ANTHU ADABWA NDI ZOMWE ZIKUKAMBIDWA MWA REPORT LA NDENGE

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 13 ธ.ค. 2024

ความคิดเห็น • 81

  • @PeterMwakihana
    @PeterMwakihana ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    God have mercy with my country 😭😭😭😭😭😭. You are just wasting our bundles here. God is watching one day tizaziwa chilungamo

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    U will pay heavy price not today but u will pay heavy price mark my word

  • @SynodAudit
    @SynodAudit 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    ndenge yimayenda mwa zigzag (GPS data) Chifukwa chani???? Reconciliation ya mafuta bwanji???? Black box yili kuti????

  • @AgnessBanda-pw2ru
    @AgnessBanda-pw2ru ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    😊Koma athu awa akuseweretsa imfa ya mwana wa mzawo bwanji

  • @LimisonSymon
    @LimisonSymon 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Zaukape panyapanu nose ndi report lomwelo ife athu aku Malawi tikumudzia emwe anagwesa ndege ndi lazalas chakwela chimwendo banda ndi yudas maiko usi

  • @PatrickZinenanie
    @PatrickZinenanie 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Muzaulula zoona zenizeni chikangawa akazapha azibale anu

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Kkkkk muli thawi yoononga ndalama yamisokho, palibe chomveka apa chakwera anapha chilima zilipoela palibe chomwe mungauze mtundu wa malawi apapa masowa zochita yeti? Ngati munakana kupanga public repot apa muzinamiza ndani kkkkk amfiti inu

  • @AubreyWiskes
    @AubreyWiskes 31 นาทีที่ผ่านมา

    Mwadya idya ndalama kukhalira chilungamo mmmmm mulungu ndamene ali ndichilungamo chonse nonse anthu oipa inu ana anjoka

  • @PatrickZinenanie
    @PatrickZinenanie 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Inu a inquiry mudikire September 2025 kuti muzamangidwe bwino ndi zi ma bribes zomwe munadyazo kwa chikangawa pa ujeni panu

  • @iangondwe6857
    @iangondwe6857 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Kodi aku Germany report la fake awaso report la fake ndiye lachilungamo tilipeza kuti

  • @JoshuaJuwawo
    @JoshuaJuwawo ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Mesa a president anatiuza kuti inafika ku mzuzu

  • @EnockMvula
    @EnockMvula 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    koma chakwera uri ndizambi ambuye akukanthe ndiguru rakoro nose murungu akuwonani ndizimajeketi zanuzo ndinu agaru kwambiri

  • @KimBaluwa
    @KimBaluwa 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Palibe chomwe amafufuza awa anangokhala nkumakambilana kuti tinganame chani nkumalemba pa paper basi

  • @KelvinBandah-o5v
    @KelvinBandah-o5v ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Bodza lenileni onse aboza ndizisilu

  • @LenoMvulaMvula
    @LenoMvulaMvula ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kuno ku malawi mulungu akulange inu nonse mnatengepo mbari pa ifa ya chilima makamaka iwe chakwera nd chimwendo inu mzafe ifa yowawa anthu oipa

  • @AubreyWiskes
    @AubreyWiskes 29 นาทีที่ผ่านมา

    Kusewelesa infa amzanu mulungu akuoneni mwapadela

  • @innocentkapachika6591
    @innocentkapachika6591 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Shocking, the presenter is visibly stamering and even fail to put the grammar correctly like this investigators instead of investigator or rather these investigators. Vuto lolena bodza limapatsa busy😂

  • @RaphaelWinford-t7u
    @RaphaelWinford-t7u 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mbuzi za atsogoreli 😢😢😢😢😢 one day is one day 😢😢😢😢ayudasi.....fiti za ku Malawi

  • @MarkMphadzo
    @MarkMphadzo ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mukuyankhula ndi zibwibwi bwanji?????? Anthu oipa inu Mulungu akukuonani

  • @starorkunje
    @starorkunje 33 นาทีที่ผ่านมา

    owelengayo olo manyazi.Mulungu awalange

  • @EnockMvula
    @EnockMvula 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    koma mziwe kuti murungu simunthu zowona kuyima pamaso pamurungu kuwerenga nkhani ngati yimeneyo zowona abusa muri ndikorara pankhosi ambuye akuyendereni ndipo mizimu yaanthu awa nine yikukatheni usiku uno nose

  • @EviChio
    @EviChio 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kupemphela kwanu ndikopanda ntchito, ndipo mulungu akadali nanu mlandu. Ndipo mtendele simudzakhala nawo mpaka kale

  • @StaffordNgalande
    @StaffordNgalande 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndalama zakusekani pakamwa choona chake mukuchiziwa mwabisa ma jekete mwa ngovala km muli nbi Ana inu Mulungu akukathani nose mukubisa chilungamo ndithuu

  • @StevenMasamba-y1p
    @StevenMasamba-y1p ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Inuyo mukuzinena kt ndinu azibusa muzakhala mboni pasogolo musaone ngati nkhani imeneyo others pomwepa.kodi amalawi sitingasonkhanise ndalama dziko lonse lamalawi ndikupanga kafukufuku wathu?

  • @MarthaBango-s3y
    @MarthaBango-s3y 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Anyirenda anazileka kani

    • @bryan4jc356
      @bryan4jc356 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      T nyirenda Anapanga za nzeru kutuluka mu commission ya chinyengo iy

  • @PetrusTlhokwane
    @PetrusTlhokwane 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Agalu inu nose pamodzi ndi Chakwela wanuyo ndipo tikuuzani zeni zeni Chaka cha mawa Chakwela adzaziona kutiphela anthu ngati chochi ndipo inu nose Mulungu akulangani mumanyumba mwanumo.

  • @evansjohn7766
    @evansjohn7766 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kkkkkkk.. .....azibusa a nthawiyi ambili ndi ayudase .ngati chinyengo chili mwazibusa ziko silingakale bwino ndipo a christu alimavuto yazaoneni coz owatsogolela alindi sambi.

  • @OliverChimsewu
    @OliverChimsewu 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    The question arise why you didn't include the family

  • @Enock-gu5ff
    @Enock-gu5ff 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Akamaka_agwa acakwera inuso azibusa mwathera pompo ndipo mwazipaka zitosi zoti zakuvutani kuzipukuta

  • @IsraelMajamanda
    @IsraelMajamanda 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Dziko la Malawi linkhalabe pa mavuto chifukwa chaifa cha wanthu amenewo inuso mukudikila komweko

  • @StevenJana-m2e
    @StevenJana-m2e ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zopanda ndi mutu izi,mwangowonongaso ndalama zanthu apa,Bro Namiwa amaziwa kuti nyasi za report zizakhala chonchi

    • @JulioChiwalo-t4f
      @JulioChiwalo-t4f ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Mulungu yekha ndiye amene akuziwa zomwe zinachitika zokhuza ngozi ya ndege

  • @SteynMaduka
    @SteynMaduka ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Tinkfuna report la ndege ndife Eni a Malawi bwanji osafotikoza mu chichewa? That means chiseko chakupanani

  • @HarrentBanda-f7o
    @HarrentBanda-f7o 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Zamanyi basi nonse zisiru nanu muzafa siku likuza

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mboni yayikulu ndi Mulungu zikomo

  • @RaphaelWinford-t7u
    @RaphaelWinford-t7u 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chilungamo mukuchidziwa koma ndalama zakubisani......

  • @EllenKanada
    @EllenKanada 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Vote ndi mu ntima

  • @GeofreyBandah
    @GeofreyBandah ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ukupeleka report we pamtumbo pa amai wako chitsiru

  • @RemitterFlik1130
    @RemitterFlik1130 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Buku lopatulika limanena kuti palibe chobisika pasi pa thambo lakumwamba watsoka yemwe apelekela umboni Onama ndipo mulungu sazamuchitila chifundo pamalamulo khumi amulungu akuti usachitile kapena kukhala mboni yonama anthu Inu ngati mukufuna kusangalasa muthu wadziko lapasi dziwani kuti mukudana ndi mulungu wakumwamba

  • @AndrewMdala
    @AndrewMdala ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Nthawi ikubwela boma likasitha osadanda amalawi awa ndi agalu panyapanu nonsense

  • @memorygondwe1635
    @memorygondwe1635 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mulungu akakuwotchani ndinthu agalu inu

  • @PetroHerman-z5g
    @PetroHerman-z5g 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Palibe chinsi pa dziko lapansi olo patapita zaka zochuluka maka choonadi chidzatulukila poyera

  • @JACKSONHULUWA-j2n
    @JACKSONHULUWA-j2n 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Black box munaipeza agaru inu?

  • @RemitterFlik1130
    @RemitterFlik1130 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mupelekeso uthengawo muchichewa kuti akumudziso amvenawo bodzalo

  • @SamukLungu
    @SamukLungu 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Pamatako pinu

  • @HolmanDazah
    @HolmanDazah ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Being a boghop and whatever the position you are in , the thing is Nonse ndinunokupha. Am saying this , from the bases of your course, malawians were waiting to hearing from your asking the blach where is about, and Richrad Chikalundi, why he failed to have his own seat in the plane yet he was accompanied,. But in your report there's not , all these evidences that Malawians have in their mind. You know when we say, stop , if you know that all the above evidences are not there stop it. Lets Malawians have what we had since 1972 when Tembo and Kamuzu stragise to lead malawins ndi chipani chimodzi. History is the best teacher.

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Palibe ca mzeru angatiuze mbuzi zimenezi lets watch & c.

  • @captainb6506
    @captainb6506 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mutiyesa ife zitsiru zanu eeee,

  • @EneyaManda-r1p
    @EneyaManda-r1p ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Cry my beloved Country, who is fooling Who

  • @WilliamNhlane-fd9hi
    @WilliamNhlane-fd9hi 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zikusalirani tikuziwa kuti chakwera akupasani chibanzi zazii tikusakani ife angoni

  • @PatrickZinenanie
    @PatrickZinenanie 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mwakhuta khutha zinyemba zanuzo agalu inu

  • @AWARIBLACK
    @AWARIBLACK 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    225 tikumana tiziwa zoona tigoti phee

  • @OliverChimsewu
    @OliverChimsewu 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zabodza zimene mukunenazo ,matembelero ali pamutu panu

  • @OggieChinchen
    @OggieChinchen ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Panyapanu nose mukususa report bwelesani lanu pamtumbo panu

    • @starorkunje
      @starorkunje 22 นาทีที่ผ่านมา

      olo mutukwane komabe munawapha anthu aja ngat Mulungu amayakha akuyakhe zosezo

    • @RachealHarawa-xc9gs
      @RachealHarawa-xc9gs 18 นาทีที่ผ่านมา

      Galu okupha iwe

  • @johnjoachim3820
    @johnjoachim3820 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Tangopitani mutiuze fast kuti mwapezako chani zinazo zopanda palibe

  • @DavieChiwale
    @DavieChiwale 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Onsewo ndi afiti okhaookha

  • @mussahprecious9633
    @mussahprecious9633 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Tiona ngat tinva zazeru😮

  • @GraceChenda-q2g
    @GraceChenda-q2g 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Akanakhalapo mmodzi kuti anali mbale wanu mukanatelonso

  • @AbdulJohn-t7l
    @AbdulJohn-t7l 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Pathako panu nonse zisilu palibe chazelu

  • @PatrickZinenanie
    @PatrickZinenanie 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zimagalasi mmaso ngati chojambula

  • @YoungMwacho
    @YoungMwacho 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    A story of events or a report?

  • @LottiAffati
    @LottiAffati ชั่วโมงที่ผ่านมา

    osamayankhula chichewa bwanji agalu inu, koma abale amalawi mmmmmmmm

  • @PatrickZinenanie
    @PatrickZinenanie 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ma report a fake anuwo kagwereni nawo uko munapha chilima ziko lonse likuziwa shatapu zanu

  • @TenganiObety
    @TenganiObety 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chokani agalu opanda nanyanzi kuipa ntima kuposa manyi

  • @Spaw-BTheGogoBoy
    @Spaw-BTheGogoBoy 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zapathako zenizen

  • @BIZIWECK
    @BIZIWECK 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kuwapusisa Malawi

  • @Mosa-b6g
    @Mosa-b6g 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zapantumbo agalu inu zaziiiiii

  • @hassammaulana4529
    @hassammaulana4529 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kodi mukuti chani coz mukudipwanisa mutu pa zithu zomwe zikuoneka zikha inu nonse mlungu akuyedeleni ndipo muzakawayakha pa zonse mwabisa

  • @PatrickZinenanie
    @PatrickZinenanie 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mukungoputiliza kuononga ndalama za boma afiti anyapapi akasongo ziwalo zanu zobisikazo

  • @StevenMasamba-y1p
    @StevenMasamba-y1p ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Azibusa ndalama zimene mwapasidwazo mulungu azidalise zikugwirireni ntchito

  • @RaheemNgoma-pk1ev
    @RaheemNgoma-pk1ev 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zadziiii dzen dzen

  • @AlihIbrahim-s7v
    @AlihIbrahim-s7v 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zaziiiiii

  • @memorygondwe1635
    @memorygondwe1635 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mulungu akakuwotchani ndinthu agalu inu

  • @MarryMartin-z6u
    @MarryMartin-z6u ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Zaziiiii