COMRADE CLIF CHINYAMA - WAIBWERETSA POYERA ATATOPA NAZO

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 26 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 261

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole วันที่ผ่านมา +21

    Bon kalindo adanena kale kuti kupha ine kubwera Ena mafana omwe ndi a chabe kwambiri uyu ndi namanyonyolo mm bravo brother ❤❤

  • @PetrosMunthali
    @PetrosMunthali วันที่ผ่านมา +14

    I love this guy 🎉🎉🎉🎉 his reasoning on the agreement is very perfect.

  • @IshmaelNgeyani
    @IshmaelNgeyani วันที่ผ่านมา +22

    Commission of inquiry yanga ndi iyi kamlepo kalua,born kalindo,anamiwa,lyton mangochi,Norman chisale,Rv kambiri comrade mtanyiwa, bakili tv,Elizeyo mtalika,a njawala wakubanja kwa achilima senior kapeni munthu mmozi wa onse oferedwa comrade cliff chinyama,Timothy mtambo,Sameer Suleman

    • @BrightZionga
      @BrightZionga วันที่ผ่านมา

      🎉🎉🎉🎉

    • @thomaswyson-e2q
      @thomaswyson-e2q วันที่ผ่านมา +2

      Iwetu ndiye wasankha bwino komit imeneyo ndiyeingabwelese chilungamo chenichen

    • @eliffagondewe8214
      @eliffagondewe8214 วันที่ผ่านมา

      😂😂😂😂🔥

    • @IshmaelNgeyani
      @IshmaelNgeyani วันที่ผ่านมา

      @@thomaswyson-e2q nanga apanga release commission of enquiry opanda kalikukumwe kamenekaka

    • @MveraNambala
      @MveraNambala วันที่ผ่านมา

      True​@@thomaswyson-e2q

  • @georgesmart3791
    @georgesmart3791 วันที่ผ่านมา +5

    Comrade Chinyama ndi namandwa sure ndipo akukamba zoona zokhazokha... salute ❤❤❤❤

  • @aggogokina8992
    @aggogokina8992 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Komatu munthu walankhula chilungamo uyu guys. Ndipotu wanena zinthu zomveka kwambiri. Ee uwunso ndi mtunda okwera ndizikhadabo simasewera. Akulankhula live mopanda mantha💪💪💪

  • @M.shukriAdams
    @M.shukriAdams วันที่ผ่านมา +9

    Ndipo live imfa imene inja imandiwawa zed choipa chisata mwini

  • @lytonmwiya-b1g
    @lytonmwiya-b1g วันที่ผ่านมา +4

    This man has an organised brain, I love this guy

  • @ChidaPhiri
    @ChidaPhiri วันที่ผ่านมา +8

    150% mau awa ndioona ndithu ndipo chonde aMalawi mau awa tiwatenge serious aChakwera nthawi yawo yakhala president inatha ndithu. Mgwirizano unatha nawo aChakwera anayenela kutula pansi upresident

  • @DeliaKaduya
    @DeliaKaduya วันที่ผ่านมา +7

    Ambuye akubiseni mmapiko mwake malume, cz chikangawa safuna kuzuzulidwa ngati pena pake sipakuyenda bwino, anthu oterowo akumasowesedwe

  • @johnjoachim3820
    @johnjoachim3820 วันที่ผ่านมา +9

    Uyu ndiye sakuopadi coz ndiza live ❤

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo วันที่ผ่านมา +15

    Uyu ndiye sanyengelera akung'alura eeee

  • @MakabaBauleni-c2i
    @MakabaBauleni-c2i วันที่ผ่านมา +5

    Akamangidwa palibe omusata a Malawi comwe timadziwa ndikungocemelera tili kumastand akagwa ground tonse balala nde conde tiyeni timpatse munthuyu sapoti cz akuankhula zikungamo zonkha zokha ,monga ndli kumbari yanu akulu olo mukumane ndi zofinja ndli pa mbuyo panu

  • @MalickMkweche
    @MalickMkweche วันที่ผ่านมา +9

    Chakwera wabararika mix achina ntanyiwa bakili tv bon kalindo

    • @Belinda-c6e
      @Belinda-c6e 23 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Ndipo amagofuna atawapha kma alibe kuthekera😢

  • @BrightZionga
    @BrightZionga วันที่ผ่านมา +1

    Khokhokho samala mmbale iyi ndichikangawa asakupeze bravo ❤❤❤

  • @trifoniachilunda6263
    @trifoniachilunda6263 วันที่ผ่านมา +6

    Kachilumamo aka Koma bola asakusowese bro❤

  • @JohnWame-u3l
    @JohnWame-u3l วันที่ผ่านมา +3

    Yeah, exactly,,.Koditu Ndi sikusinja.....

  • @OssmanAbubaker-v7t
    @OssmanAbubaker-v7t วันที่ผ่านมา +2

    Zoonadi brother chilungamo. Osaopa osafooka osatopa. Brother Mulungu Zikutetenza we are supporting you

  • @lingsonmitunda293
    @lingsonmitunda293 วันที่ผ่านมา +1

    Cliff ndiwe superpower asee

  • @aggogokina8992
    @aggogokina8992 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Pano anthu atopa bas ndipo alimba mitima akungoswa chilungamo mopanda mantha 💪💪💪

  • @LydiaMsazurwa
    @LydiaMsazurwa 21 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    A Wilson Jackson,mumutu mwanumo ,anthu akumukayikilani ngati,ulibwinobwino,zinthu zikuchita kuwonekelatu ,kapena ndikuwuzilenitu bwino kwambiri mwina mundimva,Awilson Jackson,Muli ombwambwana kwambiri,umboni ukuchita kuwonekelatu,mukufunilanji umboni wina

  • @StarchJonas
    @StarchJonas 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Born Kalindo sali yekha. Ng'alulaisation group yabwera kuzakhala.

  • @cmsanyama200
    @cmsanyama200 วันที่ผ่านมา +2

    A Chakwera chifukwa cholephera kupanga ziganizo mopanda kudalila owazungulirawa,apwetedwa pa zinthu zoti sanatengepo gawo nkomwe MOTi chimene akachita after the incident nduna zonse zokhudzidwa akanazichotseratu maudindo kuti Iwo akhale clean!

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 วันที่ผ่านมา

    True man Chakwera kaya akuganiza bwanji? Munthu uyu wadusa pa nebukatinezala or herodi kuzimva anthu amene asankhidwa asapite ku State kukawalumbilisa kuri chimuzimo choyipa kumeneko. Amalawi mukuziwa kuti kumalawi tili ndimutumiki wa Mulungu wamoyo yasini gama chakwela ndi kabineti yake apite kwayiye akalumbire pamaso amutumikiyo ngati sanachite chiwembu akambwera ndimoyo koma ngati anachitadi aliyese muzaona chimene chizamuchitikire.palibe oposa Mulungu ngakjale akhwime bwanji kumbukirani eliya ndi ambala eliya anapambana

    • @MeddyNdalama
      @MeddyNdalama วันที่ผ่านมา

      😮

    • @BrightZionga
      @BrightZionga วันที่ผ่านมา

      ​@MeddyN🎉🎉🎉🎉dalama

  • @MarcyKamaga
    @MarcyKamaga วันที่ผ่านมา +5

    Amen ambuye akudariseni achimwene

  • @EmilyEmuzy
    @EmilyEmuzy วันที่ผ่านมา

    That's true Brother. But this World hate the truth

  • @papelariareis.e.
    @papelariareis.e. 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Best one ❤❤❤❤ koma chinkhumba chaona haha😅😅

  • @HusseinKalima-f4z
    @HusseinKalima-f4z วันที่ผ่านมา +2

    Imeneija inali plan ndipo anayiyambila patali, angakhale imfa ya Kasambala ija anachitaso kuphedwa, anapanga plan yopha Kasambala podziwa kuti anali Lawyer wake wa Chilima komaso anali pachimzake kuyambila kale, so anati tiphe kaye Kasambala ndipo Chilima timupangile chiwembu akamapita ku maliro a Kasambala, ndi mmene anapangila, so pakali pano sikuti iyi ndi commission of Inquiry no, apa ndikukaniza kuti ma Demostration asapangike, chifukwa zikanakhala za chilungamo sibwezi atapanga exclude aku banja komaso azipani zina za ndale.

  • @mollymasangano473
    @mollymasangano473 วันที่ผ่านมา

    Kuyakhula kwa chidunji inutu Mulungu adzikubisani ngati Bakili muluzi TV, ndi. COMrade NTanyiwa ,komadi Chakwera sakuyenera kuyima upulesidenti because ALLIANCE inja ndi Zomwe anangwirizana iwe tsolongo ,Ulendo uno unakakhala wa Chilima unfortunately he no longer there may his soul continue to rest in peace Atati Chakwera wavora kuti sayima ndekuti ayima ndi Manganya😅😅😅😅 Dzimvete mutolo❤

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza วันที่ผ่านมา +2

    Kuyankhula mwa chilungamo our brother❤❤❤

  • @MrMagombo
    @MrMagombo วันที่ผ่านมา +2

    Maliro aja munapita nawo ku Parliament ndiye Pano akalumbile ku Parliament.

    • @BrightZionga
      @BrightZionga วันที่ผ่านมา

      Mwana wa chikangawa

  • @AstonMuneer-x3i
    @AstonMuneer-x3i 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Respect bro kuyankhula chilungamo

  • @LindaMalunjika-k4l
    @LindaMalunjika-k4l 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zovuta....koma olo atatani izi zidzaululika....zizezakhala poyera koma a MCP ayasetsa kuphimba chilungamo koma awawa alephera.....A Malawi siopusa ayi ndipo timaona

  • @StyceChikwenga
    @StyceChikwenga 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    All the way from former capital city of Malawi

  • @LydiaMsazurwa
    @LydiaMsazurwa 22 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Achakwela kodi ndimunthu ,oganiza bwanji? Kodi adaphuziladi awa? Kapena anangophuzila chizungu kunja?

  • @gladysmanthimba7851
    @gladysmanthimba7851 18 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Mau koma amenewo 🎉

  • @Chikwawa
    @Chikwawa วันที่ผ่านมา +1

    Mdala ameneyu wasavuka, akufunanso adyenso secretary general, Dzuwa likuswa mtengo Kaliati.

  • @ChrispineMuzungu
    @ChrispineMuzungu วันที่ผ่านมา

    I love the courage boss bg up🎉🎉

  • @Chikwawa
    @Chikwawa วันที่ผ่านมา +1

    Apa ndiye wabaya ndipo panalibenso chokhazikitsira inquiry.

  • @chifundokachola7532
    @chifundokachola7532 วันที่ผ่านมา +3

    Mmene mulili mmalawi muno,panopo tilibe a opposition kutereko tiyamike anthu ngati aawa akumabwera pa social media wa ndikumalankhula zomwe sizikuenda bwino coz a opposition angokhala chete....

    • @SaedJafari-z7r
      @SaedJafari-z7r 17 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Inu amenewo mwamasukatu

  • @MosesTangwe
    @MosesTangwe วันที่ผ่านมา +2

    Ichi ndiye chilungamo chake👏💪

  • @ShillahLawrence
    @ShillahLawrence 23 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Commission of enquiry imakalumbira Ku Parliament osati Ku Nyumba ya munthu ayi

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu วันที่ผ่านมา +1

    Chilungamo ndi chimenecho palibeso chilungamo choose apapa, amalawi ambili amaopa kumasula chichewa ngati ichichi ,palibeso kukamba nkhani chilungamo ndiichi malawi akudziwa koma matha kumasula kunena chilungamo

  • @DjshukulanGift
    @DjshukulanGift วันที่ผ่านมา

    Kwambili aa akuona ngat ife sitiziwa ngat ? Asatiphimbe kumaso

  • @Chikwawa
    @Chikwawa วันที่ผ่านมา +1

    Mbava, yakuba u leader, asiye akalape koma zinazo ndiye mmmm Mulungu zangamve, kupha.

  • @UmariBashiri
    @UmariBashiri วันที่ผ่านมา +2

    Zoonadi Brother zikumveka

  • @JeanBanda-zy6wu
    @JeanBanda-zy6wu วันที่ผ่านมา

    Wise man, may you be protected by the blood of Jesus anthu olimba mtima ngati inu ndiwochepa

  • @JailosIsaac
    @JailosIsaac วันที่ผ่านมา

    Help Malawi God 🇲🇼 🙏 Rise people are anxious to see the truth of the plane crash
    It's still paining to those that have humanity feelings eeeeeishhhh

  • @ChidaPhiri
    @ChidaPhiri วันที่ผ่านมา +3

    Akulu inu mukunena chilungamo ndipo zoona Chakwera ayenela kuimitsidwa ndithu. Chilungamo chioneke mapepala atulutsidwe ndithu. Asakhale pa balot

  • @FestonMoopa
    @FestonMoopa วันที่ผ่านมา +1

    Yes Uli boooo tonse inatha palibenso chifukwa copitilizila kulamula

  • @Chikwawa
    @Chikwawa วันที่ผ่านมา +2

    Ameneyu ndiye anayenela asatenge gawo posankha anthu.

  • @LydiaMsazurwa
    @LydiaMsazurwa 21 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Awison Jackson,musamayankhule ngati mwina ,inu mukuziwapo kanthu pa Imfa ya Chilima

  • @AARONCHISUKAMZION-we3vp
    @AARONCHISUKAMZION-we3vp วันที่ผ่านมา

    Anthu anachosa manthongo mmaso,
    1964 inapita
    Ngati palibe Cha kabisila ku State House,
    Ndikuti kwina kungabisike china chilichonse muboma limeneli
    Babulo agwe basi
    Kaya Ali pa Swindi
    Basi agwe pansipa
    😢😢😢

  • @AudtinEliya
    @AudtinEliya วันที่ผ่านมา

    Koma ndichofukwa chiyani boma rikumanga anthu oyakhura nzakukhosi?
    Bwanji osamanga anthu amene akupha anzawo bwaji.pamenepa dziko ramarawi kuribe purenzident.

  • @BiliatMzungudala
    @BiliatMzungudala วันที่ผ่านมา +1

    Anthu opanda mantha ngat awa ndi onwe akufunika mdziku mwanthu muno😢

    • @SaedJafari-z7r
      @SaedJafari-z7r 17 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Nanga iwe

  • @DixonChimanya
    @DixonChimanya 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Izo ndiye ndizoona ndithu
    Chilima adapita chifukwa chidali chiphinjo kwa chakwera chifukwa cha mngwirizano

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe วันที่ผ่านมา

    Eya Anthu onse asa vote.kufikira chakwera wachotsedwa pampando.waupulezident chifukwa chakwera anapha chilima.ndipo zisankho.zilephereke basi ..chakwera achoke basi malawi adzasankha pakalhala pulezident wina wosankhidwa bwino.amen

  • @Andrewmwamadi
    @Andrewmwamadi 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ada inuyo ulemu wanu anthu amalankhula koma inuyo palibeso ndi 1 keep it up more fire God is in control ndnu otetezedwa

  • @RosinaPatel
    @RosinaPatel วันที่ผ่านมา +2

    Anthu sakuopa Pano..chilungamo ndi chowawa

  • @Creslevison-vj2sl
    @Creslevison-vj2sl วันที่ผ่านมา

    Eeee nkhani iyii man mwang'alura ngamo kwambri i❤ this one

    • @Bonisiwentamo
      @Bonisiwentamo วันที่ผ่านมา

      Zoona zake zimenezo mofaya

  • @LydiaMsazurwa
    @LydiaMsazurwa 22 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kodi Ndichifukwa chiyani Achakwela,pankhani ya kafukufuku,akuyikapo ,cholesa.

  • @brianjames211
    @brianjames211 วันที่ผ่านมา

    Everyone must have not accept this to happen, no enquiry should start and nobody must not accept the positions, the ball is gonna be in your court and the Malawians will tare you apart believe you me

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu วันที่ผ่านมา

    Kodi Mr. Cliff Chinyama unali kuti nthawi yonseyi a Malawi tikufuna munthi wa mphamvu ngati zimenezi? Eish! Ukubaya penipeni osati masewela ayi. Ukukwana brother.

  • @Belinda-c6e
    @Belinda-c6e 23 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    ❤❤❤❤❤clif chinyama ndpo ndi zona athu ndi oipa

  • @JonaSato-j8e
    @JonaSato-j8e วันที่ผ่านมา

    Big bro the truth is good ❤😂😂🎉

  • @MarcyKamaga
    @MarcyKamaga วันที่ผ่านมา +1

    wakufa sakuziwika oroso iwowo ankhoza kufa achakwerawo ndipo ife amarawi atitora ngati ife ndife zisiru koma akunama murungu ariko kumwamba uku ayankha

  • @HawaHussein-d4l
    @HawaHussein-d4l วันที่ผ่านมา +1

    Inu nde mwaloza point nde nde nde mchomwe anaphela nde azisankha anthu amu enquiries ayi sisatheke asankha achipani chake kuti abise chilungamo

  • @ShillahLawrence
    @ShillahLawrence วันที่ผ่านมา +1

    Tikati titsatile malamulo , a Chakwera anasankha a Maiko Ussi potsata chilungamo chamgwirizano ndi Malamulo. Koma a Ussi ndi a UTM Di? Ngati sali a UTM ndiye mwaphwanya malamulo

    • @Mpungwe123
      @Mpungwe123  วันที่ผ่านมา

      Very good ndiye posunga malamuro pompo amulore MANGANYA aimiletu 2025 ngati president WA tonse alliance

  • @MussaAndreQuenessi
    @MussaAndreQuenessi วันที่ผ่านมา +1

    Mau away chikangawa ndi gure

  • @DumisanPhiri
    @DumisanPhiri วันที่ผ่านมา

    Kunali kusewelesa amalawi kumeneko tizingokhalila kuvota?

  • @InnocentBanda-ze8de
    @InnocentBanda-ze8de 23 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Brother ❤🙏💪🇲🇼

  • @LydiaMsazurwa
    @LydiaMsazurwa 21 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Awilson Jackson Kodi simudamve zoti Ndege yachilima idachita kucheledwa?simudamveso zoti vice adachosedwa lamba ndisapatonso zidachoka?ngakhale ,jombo za Asilikali adachosa ,simudamve izizi inuyo,Awilson jackson ,simukuona nokha,kuti President,sakukondwela ,ndikafukufuku wangozi ya Achilima?
    Kodi awilson Jackson,zonse zimene zikuchitika muno mumalawi,inu ndinu achilendo kapena tiziti ,mwamwa kadansana?

  • @ChristianMalingamoyo
    @ChristianMalingamoyo วันที่ผ่านมา +1

    Muuzeni muuzeni anapha yekha anthu omwe wawasankha wawalowesera kale ndalama.

  • @MussaZakeyu
    @MussaZakeyu 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Bola akanva chakwela asakuphe chifukwatu BOMA ili limadana ndichilungamo

  • @JamesChiphazi
    @JamesChiphazi วันที่ผ่านมา

    😢kafukufuku yese mwini wake akhale kamangila ndi asembe akatolika komaso brather wa saulosi ndi mwana wake baai ena oseo ndi boza

  • @CathreenKadwala
    @CathreenKadwala วันที่ผ่านมา

    Munthu wankulu inuyo ndi azanu onse Antanyiwa, Bakili TV, the DC, bro sallo, Lyton mangochi ulemu wanu nonse

  • @kasambegrace
    @kasambegrace วันที่ผ่านมา

    Kung'alura chilungamo chilungamo sichiwopsa ndipo chiziyenda ngati mtsinje Satanayo ndiwaboza ndipo kwake ndikupha ndikupha amen mpingo. Ambuye akutetezeni pamene mukuyakhula chilungamo

  • @AdaYusuf-u3f
    @AdaYusuf-u3f วันที่ผ่านมา +2

    Tiye nazo muzasangarara masiku akubwwra

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 วันที่ผ่านมา

    Anthu aku Malawi paokha saganiza amafuna kuti anthu ena waganizire. Ku nyumba ya president kumakhalanso office yake inu za mboma simukuzidziwa khalani chete chifukwa Bon Kalindo wanena male olumbiritsa ndiye aliyense osaganiza bwino angonena zomwezo.Baba mukanali mumadziwa malamulo adziko simukananenazi chifukwa inuyo muziauza anthu kuti mgwirizano siuli mmalamulo adziko ndiye popanga mgwirizano tichenjere ngakhale Chihana pamene akupita ku DPP akudziwa kuti chirichonse chikhoza kuchitika.

  • @FrankChanza-l3g
    @FrankChanza-l3g 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Eya kwambili chakwela ndi yemwe anapha chilima zopusa zanji zomwe qkuchita akuwona ngati sitimuiwa

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule 23 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Good boy ❤

  • @HusseinKalima-f4z
    @HusseinKalima-f4z วันที่ผ่านมา

    Plan yawo yomupha Chilima inali yozama,ndichifukwa anayamba kupha Kasambala ndi cholinga choti afafanize umboni wazina ndi zina poti anali Lawyer wake ndiyenso amene amatha kudziwa zambiri even zokhudza Alliance yazipani zawo, so ndichifukwa chake pakalipano zinthi zikuoneka ngati pakusowa poyambira pofuna kupanga kafukufuku kunkhani yokhudza alliance yawo

  • @AndrewjemesJemes
    @AndrewjemesJemes วันที่ผ่านมา

    Uganiza kwa booh zoona izi rest in peace legend of politics in malawi SKS

  • @lightwellsilumbu
    @lightwellsilumbu วันที่ผ่านมา

    Sindinayambe ndamva chilungamo ngati chimene ndamva lero. Zukhala ngati zumveka ndithu.

  • @Georgechimfuti
    @Georgechimfuti 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Musatiyambitsire zinthu za chabe .you are in China and you feel you can speak your mind that's your constitutional right. Chakwera has also his own constitutional rights as well. If you have evidence come in the open rather than talking nonsense . Nkhondotu itha kukhalapo but know that no one will be spared .

  • @FortunePhiri-kl7oe
    @FortunePhiri-kl7oe วันที่ผ่านมา

    Kugaza brother man

  • @richardarmittage1693
    @richardarmittage1693 วันที่ผ่านมา +1

    Ndipo ndiye ndizoonadi chilungamo chake ndichimenechi

  • @AlickJinamu
    @AlickJinamu วันที่ผ่านมา +2

    Changanga wayowadyela

  • @EvelynMaston
    @EvelynMaston วันที่ผ่านมา +2

    More fire

  • @Staphelsavimbindhlovu
    @Staphelsavimbindhlovu วันที่ผ่านมา

    Ulemu wanu big man 🫡🫡🫡 iwe ndkatundu wenwen

  • @TracyBanda-i2g
    @TracyBanda-i2g วันที่ผ่านมา

    Born kalindo watumat uyu kuti kaishoshe kuti tiiyambise yamanja ,nkuona choncho, sangalimbe mtima padera muona zowopsa Malawi ndipo a police azafa ochulula chifukwa mfut kuzaomba simuzatuluka chipolopolo muzatuluka utsi ndipo anthu azapha apolice ndimiyala komaso mikondo samalan amcp !!!

  • @WisdomJeremiah-s3y
    @WisdomJeremiah-s3y วันที่ผ่านมา

    Nafe tudabwa kodi achakwela amalingalila bwanji pamodzi ndi mbava zinzao??? Malawi tagona kwambiri ndiye Kuti eeti?? Ma demo ankapanga kale aja anapanga nthawi yolakwika amafunikila panopa Koma dzuoneka ngati Kuti tuopa tonse tungolankhula pakamwa basi

  • @husseinmponda
    @husseinmponda วันที่ผ่านมา

    Koma uyu😂 walimbadi mtima sakumuopa jezbell

  • @AnnaPhiri-b8t
    @AnnaPhiri-b8t วันที่ผ่านมา

    Okha Mr chikangawa, okhanso ndikhesa mwazi

  • @MacPherson-zq2uz
    @MacPherson-zq2uz วันที่ผ่านมา

    amalawi enanu ndinu omvetsa chisoni kwabc...zikuonetseratu kt cimene muli simukuchidziwa,may god help you

    • @SaedJafari-z7r
      @SaedJafari-z7r 17 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Iwe manyi ako mapwala ako kulankhula mokunya anthu onsewa opusa komaiweyo ndiwe galu kwabasi

  • @EmmanuelWhite-h7e
    @EmmanuelWhite-h7e วันที่ผ่านมา

    Uyu nde bakili muluzi akunama uyu akuonetsa nkhope

  • @Christopherchapeta-q2j
    @Christopherchapeta-q2j วันที่ผ่านมา

    Zimene. Zikudabwitsa ayika commission of equerely koma. Osanena ku mtundu was a malawiyangoikidwa. Mokakamizidwa

  • @MayimunaZuber
    @MayimunaZuber วันที่ผ่านมา +1

    That's true bro

  • @rashirdbanda8204
    @rashirdbanda8204 วันที่ผ่านมา

    I love you brother ng'alula osaopa osatopa

  • @Musa1828-l5d
    @Musa1828-l5d วันที่ผ่านมา

    Chilungamo osaopa brother 🔥🔥🔥🔥🇲🇼❤️

  • @NedsonKamwaza
    @NedsonKamwaza วันที่ผ่านมา

    Exactly big man