Funso ndi loti,,, kodi ndege imayamba ulendo osapangidwa service before the journey?? Musamatipusitse choonadi mukuchidziwa. Mulungu akukanthani mochuluka chifukwa cha chimene munachita anthu inu ku Chikangawa
We are just wasting time..the report is enough as the reported several irregularities the next step was to go for authorities why these were missing from......why conflicting report on destination ..... Work up let the authorities tell us why?
To be honest it’s just the way how you people you can explain abut it just the plan was old really??????????the time you dissaid to give them you didn’t think abut important things ???kuti zilimo zokwana?? Kodi ndege yomwe mukuti inagilisidwa yokwera ma pule. momwe mukagulisa simunaone kuti muzikwera chani??? Ngati inayo inalibe dzida zokwanira?? Akunkiyu dziyankhani ngati kunja kuno kuli mlungu amamenya nkhondo zaosalakwa ali chete mukuchita kuona nokha kuti mukutembenuza chilungamo nkupita ku bodza 😒 why ??? Andale akulowerera chifukwa ubale wa apule ndi a VP sunali bwino olo atalhala apolisi amagalizila kaye oyamba kuti ndi mdani wako akafuna kufufuza chilunhamo cha report aliyense akuchiona ngati zopezera umboni mulibe chona chichokera kuti???
Akunkuyu nthawi ikubwera muzayankha pa zimenezi Malawi azakucheperani apa ndinu dolo mumakumbukira nthawi ya mayi Joyce Banda wina anaziombera yenkha ataulusa kuti Amayi Aluza zisankho iweyo uzangosunga petro ukazangomva kuti kwaluza uzangoziyasa wenkha before it is too late
Kodi amalawi munakhala bwanji that report is cooked bcz ndege yomweyo yina nyamura maliro communication was there then mawa wake yanyamura chilima no communication
My question to bwana Chunga is, to what degree or percentage of the protection of the vice can we say was provided in that day considering that the vice president is supposed and always to be given maximum security It seems on this particular day the vice president was exposed to danger based on the condition of the plane whose probability for danger was so high
Iwe Kunkuyu zonse ukunenazo nchimbudzi, MANYI, tuzwi. You are talking thinking you are smarter than all citizens. Ine nkanapempha kuti atiwonetse ulendo umene udatenga maliro a Raph Kasambara, ndegeyo inkawoneka pa Radar? Both ways, ngati sinkawonekanso that's a total negligence of the Gov on the releasal of the equipment to to be used. Ngati idalipo pa Radar, then it's a proof that this time this plane was intentionally tampered so that be equipped to kill. Musaziyese ochenjera
I think the best thing is to tell CHIKANGAWA to step down as a president
Yeah
True
Indeed this Chikangawa guy should be removed for killing Chilima
Pamodzi ndineneri wake, yemweyo.
Kodi Mesa chakwera anati chilima ayezeka zobbisaliranazo ai mkukuyu chakwera namajeket anapha chilima
Kuyankha kwake nkosagwira mtima
Ooooh my God!
Very powerful bwan kumkuyu
IFETU NGATI A MALAWI SITIVOMEREZA CHIFUKWA NDEGE ISANANYAMUKE IMAYENERA KUPANGIDWA SERVICE, NKHANI NDI YOTI ZINATHEKA BWANJI KULAMULA NDEGE KUTI INYAMUKE CHONSECHO I ALIBE ZIPANGIZO ? KODI BATTERY LINATHA CHIFUKWA CHOTI AMAKWERAYO ANALI CHILIMA? PAMENE CHAKWERA AMAKWERA SINATHE BATTERY BWANJI? OSATIPUSITSA IFE AMALAWI CHOONA NCHAKUTI CHIKANGAWA ANAPHA SKC CHIFUKWA CHOFUNA KUIMIRANSO PAMPANDO.ZIDA MUNDEGE ANACHOTSAMO ATAIGWETSA NDEGE SINGANYAMUKE POPANDA ZIDA ZOZIYENEREZA ZOSATHEKAYI NDIPO CHAKWERA AKANAKHALA WINA AKANATULAPANSI UDINDO PAMODZI NDI AFITI ANZAKEWO ASATANIC INU AGALU TIRI NANU,
Zoona sukunena bodza
Inu zinthu zinachita kuchoteedwamo osamapusitsika ndimabidzawo
Amalawi tisavutike ndizambili pa. Ifa ya VP ndi anthu 8.chilungamo chizaziwika chakwela ndi dzigawenga zakezi. Zikatuluka boma. Ngati tikufuna chulungamo tikangovota nkuchotsa zigawengazi
Kunkuyu is a big cruck Chilima killed like a baby shame why chimwendo not flying together in the plane
Moses kumkuyu simalawi ayi mumufufuze bwino bwino
Funso ndi loti,,, kodi ndege imayamba ulendo osapangidwa service before the journey?? Musamatipusitse choonadi mukuchidziwa. Mulungu akukanthani mochuluka chifukwa cha chimene munachita anthu inu ku Chikangawa
We are just wasting time..the report is enough as the reported several irregularities the next step was to go for authorities why these were missing from......why conflicting report on destination .....
Work up let the authorities tell us why?
Ndiye mmene a kunkuyuwo akunenera kuti ndegeyo idali yokwanira kuuluka ndiye akunenazo kuti munalibe achina black box why?
Inu nanga dzovala inawavura ndi ndegeyo,inutu mtendere mulibe, muone olo thanzi lanu likusowa mtendere
Nkukuyu ameneyu mayankhulidwe ake mmmmmmh!!! Akundikaikitsa kwambiri. Chilpo akudziwapo nthawi yakwana yoti chonse tichidziwe nkhani ya ndege yija. Ambuye muwakanthe anthuwa ndithuuuu!!!
If munalibe ma communication devices, pilot amatela ndikuuluka bwanji, mma airportmu?
Bayana you are saying black box is important and other devices so the question is why those important devices were not there and from when ?
Noma lopandachitetezo nfakhaletiwelenge sitidziwacholichose mabodzawakulu anthuakupha oyipantima lipotilomeneli apitisekwaazibalewawo vuto la transponder and brack box azibwelesetiwone umboniogwiloka
Ndiwonama akunkuyu akubisaumboni idea malawi tulila brack box olikuti ?
Anthuwa zoona ndi zoti sanapangane zonena onse atatu amanena zomwe akuganiza komabe pangatalike chilungamo chidziwika
To be honest it’s just the way how you people you can explain abut it just the plan was old really??????????the time you dissaid to give them you didn’t think abut important things ???kuti zilimo zokwana?? Kodi ndege yomwe mukuti inagilisidwa yokwera ma pule. momwe mukagulisa simunaone kuti muzikwera chani??? Ngati inayo inalibe dzida zokwanira?? Akunkiyu dziyankhani ngati kunja kuno kuli mlungu amamenya nkhondo zaosalakwa ali chete mukuchita kuona nokha kuti mukutembenuza chilungamo nkupita ku bodza 😒 why ??? Andale akulowerera chifukwa ubale wa apule ndi a VP sunali bwino olo atalhala apolisi amagalizila kaye oyamba kuti ndi mdani wako akafuna kufufuza chilunhamo cha report aliyense akuchiona ngati zopezera umboni mulibe chona chichokera kuti???
Ndipo zoona izi
Why was Achipofia cut off.
kunkuyu iwe ma pwala a gogo ako galu iwe chigawenga
Koma ndipo. Wittika too atiuze
Ndikukumbukira poyamba ananena kuti black box yasungidwa pa malo abwino, komanso otetezeka. Palinso chifukwa chofunira mapepala kuti anene kuti pogula ndegeyi munali black box kapena ayi?
Akunkuyu nthawi ikubwera muzayankha pa zimenezi Malawi azakucheperani apa ndinu dolo mumakumbukira nthawi ya mayi Joyce Banda wina anaziombera yenkha ataulusa kuti Amayi Aluza zisankho iweyo uzangosunga petro ukazangomva kuti kwaluza uzangoziyasa wenkha before it is too late
Kodi amalawi munakhala bwanji that report is cooked bcz ndege yomweyo yina nyamura maliro communication was there then mawa wake yanyamura chilima no communication
Zachibwana zautsiru
My question to bwana Chunga is, to what degree or percentage of the protection of the vice can we say was provided in that day considering that the vice president is supposed and always to be given maximum security It seems on this particular day the vice president was exposed to danger based on the condition of the plane whose probability for danger was so high
ASAMANAMEYAWA ZOTI EXPAY PONAMILA INEYOSINDILANDILANAWO ANTHUOKWIYIRSAWANTHU
Bvuto ndiloti a boma mulubwalubwa pa nkhani imodzi .Chakwera kunena zina ,Kumkuyu kunena Zina. Tikhulupirire ziti ?
Chilima anaphedwa ndichakwera nkunkuyu chimwendo zikhale
Wasala ndi chikangawa he must step down chakwela
It’s not the true because if it was Ancient then how took out his shoes and clothes please can you explain to me god bless all.
Tiona tokha zochita osati pangila 2025
Chikangwa kkkkkk
😵😵😵😵😵😵
A tchunga musapusisidwe ndi report la fake lo ayi
Chillima aphedwa ndi chakwela
aaaaa brack box linasungidwa ndi boma ku state house ndi ma4n anthu anaphedwawo
Kunkuyu ponyela pako, ufiti wakowo uziona malawi siwako ndi KACHAKWELA kakoko inuyo mulibe umunthu chilima kukuwinisani lelo ndikumupha AAA mumaganiza bwanji
PK kodi uzalowa liti ndale
Mwa iwe muli usogoleli not moses kunkuyu
Mkukuyu iwe nd munthu opusa kwambiri ndipo ndiwe galu wamunthu coz ukuona ngat malawi aliyese ndi ogona eti koma dziwa kut sitingavere zopepela izi
A president a JB anati Moses kunkuyu machende ake
Boma la mcp ndilakupha asadzimbakire
Iwe Kunkuyu zonse ukunenazo nchimbudzi, MANYI, tuzwi. You are talking thinking you are smarter than all citizens.
Ine nkanapempha kuti atiwonetse ulendo umene udatenga maliro a Raph Kasambara, ndegeyo inkawoneka pa Radar? Both ways, ngati sinkawonekanso that's a total negligence of the Gov on the releasal of the equipment to to be used. Ngati idalipo pa Radar, then it's a proof that this time this plane was intentionally tampered so that be equipped to kill. Musaziyese ochenjera
Awa akuyankha zaboza
Tivomeleze bwanji?kodi bwanji inu simunavomeleze 2020 ija nkhani ya zisankho,,,zinavuta bwanji kuvomeleza unali moyo umeneuja,,,panoso sizitheka kuvomeleza chifukwa ndi miyo ya anthu
Eti amwene, tivomeleze zimenezi?
M'fiti ameneyu ndichakwela machende ake
Unapha witika iwe galu kamutu kukhwimako
Mxiiiiii
Pena kukuyu amalondola
Kkkkkkkk zilipo zambili amangoziliza kupanda 😅😅😅 osawuluka
Akulu awa kupupuluma too much
Wabodza uyu
Uyuso ni mbuziso kagwere uko
Anali ndicholinga kuti aphe achilima awa anthu onsewa ndiwokupha
Iwe okupha galu iwe
Maonekedwde a matupi a anthu ofa pangozi imeneyi ndi zimene zikukaikitsa mmalawi aliyense . Kubvulidwa dzovala , mabala oonekeratu kuti sanali chifukwa chakugwa kwa ndege .