😅😅😅😅😅😅koma aise kunte iweyo umatha... But i have to give respect to all of you coz you always be serious And tikaona inuyo timaziwiratu apa mmimba mupweteka mkuseka😆😆😆
Mkazi wokanda zida-sizimamukhuza za umwini wa company.Azimayi anamizidwa mwamuna kuvala suit yaweni koma kuzathera muchikondwelero banja.Mkaziyu sankakonda mwamuna mmene Ali but materialistic lady
Kunte band! 😂😂 Seriously this guy deserves a spot in the film and entertainment industry.. Sakakamiza he's natural!
Amayi zisakukhudzeni mwamva Kunte machine baba fire mabomba🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Umakwanitsa Master yomaliza🎉🎉, you never disappoint keep it up😅
😆😆😂🤣🤣 kunte ndidolo ...munalakwisa kumutengera Teleza yo ku office 🔥🔥
Blunder yowopsa
Ati sanasiyee kunamaa😂😂😂.. aaah ati anthuu ongoyera alibee kalikonse🤣
Kunte ulibhooo... ipase moto kwambiri... potential ilibho
Great talent a Malawi. We love you. 🇿🇲
Man mumandisuntha kwambili keep it up
😅😅😅😅😅😅koma aise kunte iweyo umatha...
But i have to give respect to all of you coz you always be serious
And tikaona inuyo timaziwiratu apa mmimba mupweteka mkuseka😆😆😆
Love it
Alipodi anthu ambiri amatchubu motere Koma alibe chilichonse 🤣🙌
Awesome comedian 💪🇲🇼🇲🇼 😂😂😂
Kunte sazatheka.... 😂😂😊😊He is the best💥💥🔥
Kkkkkkkkkkkk
Kunte wazionatuuuu!!!!😂😂😂😂😂😂
Iwe ndi Galu kwambiri 🤣
Kunte ndiwe dolo adah ..heavy
Mkaziyu wndisangalasa Kwbiri she akusekelela bwino kwambiri
Kunte ati unangoyera ulibe kalikonse hahhaaha amakunena abwana
Mkaziyu musamutaye bwanawe atipindulila heavy
John Chriss❤❤❤
Koma kunte iweyo ndi one😂🤣🤣🤣🤣
😂😂😂😂😂😂😂
Ase Kunte, koma iweyo siopengadi???
Asaaaaa
Congratulations
Ati ngt muli nayo ndagaileni😂😂😂😂
Keep it up Dyna.
your always best
Kunte sininazindikire mwachangu kuti ulikonso ndi nthabwalai
Zama ex😮😮
Nice
koma kunte 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Kunte ngati ukufuna anthu oti akuthandize kumenya abwanawo tilipo ife. Ndi munthu oyipa kwambiri
Kkkkkkkkkkkkkkk ndili ndi business
❤
🤣🤣🤣🤣🤣🙌Koma kuntee
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 koma ndaseka kulandidwa nkazi mukuona
Kkkkkkkk Kunte my favourite comedian kkkkkkk matama azakupha
Kunte umasowa koma! Kodi sungamatulutse ma video each n every week?
Komatu kunte umandiwaza 😂😂😂😂
Smart Boss 😂😂
kodi mkuluyu amakonda kuvala ma watch awiri bwanji? kkk
Madoba doba asapusa nawo akuberani zambiri 😂😂
Amugwila 😂😂😂🤣🤣
Sapato iyi imandisekesa bwanji
Kute ufzinamizilanji matama ngati ajokisibwanji osadzivomeleza eeee zikupatsa mavuto
😂😂🤣🤣 adha inu ndi 1
Kunte is Underated
Ndipo kwambiri!!
Amayi zisa
Kunte always funny 😂😂😂😂😂
wadzaso bigy
Kkkkk km ndizovuta
company ya nkute😂😂
Aaah kuntee
Ndiye umathawa chani
Kunte kunte😂😂😂😂😂😂❤
iwe umandidalitsa kunte
😂😂😂🙌🙌🙌 Kunte adha
Kkk
😂😂😂😂😂😂😂
Koma tanyozeka ati, 'anthu ongoyela alibe kalikose'
Kodi kukangaza ndichiyankhulo chanji
Umakwana
Kkkkkkkkkk kunte kunteeee
Kkkkkkkk😂😂😂😂
🤣🤣🤣🤣🤣umatha
Kkkkkkk koma mwati maofesi koma gunte
Kuthamangila Pena pake 😂
Ati anangoyela koma alibe kalikonse
Kunte Band Ex😂😂😂
Mbambande
🤣🤣🤣🤣🤣 uphaw sizinthu
Kkkk
😂🤣😂🤣
Koma kunte anakonza
Hiiiiii kunte 😂😂
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
A Theresa 😂😂
Kunte where is this ankolo juice
Amulanda kkkkkkk
Kunje sadzatheka.
Kunte 😂😂😂😂😂😂😂😂😂mpaka fifty kkkkk
😅😅😅😅
😂😂😂😂
Kunte is slept on here in Malawi 😂
Kkķkķ proprietor
😂😂😂😂😂
Sorry mwene Teleza wapita
Kkkkkkk koma kunte man kkk
Kunte umakwana ase🔥
Umakwana gunte
Kkkkkkkkk
Kunte umaziyamba aaa😂😂😂
🤣🤣🤣🤣
Or muli inuyo mukanatan😂
Kkkkkkkkkk kkkkkkkkkk aaaaaaaaaaa kunte
Mkazi wokanda zida-sizimamukhuza za umwini wa company.Azimayi anamizidwa mwamuna kuvala suit yaweni koma kuzathera muchikondwelero banja.Mkaziyu sankakonda mwamuna mmene Ali but materialistic lady
🤣🤣🤣🤣 agama mumatha 🤣🤣🤣
Kkkk nafwa
Kunte suzatheka 😂😂🤣
Kunte umakwana😂😂😂
Yalakwa bwana Kunte
Kkkkkkk koma Kunte kungoyera alibe chirichonse