THE HOT CURRENT SHOW

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 8 ก.พ. 2025
  • #Hot_current

ความคิดเห็น • 12

  • @SylvesterLikumba
    @SylvesterLikumba 6 วันที่ผ่านมา +2

    Aaa km atimes ulemu wanu😅😅😅

  • @IsaacMusa-py2jm
    @IsaacMusa-py2jm 6 วันที่ผ่านมา

    Loud and clear here mpumalanga

  • @AtupereSadiki
    @AtupereSadiki 6 วันที่ผ่านมา

    N I quote a bwanji moze mwanyika kkkkkkk ndaseka

  • @KendrickLuckyc
    @KendrickLuckyc 6 วันที่ผ่านมา

    Amozee anyika😂😂

  • @JanetNyamayalo-f4r
    @JanetNyamayalo-f4r 5 วันที่ผ่านมา

    Akufuna adzitipusitsa nduna zopusa kwambiri, koma nde mwaparatu

  • @PeterKainga-e3h
    @PeterKainga-e3h 6 วันที่ผ่านมา

    Koma zimezija sizingathandize amalawi osaukafe , tourism has no value to us , koma mtengo fetelezer komaso zise zadulazi

  • @TisopeChagala
    @TisopeChagala 6 วันที่ผ่านมา

    MCP sikugona tulo ma meeting aja amapqngira kumbali panopa ayamba kubwera poyera ponamizira kuti Press briefing

  • @RajaboSaraivaVicente
    @RajaboSaraivaVicente 6 วันที่ผ่านมา

    Koma ndimakunyadilani mabwana nose chifukwa simumagawa kamba pamenepo ndimakutsatilani mwa chidwi

  • @DixonChimanya
    @DixonChimanya 6 วันที่ผ่านมา

    Komanso musaiwale bwaja kuti boma limeneli ndi la mamafiya
    Koma choti adziwe chochejera sichikumba una

  • @DixonChimanya
    @DixonChimanya 6 วันที่ผ่านมา

    A makosana choti mudziwe agalu amenewa sagona nthawi ina iliyonse amakhala pa meeting chifukwa akudziwa kuti mavoti awavuta
    Ndiye akuyetsetsa kuti mwina awatembenuze anthu maganizo awo koma achedwa
    Dolo adali chilima adamupha uja kuti chakwela apilize koma auponda
    Kuti muone akuyetsetsa koma ndi opusa kwambiri
    Ndipo pa hot current panupo mudziwatsikidzira.kuti abweze kaye moyo wa chilima

  • @moseskavalo3304
    @moseskavalo3304 6 วันที่ผ่านมา

    Achunga you are wrong on Northerners, dziko silikuyenda bwino so whether Chakwera gets Gotani or Mumba still can't got a good number of votes

  • @FemiaNTalakwes-i5v
    @FemiaNTalakwes-i5v 6 วันที่ผ่านมา

    Live for pot Elizabeth sauf African