Ena Akuti Malawi Akufunika Kugula Zindege

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 11 ก.ย. 2024
  • Morton akuti nje.

ความคิดเห็น • 18

  • @GeraldShaba
    @GeraldShaba 2 หลายเดือนก่อน

    Auzy big MN kumalawi ndiku manda bas kumasano😅😅😅😅

  • @InsideMalawi
    @InsideMalawi 2 หลายเดือนก่อน

    Ndege zikufunika wawa.. nkhani si imfa yonkha komanso ngozi zokugwa mwa dzidzidzi.. dziko lopanda ndege sidziko wawa..
    Mwanena bwino kuti ndege sizichita ngozi kawiri kawiri ndipo iyi sinachite ngozi koma yagwetsedwa ndi amaliwongo a pansi pa nyanja.. timenya nkhondo komanso tiwina mu nthawi yoyikika..

  • @EmmanuelVSPhiri
    @EmmanuelVSPhiri 2 หลายเดือนก่อน

    Akamuna❤

  • @MissionStafford-pl8wy
    @MissionStafford-pl8wy 2 หลายเดือนก่อน

    True

  • @Amgwagwa
    @Amgwagwa 2 หลายเดือนก่อน +1

    Walankhula bwino osati Zija nthawi Zina umalankhula zotukwana

    • @petrokagona1708
      @petrokagona1708 2 หลายเดือนก่อน

      Koma ndiye kutukwanadi. Kutukwana mpaka kumuposa satana. Kkkkkkkk.

  • @KondwaniOdala
    @KondwaniOdala 2 หลายเดือนก่อน

    Penat Baghaya umagwra mutu km pena manyqka

  • @jamesgama5489
    @jamesgama5489 2 หลายเดือนก่อน

    Koma iweyo utakhala mayor wa mzinda wa lilongwe ukhoza kusintha zinthu

  • @Michaeldango-nj5vp
    @Michaeldango-nj5vp 2 หลายเดือนก่อน

    Perfect said

  • @RemmieNgomba
    @RemmieNgomba 2 หลายเดือนก่อน

    Ndaonako munthu chakumbuyoko.

    • @mutafire
      @mutafire  2 หลายเดือนก่อน

      ndimayesesa kupanga avoid anthu of course

    • @RemmieNgomba
      @RemmieNgomba 2 หลายเดือนก่อน

      Understandable.

  • @petrokagona1708
    @petrokagona1708 2 หลายเดือนก่อน

    Ayi. Akulu imodzi kapena ziwiri ndege zikufunika. Kumbukirani Namondwe kwa mkando adafunanso helicopter for rescueing victims. Chopper may be required even for the poor.
    Aim high. Kodi ma basics tilimbana nawo mpaka liti? 1964 up to now, should we still be talking of basics?

    • @mutafire
      @mutafire  2 หลายเดือนก่อน

      that is how it works, no basics, no luxury. No shortcuts.

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w 2 หลายเดือนก่อน

    Malawi yikupangatsa manyazi, zoona kuchita kubweleka ku Zambia ndenge! Ndipo ukunena zoona misewo kulibe . Koma a mu bomamo akungowononga ndalama.

    • @mutafire
      @mutafire  2 หลายเดือนก่อน +1

      akuononga chifukwa sakulandira punishment

  • @bonfaceordhurrohgondwe1366
    @bonfaceordhurrohgondwe1366 2 หลายเดือนก่อน

    You always look down upon your country iweyo... Your in China what's your impact on someone here in Malawi

    • @mutafire
      @mutafire  2 หลายเดือนก่อน +1

      I am a vlogger.