Wa hit a bwino kupepesa mtambo ku mtundu wa Malawi unazitenga for granted kuli konse ukupita uwapepesedi a Malawi inawononga Malawi ndi iweyo kuwaphuzitsa ma demo achimata amaononga katundu wa anthu ndiye mupepesedi amtambo
Mr Mtambo Thanks for help Malawian to remove APM anatikwana makamaka ndi Chisale wake uja Thanks for giving us good government ever. Better you stop here otherwise you can't manage to remove our almighty Dr Lazarus MacCathy Chakwela. Viva MCP,Viva Malawi MCP Upto 2050 wooooh
Apm my vote
ANTAMBO ACHIHANA MWAYANKHULA BWINO KWAMBIRI GOD BLESS YOU
koma MTAMBO ukatichotsela a Chakwera.IWEYO UKHALADI HERO.CUZ TATOPA NDI CHAKWERA
Ubalira Ase . MCP 2025 Bomaaaaa , DPP is just useless.
Wachita bwino kupepesa malangizo a the DC ❤❤❤❤
Mbuzi yamunthu yomwe inapeleka miyoyo ya anthu kwa mimbulu
Ukapepesa umapeza mtendere thanks 🙏
❤❤❤ kuli wa mcp ko akhoza kuzikozelatu😂😂😂
Chilungamo chiyende ngatu madzi chihana
Aford sidzawinaso muja anayambila ndiliti limenelija ndiye akawine pano 😂😂😂
🎉wachitabwino kupepesa mtambo.❤❤❤❤
Comrade kumeneko nde kukhala zinthu zikavuta kumapepesa akhwana heavy.
Mwa inu nokha simungawine,pangani alliance
Apa Mtambo nde wayankhulano kupepesa ndegwelo logonjalo big up
Eya zimafunika choncho,muthu azimva malangizo kwa ena mwapepesabe,bolaniko.
Onsewa ndi akuba
Big up Brother Ntambo pena umaganiza boo penaso umayitaya Game.
nice speech....
Moto buu Good message ❤
There's hope, afford party is going to rule this country
Nonse ndin mbala
After kuchotsedwa unduna
Yes it's true make alliance kuti muphe chakwela mbava
Sitingataye thawi kuba 'fundo za ntambo Tambo ndiwa boza owukira amakamba zithu akawina kut wavutika korowera Bora komawonera TV osat zakhutu kuve iyi
Iwe ndiwe garu kwabs chifkwa anakuchosa garu zakouja
Good message
Koma mulungu amasadamuzadi zithu. Ndaonera Timothy
Mtambo,wabudula nmemo wagulu
🔥🔥🔥🔥🔥
❤❤❤ number one moto buu
Ndinkafuna ndigale ndichidwe.. koma chifukwa Cha Mtambo... Aaaaaaa.. bsi
Chiphwala cosadulacho GaLu
Or mutabwaza bwanji km chikhulupiliro chikataika zimakhala povuta kut uchibwezeletse
Ayi man peter munthalika anthu anataya naye chikhulupirilo lero bwanji anthu abwezeletsaso chikhulupiro mwa iye
Popanda nfundo, tingonva za akamuzu apa.
Sindi sapota zipani zotsogozedwa ndi banja limodzi.
A Ntambo kutha ma plani kanamizeni ena
Wa hit a bwino kupepesa mtambo ku mtundu wa Malawi unazitenga for granted kuli konse ukupita uwapepesedi a Malawi inawononga Malawi ndi iweyo kuwaphuzitsa ma demo achimata amaononga katundu wa anthu ndiye mupepesedi amtambo
Mwadziwa liti kuti ndinu adolo inu 😂😂😂😂 abusa aja osadzawaphwekesa anasefa zisilu zadyera zonse
Pa mtumbo pako mtambo ndi mzakoyo
Timothy ntambo ndinu opepela munaononga kale ziko la malawi ndipo tikudziwa kt mwatumidwa ndi chakwera musokoneze DPP nkhanga zaona. APM my vote
What ever koma walakhula za dzelu antambo tiyeni nadzo tilimbane nawo mpaka tikafike
@@user-fl7br3dw4h u r right
@@user-fl7br3dw4hThe devil 👿 also knows the bible, do not be blinded
Kusowa zo sapoter
Zikomo kamba kopepesa Mr mtambo,coz eeee tipseleratu PANO tasala thako limodz,Lina ladyeka ndi njala
Kkkkkk
😂😂😂😂😂😂 kma abale
Mtambo ndiwe oseketsa kwabasi, posachedwapa pa zodiak unanenetsa kut sungapepese chifukwa palibe chifukwa chopepesera, ndie lero uzikat ndikukupepesani amalawi zoona????? Koma anthu mukamafuna ma votii, ayi zikomo.
Or pa chikondi mukhale mwasiyana ndee muzbwerelaneso mmmh Love imasiyana amwene than the past nde awawa asatipepeleseso😅😅
Following
Kuzaononga chipani
apa afod basi siyingawineso
Masanje eni eni
More fire Aford
Apology received
We take neither side in receiving
Still we feel pain because of those whom you put in power
Chikapanda kukuthamangisa ku m c p ukanakapepesera kutu ? Tikudziwa kuti ukupepesa chifukwa anakuthamangisa ku m c p
Mwana wathu wathu, osaopa
Amtambo azindikila liti kuti amalakwisa kkkk my malawi
Freedom fighter
Mtsing,anga ndi meneri saona za kutsogoro ayi ,never apo ayi ,only Mulungu amaona za tsogoro
Mwayankhula bwino lelo silut mtambo
Kuyenda ndi chisekwete chimenechi zachiziwikire kuti ma mp olo atatu sazawapezanso kkkkk
Asilikali or a security 🤔 😅
Camera man is not doing his job...
Moto moto
Chitsiru iwe ndi mcp yako ndi lazaro wako wakuba ngat bambo ako omwe
Mavuto alipo ,ndipo ndale nkanyama nkofutadi kkkk
Takambani mfundo apa history ya kamuzu ndi chani nthawi ino ndiyoti muzitiuza mfundo zogwira mtima osati zama history
Mpunga uja wathulidwa Tchenga bansi
Palibe president amakwanisa kuyamkhula chichewa
Ndinu makape kobas
AFORD......😂😂😂😂😂😂😂
U can't even thanks chakwera iwe pakati pano mulindindalama coz of chakwera
Zachibwana zenizeni
I feel ka fungo ka mcp umumu
Ndiye lero ukupepesa ku mtundu wa Malawi lero mesa pa zodiak unka kana kupepesa ku mtundu wa Malawi lero wapepesa bwa?
Khakhakha kkkkk
Mafakitale ake mubuwerse muwatenga kut palibe chachilendo chomwe mungatiuze
Media people??! Voice and capturing is so poor
Aford boma kale wina afune asafune
Chakwera iweyo nkhati ukudziwa kuti udzawina ,2025 usiye kutuma zigawenga zinzako kukhapa anthu pansonkhano anthu tikufuna machitidwe osati uchigawenga wakowo komanso usiyiretu kusaka B K
Wafuntha uyu
Komaso mwachita bwino kupepesa zikomo
Mcp yayamba kale kunjenjemera
iwe...ife tikufuna ADADIE.....APM
Nganganga kumbuyo kwa Adad❤❤❤
Nsilikali amakhumata? Aaaa
Dpp boma Apm boma basi
Chakachamawa ikupita mcp
A Ntambo sopano tinamizeninso tilipano kumvesela
Kodi atinamize kkkkkk
Kkkkkkkkkk
Can't support this nonsense,he's doing this because of his dismissal from Cabinet,he's just greedy & selfish trying to take Malawians for granted.
Koma Enoch,ndiwe waukali pitiriza Chakwera Ndi khakhakha mzake wa katumbu amangonya nkhanu zokhazokha, Koma heee zirrikoooo
Afford is just useless . T. Mtambo is a desperate man ,hz no direction 😂
Mr Mtambo
Thanks for help Malawian to remove APM anatikwana makamaka ndi Chisale wake uja
Thanks for giving us good government ever.
Better you stop here otherwise you can't manage to remove our almighty Dr Lazarus MacCathy Chakwela.
Viva MCP,Viva Malawi
MCP Upto 2050 wooooh
Mtambo nd opepera uyu
This guy has no interest to human being
Koma mulungu amasadamuzadi zithu. Ndaonera Timothy