Bravo gentlemen... you have hit the nail on the head... It is the system indeed...we can change the Political Leadership as much as we can, but as you have said it's a rotten chain in the civil service. Guess what...it is our Aunties, Uncles, brothers, sisters, fathers and mothers...when they bring home the stolen money we just enjoy and forget. It pains only when you are not benefitting.
Chitsanzo mchomwechi tikuwona a DPP wa. Anachoka kalekale mboma koma adakayendelabe galimoto zopuma, ndiyetsa Brian Banda ananenanso a DPP akukachititsa convention yawo ku Blantyre. Anthu awa siabwino ndiiithu ndikukuuzani.
Mhiiiii abale you mean it's MCP's fault again? Congress has only stayed 4 years I think it's not their fault. Inu anyamata Inu mumakondera a DPP Inu. Anatani kukoza a DPP akhala m boma kwa Zaka 30 bwanji sanakoze the whole M1 road iñali yonyasa. Angoyamba mukoza Jimenez. Nëna i chilungamo inu ndimu anthu opemphera enanu.

Nseu wa Chiweta to Karonga ma potholes aja boma limayenera kuchita manyazi. It has been more than one year mayenje amene aja. Very shameful
Not one year it has been years
My favorite program
Nsewu wa Salima kupita ku nkhotakota 🙌🙌🙌
As. Malawian living aboan sooo angry!!
Tsiku lina tadzambani za expenditure control. Kotulkira ndalama ndikifunika kutseka, zogula zina ndizosafunika. Malipiro makamaka ma benefits Ali exaggerated. Ndi zina zinayenerr kuchotsedwa pochita control expenditure.
Cant see why where the road is good thats where they have started. This Malawi no balance.
Nthawi yakale timakutengerani panopa mwanama Brian Banda akusokololetsani kwabwino muzipanga zanu onyamata
😂😂😂😂😂 point boys
DPP yachoka dzana dzanali osanama lankhulani chilungamo ndinu anthu opemphera enanu.

Zaka 30?