Mwina Tinayiwala Mmene Zinaliri 2019 Kuti Enafe Tilowe M'Boma?Kotsutsa Kutatiphweteka !!

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 27 ต.ค. 2024
  • Chilima press briefing 20219..

ความคิดเห็น • 11

  • @FelixKachera-je4yk
    @FelixKachera-je4yk 7 หลายเดือนก่อน +2

    kukumbusana nde mkofunikadi kwambiri amalawife chibazaaa too much 😅😅😅😅😅

  • @MartinMajola
    @MartinMajola 7 หลายเดือนก่อน

    Chilima atipulumusa kubagamoyo chilima boma 2025

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu 7 หลายเดือนก่อน

    Akuchokabe 2025 basi, Malawi ali pa moto

  • @greychizaka4088
    @greychizaka4088 7 หลายเดือนก่อน

    Mmalawi sachedwa kuiwala mxiew

  • @LovelyBlini-cu3iu
    @LovelyBlini-cu3iu 7 หลายเดือนก่อน

    Mavuto ndi awa not kale thumba lachimanga linali 7pin, Azam K100, Sugar K450 mafuta ophikila K14,500 nanga lero zilipati yankho mlipeza nokha

  • @YoungScott-p7e
    @YoungScott-p7e 7 หลายเดือนก่อน

    That was unconstitutional bro

    • @Littlefair7
      @Littlefair7 7 หลายเดือนก่อน

      What was unconstitutional?

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc 7 หลายเดือนก่อน

    Kupepela kwa azitsogoleli,amalowetsa,m,boma,ndi citizens of Malawi, anthu osati andale kapena sogoleli,wa chipani aliyese.ndichifukwa,akafika pa mpando po,amaiwala kuti,anaikidwa ndi vote ya munthu wa ziko la Malawi.ndipo,ndi madana ndi Anthu omwe,amatenga zikwanje,ndikumamenyana,nokhanokha.malo,motenga chikwanjecho,kukakhapha,wa ndaleyo.

    • @JonesChingaya-yf4gg
      @JonesChingaya-yf4gg 7 หลายเดือนก่อน

      Ndipo live, Iwo amakhala akumwera limodzi tea

  • @FelixKachera-je4yk
    @FelixKachera-je4yk 7 หลายเดือนก่อน

    kukumbusana nde mkofunikadi kwambiri amalawife chibazaaa too much 😅😅😅😅😅

  • @FelixKachera-je4yk
    @FelixKachera-je4yk 7 หลายเดือนก่อน

    kukumbusana nde mkofunikadi kwambiri amalawife chibazaaa too much 😅😅😅😅😅