ngakhale Bible linanena kye kuti dima umadana nkuunika so sizingatheke Ana adima kukapanga spoti Ana akuunika so zinayenela kuti Ana adima akhale pamodzi Ana opembeza mlungu pamodzi aliyense apemphele kwa mlungu wake ndye mulunguyo ayankhe pemphelo kwa Ana ake tione kuti kd Bala ndi mlungu so izizi grace chinga ananena kye kuti akumenya nkhondo yapansi pansi enawo azizatuluka kumapeto so pomwe nkhondo ikukula iwe ndne tiye tipemphele kuti mlungu amenyele ife nkhondo kuziwike kuti yehova amamenya nkhondo

    • @Halima-i4x
      @Halima-i4x 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Yes chilungamo

  • @PateinceGoman
    @PateinceGoman 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Wayimba za ziii, komabe tikuziwa kuti wangoyimbila business koma vote Yako ili ku DPP same to me
    Imba zosapsazo poti ukufuna ndalam

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 16 นาทีที่ผ่านมา

    Dpp ija osazaiphwekesa ❤❤

  • @ABIGAILMpezeni
    @ABIGAILMpezeni 29 นาทีที่ผ่านมา

    Lozani zanu ija ndye nyimb awa ndopusa mkona nyimb zawo sizikondedwa iyaaa musowa nanu kuchikangawa kwayitana mukatero

  • @thesocietynews3181
    @thesocietynews3181 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    APM our votes in Malawi now

  • @HawahMtenje
    @HawahMtenje ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mwana wanga ngat akukuseka at zosabhebha😂😂😂😂😂

  • @Dauson-j5i
    @Dauson-j5i 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mumakutu ndikukhala kwake mumalowa sosoyanasiyana zabwino zokha ndizimene zimasalamo ndalama paja ikalankhu chilungamo chimakhala chete

  • @FrancisChitsulo-f2d
    @FrancisChitsulo-f2d 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Dan luu iweyo ngat ukufuna dollar nde wanyika

  • @AdamsPhiri-h1y
    @AdamsPhiri-h1y ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Komad zowona makosana cha kwela wasintha zambir maka Maka kwa ife timadalira kulima zinthu zikuyenda.

  • @KenfordKapira
    @KenfordKapira 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Kod amapanga record amapanga ndani ngat ti ma studio ta mma kwalala

  • @VeronicaChimkonde
    @VeronicaChimkonde 26 นาทีที่ผ่านมา

    Tulani pasi ijatu eee munaphatu bgy

  • @MosesTangwe
    @MosesTangwe 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    DPP 🔵💙 yomweyo next year m'boma

  • @mcsellahntv6896
    @mcsellahntv6896 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Iwe dziko lakutula pansi, watha basi aise. Ife timadana ndi anthu adyera.

  • @VincentManyenje
    @VincentManyenje ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chakwera woyeeeeeeeee 2025 boma.

  • @DoreenSkova
    @DoreenSkova 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Iyi ndiye phwala LA nyimbo

  • @LensonPausani
    @LensonPausani ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Waipa zedii panyimbo imeney😂😂

  • @TamikaKaponya
    @TamikaKaponya 18 นาทีที่ผ่านมา

    Tikuona komwe ukathere ndi dyera lakolo

  • @SaraShohomaliMadi
    @SaraShohomaliMadi ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mbola my vote Apm ❤❤❤

  • @VincentManyenje
    @VincentManyenje ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Manyazi bwanji ma cadet a DPP.

  • @UmaliIshmael
    @UmaliIshmael 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mwanyika mabwana

  • @GustinoKamanga
    @GustinoKamanga 2 นาทีที่ผ่านมา

    Km dan luh kumpusitsa chikangawa kkk kumudyera ndalama kutulutsa manyakawa😂😂😂 kkk umatha APM WOYEEEE

  • @BoyziMeko
    @BoyziMeko 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mumati ndinu wachiayao president wanu wavomela kut azanu achiyawo azipedwa uku aaaaa

  • @user-lw4hw9ce4w
    @user-lw4hw9ce4w 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kape den lu mavuto onsewa matatuu phwi onsewo ndiwedi wasatanik wasatira anzako

  • @MagretSaizi
    @MagretSaizi 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Za ziii Dan luu hiyaaa

  • @ChifundoNkhoma-k5t
    @ChifundoNkhoma-k5t 5 นาทีที่ผ่านมา

    Km kumalawi ndalama patsogolodi nanga ndikulotadi mwamva aaaa

  • @SostenMbawo-sj8ec
    @SostenMbawo-sj8ec 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Unakati nyimboyi uzingovela wekha ase wava

  • @AiwaMedia-sh6vx
    @AiwaMedia-sh6vx 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kujoyina MCP zimangofanana ndikujoyina UFITI

  • @DanielDoctor-t3p
    @DanielDoctor-t3p 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    DAN LU NDIYE CHANI MANYAZI ULIBE

  • @sibaleweddingsibale6232
    @sibaleweddingsibale6232 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Dpp my vote

  • @BlessingsMarley-l2x
    @BlessingsMarley-l2x ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Manyaka anyimbo ndipo iwe ndiwe kape zedii ngati kuli kufuna ndalama mmmmm!!!!! Wapala zedii koma choti uziwe adad ndi moto ndipo ife tikhala tikusewela nyimbo monga izi. Lozani zanu ife tiwoneee komaso winaso ayiiii!!!!! Eyetu osati manyaka anyimbo iyiyi ndipo kumeneko udikilile iwe ndi skefa chimoto kupeleka nsembe

  • @RajiChapollah
    @RajiChapollah 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Km many amenewa ndiy ayi
    Bolas kumavela mishion

  • @Zamwano
    @Zamwano 7 นาทีที่ผ่านมา

    Kumaimba ukuziwa kuti u need money koma not zoti Chakwera wawinaso

  • @JoshuaSiamoonga
    @JoshuaSiamoonga 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ziwoneka pothela galu wamuthu ameneyo

  • @ZionekaMember
    @ZionekaMember 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Dpp my vote 😂😂😂😂😂😂😂 wapala galu💙💙💙💙🩵🩵🩵🩵🩵🩵🩵🩵🩵🩵🩵🩵💙💙💙💙💙

  • @BlessingsTembenu
    @BlessingsTembenu 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Za ziii,koma ndalama ndisatanadi ndithu.mboli yanu man apa mwatha basi

  • @KeffasiJonathan
    @KeffasiJonathan 51 นาทีที่ผ่านมา

    Kod nde kuti ma commet osewa sindipeza yomuyamikila eeet

  • @EdnaBenjamin-bl7bw
    @EdnaBenjamin-bl7bw 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chopanda nthandauzo mkomwe zaziiiiii lozani zani woyeeeeeeee iyiyi mwapala bambo

  • @mphatsosadiki4983
    @mphatsosadiki4983 44 นาทีที่ผ่านมา

    Odi ndikamvele nyimbo za Jetu

  • @EdwinKachepa
    @EdwinKachepa 56 นาทีที่ผ่านมา

    Manyaka enieni.

  • @Halima-i4x
    @Halima-i4x 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    😂😂😂😂😂😂😂zachison ndi 2 🙌🙌

  • @ThokoNandolo
    @ThokoNandolo 59 นาทีที่ผ่านมา

    wamisala dun luu

  • @JamesSaiti-h1l
    @JamesSaiti-h1l ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nyimbo unayimba kale

  • @mohamedriazshreef8697
    @mohamedriazshreef8697 45 นาทีที่ผ่านมา

    Chikangawa party 😮

  • @MustafaEdward-bp2ip
    @MustafaEdward-bp2ip 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    DPP my vote adad

  • @Iponga
    @Iponga 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    AAA zapamtumbo zeni zeni palibe chikunveka

  • @chakather7132
    @chakather7132 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Eeeh kumalawi😂😂😂🎉

  • @MusaMajudu
    @MusaMajudu 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Anantha uyu anayesa kulimbana ndi onesimasi mbuzi yamuthu😂

  • @hardworkkayuza6353
    @hardworkkayuza6353 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zaziii mbola ya nyimbo

  • @MosesSolomoni
    @MosesSolomoni ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Gays enawa ndi amalonda nyimbo zawo

  • @BrianMuleke
    @BrianMuleke 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Aona kutulusa chibale kumaposedw ndi jetu ali bola ndiimbe za ndale kkkkkkkkk

  • @PatrickLigomeka-c8b
    @PatrickLigomeka-c8b ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Koma kwanyimbo iyi ngati amupasa ndarama abesa kkkkk

  • @HezelChisi
    @HezelChisi ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Inetu maonangati Iposa lozani zanu ija osadziwa ndi manyaka anyimbo kkkkkkk apapa pamene ndadziwa kut sendera sister's ija imatha kuimba

  • @Benjaminmachinjili
    @Benjaminmachinjili ชั่วโมงที่ผ่านมา

    A dan lu mwayamba kupita kuma studio ama 2500? Zamanyaz kwmbil😂😂😂😂😂

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    😂😂😂😂😂😂km lozani zanu ija adakwapula iyi wayaluka nayo ndimayesa mzakupsyatu APM 💙💙💙💙💙

  • @JoeAbasi
    @JoeAbasi ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Simene kulili kumalawi maluzi anyanya

  • @georgengwira3152
    @georgengwira3152 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zaziiii mphala leni leni

  • @EvanceEdson-fz1vn
    @EvanceEdson-fz1vn 11 นาทีที่ผ่านมา

    Wapala zedi. Ndimaona ngat muzinena zitukuko zomwe wapanga ngat nyimbo yalozan zanu ija. Apapa ndimanyaka

  • @EvanceRazaki
    @EvanceRazaki 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Uzivele chison imeneyo ndinyimbo

  • @EvanceRazaki
    @EvanceRazaki 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kachiken Dan lu kumbuka mene nyimbo zako unayimbila za DPP ndizimenez zikufanana kkkkkkkk chimene ungaziwe ndichi kukanakhal kut boma limenel ambuye akulifuna bwedzi ambuye atayikapo zanja panyimbo imen wayimba k mcp km chifukwa ambuye sakondwela nazo uthenga wako wanyimbo ukufalisa ndchifukwa aliyes kukomet akungot za ziii😂😂😂😂