Koma ya yokhayo ya ma ARV kuti muyambe kugulitsa ndiye ndi boza tanthauzo lanu inu aboma ndi chani?mukufuna muziphabe anthu? Kodi inu nonse amene mumagwira ntchito boma ngati achipatala kwanu kulibe anthu odwala omwe amalandira ma ARV's ARV's ndalama yogulira mankhwala mwezi ndi mwezi achiitenga kuti ?just imagine this is not fair 🙆♂️🙆♂️🙆♂️
Kodi mcp ikufuna khondo, chakwera ndiamzako usationongere dziko lamalawi wanva chisiru chamunthu iweyo kwambiri,koma uziwe kuti mkayidi akadya nyama kundende sikuti watuluka ayi, one day is one day soon u will get problem galu kwambiri munthu oipa iwe
Number one
Welcome back comrade.
Mbambande 💪🏽 munabwera kudzakhala inuyo ✍️💐
Mcp ikhoza kupha aliyese wandale kaya kumanga anthu Koma zowina kulibe chakwera mkutumbo kwake ndithu
Takhala tikudikilira Mr comrade apa mwabwer chisale sangamukwanise
P0❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Welcome back mr mtanyiwa 🔥🔥🔥
Yesesani Mr Mtanyiwa, ngati akufuna kumanga Chisale Valentino amangidweso
Ndimadikila inuyo paja kunatilinjeza ❤❤
Uuuuuuuu kulakwa phaka kutengera athu alikuzuzika ndikale zooona😢
Comrade umatiyimilira
Mcp yarephera basi kuyendesa dziko amalawi atopa ndi chipani chakupha satanic team muzipita crocodile team
COMRADE NTANYIWA, MAPHWIYA MULHUPALE , INUYOO NDI AKATUNDU PALIBE CHOBITSIKA PANSI PANTHAMBO
Big munasowa Tili mu ichope mozambiki. WA kumalawi. Takumana Ndi yaiwisi nkhanga zaona
Comlade nyimbo imeneyi imanfibandula kwambasi❤❤❤❤❤❤❤❤❤ntanyiwa
Only hope Limpopo FM 🎉
Mulungu alipo wamphamvu awonesera kuwopsa kwake chifukwa dzikoli si la achakwera ndi la mulungu GENESIS 1
APM 🌽🌽 My President & DK.🔥🔥
My Vice President
Alomwe okha okha we can't do that
Mtimadikilira.wailesi.ntanyiwa❤
Kodi kulamulira kumakhala kokakamiza?
Chitani manyazi abusa onyenga inu.
Komatu chikudziwa kuti anthu akuchikana
@StandwellNjoka ndichiwanda ichi mu form ya munthu.
Bola tonse tisadzatuluke kukavota ingofera fawo
Inspector Kalambo ndinu woyipa mtima ndipo mwayaluka.
boss ntanyiwa mwabwera ndiye andale onse amene akulamulila azinyera
Makolo ena akutiberekera achina Goliyati ndithu mzimai wa mzeru sangabereke goliati ngat uyu mkumazuza anthu
Zingowotchedwa zimatowazo basi payere payere
Anthu omweo akuti mcp ndi vote ya mutu sukugwira mcp manyi
Antanyiwa inuyotu changotsala ndikuti tenga ndikuti tsogolera kukadzimenyela nkhondo
May the The Lord continue to protect you
Mulungu aKusungen ndi moyo wautali , ndipo azikudalitsan ndi mzelu zochuluka
Kd comrade ulamulilo wa adad uja timafuta tikangosowa pang'ono kumachitika mademo zithu zikangokwela pang'ono anything change suddenly amakhala mademo koma chomwe chikundidabwisa ulendo uno mafuta akusowa hvy zithu kukwela monyasa and tingoti zafika poilatu koma mademo sitikupanga bwaj a Amalawi kd boma aku user strategy yanji yomwe athu ikutipusisa
Umakwana ntanyiwa awuzileni mayesowa amenewo bomali liri pa katangale kwambiri ineyo ndinapita kubwayila ndi mwana anatchyoka mkono kt amumange chinkhankha akt ndipereke ndlama yokwana 9000 Ngati sindipeleka ndiekt ndibweretsa choncho Moti ndinapelekadi Malawi anthu sakutifuna anthufe ndichipatala cha boma chomwe kulipilitsa nanga kd momwe tikuvutililamu tikadwala tidzilowera kt ife ndlama tilibe
Koma ya yokhayo ya ma ARV kuti muyambe kugulitsa ndiye ndi boza tanthauzo lanu inu aboma ndi chani?mukufuna muziphabe anthu? Kodi inu nonse amene mumagwira ntchito boma ngati achipatala kwanu kulibe anthu odwala omwe amalandira ma ARV's ARV's ndalama yogulira mankhwala mwezi ndi mwezi achiitenga kuti ?just imagine this is not fair 🙆♂️🙆♂️🙆♂️
Mumatiyimilira boss
Ana kamuna comrade Ntanyuwa
Kumafunabe mcp chonsecho mukugona ndi njara hhhhhhhhheeeeeee😂😂
Alomwe muli pachi ntchito ndi kachipani kwanu ka dpp koma mwatiwonongera ziko
Athu oipa kwambili agalu awa mcp
Ndipo boma ilili alisiilad panjir mbuzi za anthu izii
Kodi mcp ikufuna khondo, chakwera ndiamzako usationongere dziko lamalawi wanva chisiru chamunthu iweyo kwambiri,koma uziwe kuti mkayidi akadya nyama kundende sikuti watuluka ayi, one day is one day soon u will get problem galu kwambiri munthu oipa iwe
Kodi chakwelayi alibe makolo Ake kuti amulangize chifukwa izizi sizoona ayi
Game yache ikhala ku mcp masamba ku DPP masamba chisale ku ndende valentino kundende ndiye nkhaniyo
Kodi Gard of owner ndichani
🎉🎉🎉🎉
Pano ku army anthu ambili amagwiritsa ma satifiketi osakhala awo nawonso afufuzidwe ndipo amanga ambili
Comured osaopai achoke bas mcp
Koma ndi phavu ya MULUNGU sizitheka chilichose chomwe kufuna milandu umenewo usitha
I thought mumati simuyankha ma calls koma ma text okha
Kkkkk
Amcp mukuchepa mukabadwenso
iwe ife vote yathu ndiya MCP
Vote yako iri mgulu la mavoti a zitsiru.Tingakudandaule ife?Uzinena kuti voti yanga osati voti yathu.
Za ziiii
Aaa iwe ndiwe ulibe mzeru chitsilu chamunthu iwe nkhuku yeniyeni pita ukavote mcp yakoyo. Koma DPP BOMA
Ndichisiru chosecho chakanika kulima fertilizer akanika ku gula basi kuchikamwa mcp mbuli iyo
Yaaaa