Iwetu umachwedwa jokes nd tisakutengere, Solomon naye akachedwa solomo kani anakhala ndi izozo, wina ndi mr James ayesere za solom zimunyambita. Kani ambiri amafuna ayesere za Ambuye Yesu, zimawanyambitsa. Live as per based name Given b Heaven. Don't be deceived, he live in his name jokes.
... nanga atapenga kkkkkkkkkkk
ويفك يا جكس chikukutsocheresa ndichani jocks . Ndithudi wallawalumpha wire ofiyila . A siyeni atumiki amulungu chonde please .usapange chotseweresera . Ndikanakutukwana ayise komano ndamuwopa Allah . Tsoka likhale paiwe jocks.
Kkkkk komo satana akamalankhula amachita ngati ngati akulankhula zabwino😂😂😂😂
Kkkkkkkkk
Iwetu umachwedwa jokes nd tisakutengere, Solomon naye akachedwa solomo kani anakhala ndi izozo, wina ndi mr James ayesere za solom zimunyambita. Kani ambiri amafuna ayesere za Ambuye Yesu, zimawanyambitsa. Live as per based name Given b Heaven. Don't be deceived, he live in his name jokes.
kkkkkk km iwe
Sono iweyo ukwatire 300 .....45 mwaiowo umenyano nawo aliyese akuchoseso Dzino limozi .....usala.ndi mano ??? Poti apo ena anakududulapo kale
😂🤣🤣😂😂😂koma makani kwambili
Kkkkk koma kulu iwe umathakoma
Kodi osangoyamba u pastor bwanji...nthabwala zija zikukukanikani🤣🤣
Komatu Jokes 😂😂😂😂
😂😂😂😂😂
Kkkkkk koma nde ukwatire akazi amapasa, akamapita mmodzi winayo angatsare😃?
Ewe Ulindiangati
Iwe uli ndangati? Mesa ma twins aja achina mada anakukanika
Iweyo uli nd awiri?😂
Ndikuyesetsa
kususana ndimalemba2 uku
Bible will still stand
Iwe ndi galu eti
Kkkkkkkkk
Iwe olo mmodzi ulibe
Ndipo inu
@@mrjokes001 Kodi akaz awiri aja unawakwaira
Nanga timadabwa nd zmene amalakhulaz coz munthu sungakhale nd akaz 1000
Iwetu anakukanika mitala ija
Eish