Thanks for Gwedegwede... but when you are doing interviews come fresh not what the guy is answering and reading on the paper which shows us that you firstly discussed.....it's not good,, thanks 😅
Manganya si wa UTM, if he was president of UTM he could go to prison and visit Patricia, Why he want people to listen 👂 to him while he does not care 🤷🤦
Nkhan zotsez zikukura chifukwa chakusapezeka Kwa Brack box chifukwa mayankho otse arcmu Brack box mo ndye comition iy choyamba isake komwe kur Brack box bas
Powerful speech guys ,tatiyeni tilimbikile tchito ,za ndalezi no no muyambanapo❤
Thanks for Gwedegwede... but when you are doing interviews come fresh not what the guy is answering and reading on the paper which shows us that you firstly discussed.....it's not good,, thanks 😅
Bravo guys! straight talk boma iliri ndinyasi eish,
Steve kondwa Banda uku ndiye kuyankhula apa ndiye ukupangadi za a Malawi congratulations brother 🤝
Mau omanga dziko keep it up bwana steve konda Banda & your team
Very good love is needed
Pano ndiye muli bho guyz,big up.
Guys very good 100%❤❤❤
Manganya si wa UTM, if he was president of UTM he could go to prison and visit Patricia,
Why he want people to listen 👂 to him while he does not care 🤷🤦
Zapita bwanji kukawona muthu wa kupha president chilima
Gwede....! Gwede.....!🔥
More fire guys ❤❤
Usi Achoke kumene ...we dont want Him in our party Period...
If you dont want him then use democratic means of getting rid of him . Malawi is a democratic country
Commission of inquiry yimafunika yikhale live kumene.ngakhake kuno Ku south Africa commission of inquiry timayiwonera pa TV live.
Aaaaaah inu boma la chakwela landikwana kungovuta chilichonse anthunu aaaa ayi apa zafikapono nsaname
Wini nyondo akufunika mesa amati malemu bodyguard wa malemu chilima anamulembera massage
Ndipo timasatira iyaaaaa inu mumatiimira ndithu ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
❤❤❤❤❤❤ takunyadirani
Ndakaika ngati after convention ngati chipani sagawana
😂commission of enquiry idzafunse Patricia Kaliati
Mcp my vote
❤❤❤GWEDEGWEDE
There's no any readership in this government wanzeru akuona koma mbuli ndi zimene zikusapotabe ulamuliro opanda masomphenya ngati umenewu
Nkhan zotsez zikukura chifukwa chakusapezeka Kwa Brack box chifukwa mayankho otse arcmu Brack box mo ndye comition iy choyamba isake komwe kur Brack box bas
Popita kofufuzako tenganiko a Sembe a Catholic ajaa zinazi ndi anthu okonda ndalama
Nthawi yoyenera kuti azienda mpamene akubisala ...koma kumaenda mmmisikamu ngati palibe vuto..tulukani ku state house koooo afisi inuo
KOM NDIYE MWAYAKUL LELO NO PAIN NO GAIN
Nkhani ndi black box basi, umboni onse uli mmenemo 😢
Micle usi siwa utm ameneuja ndi wa mcp ...ameneuja ationongera zinthu
Sakuyenda a VP coz mafutadi akusowa.😂😂
This government is nonsense government guys 👦 🙄 and we don't need 💯 this government again 💯 mcp chikangawa walephera kuyendedza dziko la Malawi 😳 🙄 🤣
usi kuti amusekele ali ndi move ndi chipanichi ndiye kusawasatila zofuna zawo sikulakwa ali ndi upandu ndi chipanichi
Kumeneko kukabwele black box apoo biiiii uwona zakuda Chakwera
Eya zoona ❤❤❤❤❤❤
Kodi sitima ija bwanji siku bweletsa mafuta kodi, samati njanji yatha mafuta ngambwi ngambwi
Apresint oyiipa kwambiri abodza mafutawo alikuti
😂😂😂😂Jessie kabwira's voice
Fuso lazeru
Usi ndiwamasanje apite azikapitiliza tchito zake tikufelanji yamusowa uko
Ayi ausi achoke kumeneko
Utm yayife nd iyi ili ns kaliyatiyi bc ya usi ife ai
Awa anabwera pano kunena kuti stima anakazilandira chakwera ku nsanje kuja munkati ndi mafuta ,,,lero mwavomeleza????
Ndipo anatiuzadi ineso ndikudabwa kuti lero akuti mafuta mdziko muno mulibe why? Boma lomangokamba bodza ili iyaaaaaaaa
Manganya sakufuna kumayendera mafiringi steshon akudziwa kuti akamudurako zara akangopita kumeneku
Akamati chakwera kumenya kugwetsa pano tikumenyedwa kwambiri amalawi
Kodi program imeneyi imachitika lero?
Lachiwili amabwereza lachinayi
Manganya ndi manyii eni eni
Chakwela ndi mbuzi wakuba
Kodi nanga a Usi akufuna convention ikhale chaka mamawa. Zimenezo mulankhulepo.
Mcp yatha kaleeee
President oyipa kwambiri mafuta kulibe, dziko muli njala iiiii abale inu Apule mwaonjeza inuuu chonde
Ndiko kuyankhula UKu 100%
MCP ikulephele chilichonse a Manganya aja ali kuti amapanga matama muja apite akayendele ku NOCMA kuti chikuvuta nchiyani kunkuyu ananamiza a Malawi mukumusungabe chifukwa chiyani mbava zokha zoka Inu ku MCP
nsongoleli kulumikidza maiko 4 Kwa 3weeks. ndarama zamafuta ndikumakwerera kaparasa zoona
Guys 2025 ndikuyiwona kuchedwa kodi tingaithamangise bwanji🙆😢
tazipasanani mpata polankhula plz
kumalawi......
Kkkkkkk
Uku nde kuyankhula guys keep the fire burning
Ku gwede gwede mwakambako zanzelu lelo
Boma ndilomweri koma chipani tikuchosa afikapotu awa ationjeza yooh
Ndalama zogulila mafuta anakanjoyela Ku America ndiku China
Maganya is a dangerous person amene akusunga mpeni kumphasa
Amawapatsa ma 2pin kt atimenye
Mafuta apezeka akayamba kalembela wachisankho chigawo chapakati izi boma likupanga dala kusowetsa mafuta cholinga chigawo chakumwela anthu asakwanise kulembetsa muona week yamawayi masi akalembela akatha kumwela apezeka mafuta
Tikanakhalapo anthu 5 million ngati ine ndikanati tiyeni tikaseke nyumba ya Boma .. Tatopa
ndale zapamalawi ndizopusa tiyeni tisamale mabanja anthuwa atizezekezetsa amanewawa
Mavuto alipo ndithu ku malawi kuno
ndani angafune kupha chakwera ?munthu wopanda phinduyo ?
Muli ndi mbali n mbali yanu ndi DPP sikuti sitikudziwa.ai.mmm
Mukudan ndi chilungamo bwaj
Mukudan ndi chilungamo bwaj
Uyo wa mcp tamuwonani kudana ndi chilungamotu 😂😂😂😂😂
Ntendele watha kumalawi bwanji akutchinga museum
Zoona
Inu mungokwatirana basi
The whole “President” of UTM could not visit his SG mmmm
?
Utm singazathe ichichi amene akuchoka azichoka....
Kodi nkhani yamagutayi,, mpezeni kumkuyu muthileni mafuso galu ameneyu