ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Or mutaika mulingo koma akabwera athabe bas,ufa economy sapanga ulibe kanthu 🤣🤣🤣🤣
Muziti funsilako kuti ma generator or zigayo za diesel azipanga bwanji poti mwalesa zigubu
Kkkk yomweyo chikangawa zamuvuta basis chilichonse chikukhala panzuwa
Anthu oti sanapangepo ndale olo kukhalapo mu boma ndi awaso akulephera kuyendasa bomawa. Muuzeni Ntumbukayo Kuti zimenezo simfundo
Amalawi tikhale serious ndiye dela lawolo akazawina amene sakumufuna azizativuta kuti zisankho sizinayende bwino