And then enawo has been fired twice from a public broadcaster that should have been a lesson learnt from.his current employers... ma bwana ena they smoke too much I wouldn't hire him ndili ine. 😂
Winiyo ndi MCP akukhala kumbali ya akuphawa bwanji,zoona angati ai searching sinaimitsidwe yet a Kumkuyu ananena pa public.iye mkumati fwefweee,sakudziwa kuwawa kwa imfa ndiopu mwina akufuni kenakake kubomaku.
Iwe chawezi nthawi ya campaign ija a China bon kalindo ndi mtambo amayankhula bwanji sanamange za chamba timakudziwa kale ndiwe W mcp ukufuna udindo nawe so koma ukafa ngati galu nawe so kumeneko
Chawezi is a good example of an educated savage mxiiiiw
😂😂😂away ndi a MCP Za ziii
Deus you are lacking something very important in professionalism - sobriety and objectivity. I think you can learn a lot from your colleague Victor.
And then enawo has been fired twice from a public broadcaster that should have been a lesson learnt from.his current employers... ma bwana ena they smoke too much I wouldn't hire him ndili ine. 😂
Zaziii chosecho all ov u you know tje whole story kuti a president anuwo is involved mq'aaaa
Zanziii zoduka mitu izi
Victor now losing track wadyanso banzi uyu ithetseni yayamba kukhala useless 😮
Rather Mibawa ikusokonekera coz of these biased so-called Jonalists .... when u r n analysts u don't have to be biased.....
Victor has point, a Chawezi ndinu a MCP mwaoneka your argument doesn't make sense
Bafwethu, niyakhuluma kakuhle inkosi, a s'funi kulwa tina
Winiyo ndi MCP akukhala kumbali ya akuphawa bwanji,zoona angati ai searching sinaimitsidwe yet a Kumkuyu ananena pa public.iye mkumati fwefweee,sakudziwa kuwawa kwa imfa ndiopu mwina akufuni kenakake kubomaku.
DEUS NDI WA MCP....u have to know that anthu sangayendele ma opinion,anuwa...
good point victor
Iwe chawezi nthawi ya campaign ija a China bon kalindo ndi mtambo amayankhula bwanji sanamange za chamba timakudziwa kale ndiwe W mcp ukufuna udindo nawe so koma ukafa ngati galu nawe so kumeneko
NDIPO...MUMATINYASA ndi programme yimeneyi...
NDIPO...MUMATINYASA ndi programme yimeneyi...
Chawezi uyu akuwona ngati amalawi ndife uputsa, mlonda uja wapatawa uja nawanauze😂
A chawezi anadya Bazi..ndipo MCP siiwina muonaso ,
Cheawezi USA male mayankhulidwe okay wamva?
You talking rubbish
Achokani boma angaliwuza kut munamupha
Ndinu zitsilu
ndipo we.dont miss this babaric programme.CHAWEZI makes me sick.😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢
this programme ndiya manyi...because the people holding this programme ndi a MCP
Inuso zachamba palibe chazeru apa nanga chifukwa chan chakwera akungomanga anthu ufulu olira umenewo speech ya president wanuyo ndechan zachamba
Inu munagulidwa kale paja ku mcp zachabe nanuso imfa yanu izakhala ngati mbuzi
Komano apa malamulo agwira ntchito but nthawi ya mademo malamulo kunalibe a Malawi tiyeni tiziopa Mulungu
its clear...people dont want Chakwera next year..koma muli busy kumupopa.agalu inu
Chakwela wapha chilima or mukwiye chilungamo palibe
Chawezi AMalawi ife usati tenge ngati ndife anthu opusa ayi wava
Kugwiritsa makamulo molakwika kumeneko kuti anthu asamalankhule zakukhosi
APM oooyeeeee
APM zaziiiiiii mwayaluka ndale pamaliro komaso nkhani ili yapa Siya pitala ndiwe gonthi Garu iwe utinyase ndina m'gogonda wakoyo dzamuvotele wenkha Ife ai chimapha malubino chimechija kusenda kopanda chisoni pano asavutike patala ai dziko lathu azipita kwao Ku Mozambique
Uli ndivuto ndiwe galu
Ukunya ndi nkhalamba yokoyo sikwanu Kumalawi Kuno mutengane muzipita komwe mudachoka anyani inu
@@JackMvura-ik2td you are very stupid bro i know you are a mcp fans munya anthu akupha inu ukupita ndi chakwera wakoyo
Adawa alibe tselu ndithu akuyamikira achakwera
A MCP awa who doesn't know
Aaa cokani timaona ngati mudzilamba za nzeru ndinu amcp
Chawezi pathako pako😢
Alumisidwa chibanzi awa
Chakwera ndi wakupha.
Chokani apa agalu inu😊
Kd akuti chani awa
Za ziiii