Continue serving living God ,man of God u have all started turning million of people into God's salvation not engaging your self into this section of Satan.
sogoleli wabwino timaonela zipaso zake so zinazi sizikufunikira kufufuza maboza pano tinatopa nawo tamangoti thandizani poti mulungu amadalusa zanja lopeleka thanks man of God pathandizo lanu
Ndimakhulupirira kuti munthu osankhidwa ndi Mulungu sapanga za ndale, mukadzaona munthu wa Mulungu kuyamba ndale dziwani kuti sanasankhidwe ndi Mulungu koma anazisankha , pepani azibusa kaya ndi ma prophet gwirani ntchito ya Mulungu uzani anthu za uthenga oti anthu akakandire CHIPULUMUTSO vuto mukalowa mboma mumayamba kupha kusiyana ndi malamulo a Mulungu
Kusawakhulupirira ma pastors ndizoona koma kukamasaka chithandizo suyang'ana posakira chifukwa mulera khugwa sumudziwa, amene Ali ndikuthekera ayese bansi kaya ndi Slam kapena pastors tiyeni tiwapange support Chaka chino ziriko. let us wait and see. Thanks gyz
I as BISHOP M.KASINJA i don't even support any GOD minister to start politics and opening his or her part that's out good performing on the presence of GOD.
Abusa udzani mtundu WA Malawi kuti muli ndi ndalama zingati kuti tione ngati muli oyenera kukhala nsogoleri kusiyana ndikuti tikusankheni kuti mupezerepo mwayi wolemera apo biii Mr bushiri ntchito mwayambapo kale igotengani mpando WA u president basi wopanda vote
UTM SADZAYINUNKHA VOTE YA A MALAWI. MCP NAYO SADZAYIWONA VOTE YA A MALAWI. ANTHU AWA ANANAMIZA MTUNDU WA A MALAWI. AKAGWERE UKO ANTHU ABODZA. KUYENDETSA BOMA IS FOR BIG BOYS NOT SMALL BOYS LIKE CHAKWERA NDI CHILIMA COMBINED.
Chakwelà analinso mbusa timaona Ngati akuchosa a Malawi kophula njerwa Za Moyo koma end result kuonjezela kuphula njerwa. Soldier anati angosiyana Maina anthu awa chimodzimodzi
Iwe galu kwabasi azako amulungu ndi awa akuti zuza kalewa, mwina iweyo Bola Poti uli kale koko mwina sizizavuta, awa zikuvuta chifukwa anali mwana wamulungu then ndiku. Choka pamaso pake
Akulu thandizotu la Bushiri musaiwale Kuti ndale zimalowapo . Ndani ankadziwa Kuti Chakwera angasinthe ? Bwanji mmene ankanyozera anthu andale a pastor Mbewe Koma lero ajoina ndale . Tiwasiye anthu obwera mudzina la Mulungu Koma ali afisi yeniyeni
Mwinaditu ukunena zoona bushiri-yutu amaoneka kuti atakhala president I think kusintha kukhoza kukhalapo ngakhale sunganeneletu koma amaoneka ngati kachifundo ku ntundu wa amalawi ali nako ndithu so ndimaona ngati atha kuchitako bwino tikaelekeza chakwelayu coz mbili yake yothandiza anayambana nkale so enawa ngati nkathandiza asanakhale pampando sindikuziwa. Komabe zinakaziwika mmene ali pa u-president kuti munthuyu olo ali kunja kwau-president anali wabwino so to be honest chakwela za ubusa ndi zina lokha but inside ndi njoka ndi zinkhanila zokhazokha coz alibe picture yabwino to me, so kwa ine mmene wapangila chakwela mu usogoleri wake I decide to don't trust pastors but this guy bushiri I can trust him maybe 70% because the guy kuti mumuone bhobho life amaipanga balance saona mbali imozi kungoti basi ndine m'busa bsi bola nkosa zikubwelesa, zoti ukukama yowonda kale u doesn't care, and ngati munthu mukutchulira zina la Mulungu amafooka olo zake zikumuvuta amapeleka bsi kumene kuli kulakwa kodi mmesa chuma zonse nzake, so ndalama mumafuna zimapita kuti? Popeza simuthandizaso anthu osowa kwenkwen yet mumati kupeleka kuposa kulandila nanga azibusa mumapeleka musandiyankhulise mokwiya inu otchedwa azibusa bishop prophetess not all but ndi gulu loipa kwambili in this world.
But with all my trust only I see is bushiri bass inu achakwela olo Ali Busa anavekapo mbili yothandiza ngakhala amasiye just look at bushiri what has done to us ngakhale ena timunena Kut ndiwasataniki Koma ngiwachifundo, wachikondi wachitukuko ,ochilimika komaso pa ground alibe masewela
Ambewe pitilizani kuba mu dzina la yesu musalowelele ku ndale asiyeni agalu awiri amene adanawo
Ambewe zigolalikani musataye yesu time is over ndale zikuchosani uzimu
Continue serving living God ,man of God u have all started turning million of people into God's salvation not engaging your self into this section of Satan.
Beautiful speech minister
sogoleli wabwino timaonela zipaso zake so zinazi sizikufunikira kufufuza maboza pano tinatopa nawo tamangoti thandizani poti mulungu amadalusa zanja lopeleka thanks man of God pathandizo lanu
Nice project man of God ❤❤❤❤❤❤❤
Thanks Major 1 ,Malawi proud of u continue to serve Malawi
I wish bushili atakhala president,he is trying alot,than Government 😂
Good development, Prophet Bushiri, go ahead
Thanks bushiri major one, we need a tared road in chitipa ntharile if possible your honour
Ada amene anayankhula pomwe bushiri amasegulira bridge uja anayankhula zamphavu heavy
Good work my brother
Ndinanena ine kale Kuti mfundo Za Ambewe zinali zosonyezeratu Kuti maloto awo ndi oti adzakhale pa mpando wa u President
Nice job and a wise minister talking powerful speech
Powerful speech 💪
Anthuni mukufunanso chani makamaka, Ambuye Mulungu watiuzira kale Mayeso kuti watchito sankhala ndi mabwana awiri, okha akalalikire okha akayime patsonkhano azikanamiza anthu aaa sizowona, kwa ine Ambuye Mulungu kumwambako imvani kulira kwa ana anu.
Ifeyo timanyadikira kwambiri keep doing that good job!
Muuzeni zoona mbewe sangawine akutaya nthawi
Bruh mukukwaniratu keep it up
Good work bushiri
Ine ndikabvotera bushilitu❤
Aneneri onyenga ofuna kudyela anthu kuteloko satana walowa kwa anthu amene azitcha azibusa ( aneneri )
Ndimakhulupirira kuti munthu osankhidwa ndi Mulungu sapanga za ndale, mukadzaona munthu wa Mulungu kuyamba ndale dziwani kuti sanasankhidwe ndi Mulungu koma anazisankha , pepani azibusa kaya ndi ma prophet gwirani ntchito ya Mulungu uzani anthu za uthenga oti anthu akakandire CHIPULUMUTSO vuto mukalowa mboma mumayamba kupha kusiyana ndi malamulo a Mulungu
Kusawakhulupirira ma pastors ndizoona koma kukamasaka chithandizo suyang'ana posakira chifukwa mulera khugwa sumudziwa, amene Ali ndikuthekera ayese bansi kaya ndi Slam kapena pastors tiyeni tiwapange support Chaka chino ziriko. let us wait and see. Thanks gyz
Ziko mwalilowesa ku manzi sopano chakwera alimnthu wamlungu akukunthani ndi mavuto ndi wina abwereso ndi mawu amlungu msakhulupirire anthu amlungu please. Ndi akumazi awowo please msawamvere. Vito kwambiri Anzanthu akuchichewa please. Segulani maso
Inuyo akumtunda bwanji simunathe kuwamangila anthu bridge?? Akumadziwo amanga
Sitidzakhulupiliranso pastor or m'busa a Chakwela atiphunzitsa a Malawi.
I as BISHOP M.KASINJA i don't even support any GOD minister to start politics and opening his or her part that's out good performing on the presence of GOD.
A!! Zazitumiki amulunguzi zikupeleka chiophyezo m'ziko lathulino.
Abusa udzani mtundu WA Malawi kuti muli ndi ndalama zingati kuti tione ngati muli oyenera kukhala nsogoleri kusiyana ndikuti tikusankheni kuti mupezerepo mwayi wolemera apo biii Mr bushiri ntchito mwayambapo kale igotengani mpando WA u president basi wopanda vote
usongoleli umafunika chocho ukapanga chinthu usanalowe mboma anthu amaziwa kt akalowa mboma atinthandiza kusiya ambewe
apanga chani ku Malawi 😂😂😂😂😂😂😂
Bushiri yes, chifukwa akuthandiza a Malawi ambiri and mulungu apitilire kukudalitsani
UTM SADZAYINUNKHA VOTE YA A MALAWI. MCP NAYO SADZAYIWONA VOTE YA A MALAWI. ANTHU AWA ANANAMIZA MTUNDU WA A MALAWI. AKAGWERE UKO ANTHU ABODZA. KUYENDETSA BOMA IS FOR BIG BOYS NOT SMALL BOYS LIKE CHAKWERA NDI CHILIMA COMBINED.
I don't trust pastors involving in politics
Kkkkk busa again aaaaa talapa kwakwana
Salute HOT 265
Azibusa ndi awa asaakuyendesa bwino bomawa😂😂 ndiye sindingavoterenso m,busa ndaleka😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Chakwelà analinso mbusa timaona Ngati akuchosa a Malawi kophula njerwa Za Moyo koma end result kuonjezela kuphula njerwa. Soldier anati angosiyana Maina anthu awa chimodzimodzi
Ambewe musathawe ntchito ya mulungu mudzunzitsa anthu kumbukilani mtumiki Yona
Zikomo Papa ntchito yomwe mukugwira pitirizani
Asowa zochita prophet wabodza
Kodi president Chikomeni tatiye timuyese inu😂😂😂
Umuuze Chakwera aleke kuba ndiye oipa ophangira
Azibusa imwe ndiye yayi.
Zigawenga inu, bola tivoteŕeko mbakuwaku
Mmmmmmmm ndiboza ndi ndale imeneyo ndipodyela pamenepo inu anati chani ena aja aaaaaa
Bola so timuvotere bushiri, coz iye wakhala akulimbana ndi njala mmalawi osati boma li ayi
Nchito yabwino major,pitiriza anthu avetse
Kodi mwati kaliyatiyo amamufunsa mafunaoyo ndinzungu Kodi anthu onsetu mudzikomuno sionse omwe anapita kusukulu ambiri amamva Chichewa
Good development
Mulungu akudalitsen mejor 1
Iwe galu kwabasi azako amulungu ndi awa akuti zuza kalewa, mwina iweyo Bola Poti uli kale koko mwina sizizavuta, awa zikuvuta chifukwa anali mwana wamulungu then ndiku. Choka pamaso pake
Munthu wa Mulungu ndi ndale mmm satana akuyesanitu inu
Mmmm kmtu aMW mumachina ,pano tikudya zikhawo, kenako tizanya gede
Abusa ose kumalawi ndi dzigawenga don't trust them just eat money for them
Ndiona kuti amalawi tizithanfizana Koma nthandizo lako silimatifalisa
Usatchule dzina la chakwera pamenepa wamva iweso ndigalu zed ulemu upite Kwa bushiri bas
Iwe osathokoza chakwera galu iwe thokozani bushiri
Chidzukulu chananjairo aka, Brian banda wamangidwa amanamizira kuti ndi dotolo
Bushiri ur good man
Bushiri wachani nanu? Muvoteleni mudzitamba masanasana ndi bushili wanuyo
Osadana ndichitukuko mwayamba kunyoza ife tidzidikira sochina
Kusinthasintha ma pulesidenti sizithandiza Malawi, Kodi Malawi yasintha mapulezidenti angati? Chasintha ndi chani? Tiyeni tizimusiya pulezidenti aliyense azimaliza term yake. Chimene mungakane ndichakuti ngati pulezidenteyo akufuna kupitiliza kulamula term yake itatha.
kodi ambewe anakapelesa Kuti mgaiwa yemwe akhutayu.asatinamize😂😂😂
Km malawi aaaa ai ndithu
Good job
Tinataya chikhulupiliro mwa andale
M'busa sazapeza ntajenso muno, zina ndiye zikutivutazi.
Utsogoleli wabusa ndatopanawo
Ngat akulalikiratu abusa ena amenewo akuyamba kunama ngat chakwera
Pamarawi basic zikasinda. Kumwamba komathu andindu awa asibusa panjathu ndi.angaru ...baibro yesaya 56v11 osafothera please Malawi wanga
Malawi timwalira ndi wumphawi chonde tisazavotereso abusa tawonani mumene tikuvutikira ndi abusa amene alipowa
😂😂
Iwe usamatchule dzina lachakwera ,chakwera ndi galu
Ndele iyi munyako naye ananena chicho tiye uko azakuvotela pot malawi ndiopusa mumaganizo
Sindingavoteleso zipani zochokela kumpingo
Tangotengani dzikoli major 1 mukudikiraso chani
Kuthokoza abusa abushili moyo muli nawo othandiza athu omvutika
Aaaah palibe angavotere utm since u have failed to rule this country
Apraise team asanduka ovinila chipani hmmm
Malawi uzapeza liti chikondi kuchokera kwa azisogoleri ako? Kupusisidwa ndiye chakudya cha ife a Malawi
Andale asamakhale azibusa
😅😅😅awa nde ayi
Azimbusa, no no
Bushiri uyo wachita bwino kuthabdiza koma ziwam munthu akafuna kugwiravnyama amayika zomwe nyamayo ukumadwa ndiye imati muthu wabwino uyu wandipasa chakudwa ndikadye ndikukagwidwa iyo kuzaonjola amalawi julan maso munamixidwa mupaka liti? Pano tikuti 60 years tili paufulu koma chazeru palibe ulim ukuvuta fertizer kudula business ayi ntchito kusowa anyhu akufa chifukwa cha kusowa kwa mankhwala bola DPP ivwerere anakhalapo akuziwa ma problems
Mukadzaona munthu yemwe akuzitcha kuti ndi mtumiki wa Mulungu akuyamba ndald muike question Mark,
zikomo bwana
Ndiye chinacho ndichanfani chachiwilicho angochula dzina lachipanicho basi akusogolela ndindani
Ambewe bambo yoh
Mzika weni weni, mwaona bwanji pamenepo ndathokoza kwambiri wakonza chitukuko kwathu zikomo
Chidakwa cha chi polisi
Nice
Utm yake iti yanyuwani or yomweyi yachilima?...
Kaya
Mbewe , president???🙆🙆🙆🙆🤦🤦🤦🐍🐍🐍🐍🐉🐉🐉🐊🐊🐊🦀🦀🦀 Manyaka
😂😂😂
Azibusa mwaona ngati kolemelerela ku Bomaku amzanunso amkatero😢
Basitu walowa ziwanda naye
uyuso uyu bushili zikomo chifukwa chochitisa manyazi boma lolephelali koma bola osapanga izi muliso ndi maloto andale
Abusa ayi😂😂😂😂😂
APM❤
Awa ndiopusadi eeti!!! nkhani ya bridge ikugwilizana ndi a Chakwera,inu ndi achakwera anuwo mukagwere ukoo
Nkhope yanuo muzichotsa tikufuna tiziona ma video mmaikao inuo situkusowani tufuna tione zomwe mufuna tionezo
Usogoleli koma akanakhala bushiri uyu akanatiombola uyu
Akulu thandizotu la Bushiri musaiwale Kuti ndale zimalowapo .
Ndani ankadziwa Kuti Chakwera angasinthe ?
Bwanji mmene ankanyozera anthu andale a pastor Mbewe Koma lero ajoina ndale .
Tiwasiye anthu obwera mudzina la Mulungu Koma ali afisi yeniyeni
Bushiri kumanga bridge 120 million pamene boma lomweli likadati 2 billion kwacha.
Muthu wamulungu inu ziapasani anthu ulaliki osati izi ai
Mwinaditu ukunena zoona bushiri-yutu amaoneka kuti atakhala president I think kusintha kukhoza kukhalapo ngakhale sunganeneletu koma amaoneka ngati kachifundo ku ntundu wa amalawi ali nako ndithu so ndimaona ngati atha kuchitako bwino tikaelekeza chakwelayu coz mbili yake yothandiza anayambana nkale so enawa ngati nkathandiza asanakhale pampando sindikuziwa. Komabe zinakaziwika mmene ali pa u-president kuti munthuyu olo ali kunja kwau-president anali wabwino so to be honest chakwela za ubusa ndi zina lokha but inside ndi njoka ndi zinkhanila zokhazokha coz alibe picture yabwino to me, so kwa ine mmene wapangila chakwela mu usogoleri wake I decide to don't trust pastors but this guy bushiri I can trust him maybe 70% because the guy kuti mumuone bhobho life amaipanga balance saona mbali imozi kungoti basi ndine m'busa bsi bola nkosa zikubwelesa, zoti ukukama yowonda kale u doesn't care, and ngati munthu mukutchulira zina la Mulungu amafooka olo zake zikumuvuta amapeleka bsi kumene kuli kulakwa kodi mmesa chuma zonse nzake, so ndalama mumafuna zimapita kuti? Popeza simuthandizaso anthu osowa kwenkwen yet mumati kupeleka kuposa kulandila nanga azibusa mumapeleka musandiyankhulise mokwiya inu otchedwa azibusa bishop prophetess not all but ndi gulu loipa kwambili in this world.
But with all my trust only I see is bushiri bass inu achakwela olo Ali Busa anavekapo mbili yothandiza ngakhala amasiye just look at bushiri what has done to us ngakhale ena timunena Kut ndiwasataniki Koma ngiwachifundo, wachikondi wachitukuko ,ochilimika komaso pa ground alibe masewela
Kumtunda kwenikweni msimasewera pa ndale Hon Kaliati
Machine
Ndy usachosapo nkhope yakoy bwanj
Ziwoneka kusogolo