John 3:16... pakuti mulungu amakonda dziko lapansi kotero anapatsa Mwana wake obadwa yekha kuti yese okhulupilira iye asatiyike koma akhale nawo Moyo osatha...Chiyembekezo chathu ndi Khristu Yesu basi Sitimadya ndale ife..
The dccccc❤❤❤misewu mphatso ya china kafuku fuku wa saulos chilima ndi namiwa ndi amalawi womwe ifa ya chilima inawakhuza ndi amene ana pusha chakwera kuti akhazikise.a ccap azanga mukuwo kapena muzimu wa Mulungu wamoyo unakuchokerani.
Wabodza iwe nde wachilungamo pa malawi pano? Munthu wankhwitsi ngati iwe moti sudziwa kuti dziko lino linayamba kale kuthandizidwa pazitukuko zake iwe udzavutikadi MCP ikadzangowina iwe udzagwila ukaidi wa nyo ndipo BOMA ndilomweli sitikusintha
Dairy tizingomva zimozi mozi sunganeneko zomanga dziko? Uzikhalira kunyoza mpakana liti? Uzafa ndi bp bon kalindo.you dont have peace.auze anthu akowo azipita ku munda akalime ni nthawi ya kulima pamopa muzadyaso chiteze next year .
Vuto ndi iwe Born Kalindo chifukwa boma ili ndinu munaliyika pamene lilipa bwanji osapanga mademo ife tikusatilani koma zama V N tatopa sopano
John 3:16... pakuti mulungu amakonda dziko lapansi kotero anapatsa Mwana wake obadwa yekha kuti yese okhulupilira iye asatiyike koma akhale nawo Moyo osatha...Chiyembekezo chathu ndi Khristu Yesu basi Sitimadya ndale ife..
Kodi a born kalindo ngt nyumba imene ili ku dowa yo mukuiziwa osangotengana ndi asilikali mukawapeze anthuwo bwanji
Asilikali plus a Police onse ali mmanja mwa chipani cha MCP palibe chingachitike.
Tatopa nawe kalindo ungokuwa osapanga akishoni bwanji
Kodi, impeachment ikuvuta pati?
Iwe kalindo usamanyoze apposition wailawa Kuti ndiwe amene unayambitsa mademo 2020 panga zomwe umkapanga zija
Naweso Bon kalindo ,,akachibwenze kuti ,,ngati ukufuna kuwathandiza auze chabe osati kuwasokoneza
Iye samakaimila bwanji akudziwa palibe angavotere munthu wamisala
Komaso wafika pobowa watan kumudzudzula nzake usi zomwe wapanga zija munthu alibe udindo kuvalika anthu makamaka ku sokhano wa mcp zaziiiii ndiwe oipa kalindo@@victorbanda9039
The DC booooooon kalindo mwana oopsa kwambiri 🎉🎉🎉🎉
Chamba chimasokonezadi ndawonela kalindo pano waleka mademo ungolubwa pa social media watha basi kalindo
Inetu kalindo ndatopa ndi ma vn chifukwa ndinu munayika ng'onazi pampando, pitanisoni pamsewu osati daily heeee zikoli likuyendesedwa ndimamafia aaaa mukuopa chani kukawachotsa mamafiawo
The dccccc❤❤❤misewu mphatso ya china kafuku fuku wa saulos chilima ndi namiwa ndi amalawi womwe ifa ya chilima inawakhuza ndi amene ana pusha chakwera kuti akhazikise.a ccap azanga mukuwo kapena muzimu wa Mulungu wamoyo unakuchokerani.
Kod inu akalindo mukamati anthu akulandila ma billion nde mdziko mukhala chan better mukati ma millions osati billion koma mwati billion mmaidziwa inu
Ayi tikachipeleka kwa ndani koma zisilu.zonse zichoke
Zasiya kubhebha….tizikhalira zobelazo daily?🙄😂😂
inu anthu inu abon zawo zikuyendeyela momwemu umu molalatam komaso anabel uyu chinthucho anachita kukachitenga pa yekha tizizifusaso anthufe
Alamulileno amayi Ako iweyo watikwanano galu iwe palibet chimasintha ingakhale umasokosela galu iwe
Wamantha ndie chisilu kwambili, m'tambo mzako ankapita yekha panseu iwe ukulephela bwanji
Ndiposo
Chilibe enu wake ichi May anasiya chilima
Iweniwopenga
MCP imadziwa kuti akapha chilima palibeso wina amene angamuope..adadziwa amene amawosokoneza athu amenewa adali soulos chilima
💪💪💪💪🔥🔥🔥
Omwe munasogolera mademo nthawi imeneija ndinu ndi anzanu panganinso momwe munapangira kt anthu apite pa msewu
Tatopa ndima audio,afika pobowa,malo mongokodzeka dzamademo lelo😢
Wabodza iwe nde wachilungamo pa malawi pano? Munthu wankhwitsi ngati iwe moti sudziwa kuti dziko lino linayamba kale kuthandizidwa pazitukuko zake iwe udzavutikadi MCP ikadzangowina iwe udzagwila ukaidi wa nyo ndipo BOMA ndilomweli sitikusintha
iwe usi chonde uzipita ku mcp usasokoneze utm uzipita iwe ndi munthu oyipa kwambili
Dairy tizingomva zimozi mozi sunganeneko zomanga dziko? Uzikhalira kunyoza mpakana liti? Uzafa ndi bp bon kalindo.you dont have peace.auze anthu akowo azipita ku munda akalime ni nthawi ya kulima pamopa muzadyaso chiteze next year .
Mmm kusowa umntu
Umunthu
Anthu akakalima akathira mikodzo ya Chakwera zopusa basi ngt ukudya ndlama za Chkwera seka kuchikamwa kwakoko usatinyase apa ndpo palib amadya kwanu
Dzikol la Mulungu mukamayankhula mosamalika mudziziwa kuti Mulungu amakantha usatenge ngt Amalawi amadya kwanu.zaziiiii
Panya pako mwana wa hule iwe akudya za chakwela ndani? Ulesi basi gwilan ntchito zamanja nzambili mbili kuzolowela ma handout.ngati muli aulesi muthila mikozo kumene nanga dairy kunya mwano ntchito mugwila liti ana a satana inu mukungota misonkho yathu dairy njala kwanuko.kodi malawi yoseyo njala ikungovuta iniyo bwanji? Malawi ngwatose uyu agalu inu.nthawi yolima iyi basi kumangokhalira phokoso fotsek
Koma mai ameneyu makani amenewa chilipo chomwe akupangila makanio
The DC
apatu pa khani ya chisankho ngati mukufuna Kuti ziyende bwino anthu a dpp utm mcp pdp ndi zipani zonse ankhalemo kuti ziyende bwino anthu onse a mec achoke mec ikhale ya zipani zonse kuyambili bwedzi wamawa
Zoti ma commissioner aMEC amakhala osankhidwa ndizipani zomwezo simudziwa biggy?…..
Munthuyi mutu wake sukugwila...
Koma mwana iwe ndiwamzelu kwambili
*Kuli Mulungu inu*
The DC ma of the moment