COMRADE CLIF CHINYAMA - SINDIKUOPA ALIYENSE NGATI MUKUNDIFUNA NDIITANITSENI

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 26 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 14

  • @JEFFERYJUMA
    @JEFFERYJUMA 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Good advice mr be careful

  • @BlessingsMakalani
    @BlessingsMakalani 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mumakwana big man 🎉🎉

  • @SABITIKAISI
    @SABITIKAISI 34 นาทีที่ผ่านมา

    ❤❤ Mawu abwino

  • @MaxonKambazithe
    @MaxonKambazithe 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Sakangawine ku conversion manganya sitikufuna kuti akhale msogoleri wathu akagwere uko mulanje central ndiyotemberedwa muone manganya, nankhumwa and Brown mpinganjira mulungu anthu amenewa adawapasa mwawi koma analerephera okha iwowa

  • @SaopaThomas
    @SaopaThomas 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    😂😂😂mawu koma amenewo pajatu chilungamo chinayandikana ndimwano ing'alure wina azanama😂😂😂😂

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kkkkk awuze choona kodi unali kuti mzanga thawi yonseyi, ndikufuna athu okhala ngati inuyo big

  • @MaxonKambazithe
    @MaxonKambazithe 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Zikomo kwambiri achimwene pakufunika mademo akhalapobe ku machine ali ku MEC anabero achoke ngati sachoka mademo alipo ndithu ifeee amalawi tooonse ambiri sitifuna machine aja

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Achimwen Mulungu adxikudalisan zikuoneka zopusa apap koma mau amakom akagonera osatop mchimwene wanga from the moon we r together achimwen

  • @VeronicaMatiki
    @VeronicaMatiki 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndipo Kodi Gulu la kuphalo iwowo sadzafa, Mwina kaphanso Munthu Nzeru zolamulila dziko ankhala nazo 😂😂😂😂

  • @chippakaribafox2865
    @chippakaribafox2865 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nuff respect!

  • @FestonStima
    @FestonStima 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    👌🔥🔥🔥🔥🔥🔥💯

  • @GiftMitochi
    @GiftMitochi 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    🙏🙏🙏💪💪💪🔥🔥🔥

  • @MpateRashid
    @MpateRashid 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Festvo yandiwaza chipani cha oyimbatu osati ndale

  • @Khadija-q9r
    @Khadija-q9r 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Achintengela 😂😂😂😂😂

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kumwambako kumve kulira kwa ana anu Mulungu khululukani zolakwa zathu