I dont understand upto now. Which one should come first? Arrest or Investigation. If arrest comes first then there is no freedom in Malawi. Do we need mubusa John Chilembwe to come and intervene this
Bishop Mr Nsussa you are not Wrong ,you're true Bishop Malawian they need to know what happened with jet for Mr chirima and others, there no eny report about accident. More people dead but no eny report about this accident why
Smart matic doing well in mozambique.... Amalawi ndife mbudzi za anthu ndipo anabellle tembo ndichigawenga cha mcp.... I would wish a opposition must challenge the zikwanje party kuti apange conduct comision of inquiry ya chikangawa ndipo bishop nsusa should lead the process....muwona wina azimangilira.... The report must be challenged in court
A Bishop vuto ndiloti mwataya ndalama zomwe chilima anali kupereka ku mupingo. Kamangila wanna kale kuti he was not clean also was stealing from poor Malawiian
Msusa is the true son of God , than u behind the useless Leadership, and MCP, ifa yonse ili ndi malonje, tikuiziwa ur tricks, khalani ndi nkhaza zanu, zizauululika, same size Thambani toad
Ambiri tamasukadi tsopano chifukwa chakubwela kwanu a bishop mkulankhulapo.Ulemu wanu man of God ndipo ife tikuti report la ndege lija ndila fake,anthuwa anapha Chilima ndipo mulungu anajambula zonse munanena kale a bishop.
Zitsilu za atsogoreli amipingo ya satanic akaporo adyela ndalama...... A Bishop m'susa sanalakwitse chilichose anena ku mbali yawo, vuto ndichiyani akapolo inu tazineneli tonyenga...
Kodi mesa Chilima anali wa Catholic a Msusa amayankhula ngati okhuzidwa ndi ofeledwa cz anali mwana wao mchipembezo
Thank u bishop
Thanks Bishop you're welcome,.we stand by you don't ever afraid of this Ame
You have spoken the truth the bishop God bless you
Anthu Aku moshko tinayamba kalekale kuwathandiza Koma Iwo amatizunza tikamadutsa kwawo...God bless Malawi
I dont understand upto now. Which one should come first? Arrest or Investigation. If arrest comes first then there is no freedom in Malawi. Do we need mubusa John Chilembwe to come and intervene this
Good speech sister 🙏🙏
Amen.....Bishop msusa....osaopa...kodi musowa amakupasani...mantha A mcp inu eti ndawona......sulemani osaopa..💪
God bless you Bishop msusa
Bishop inudi ndinu munthu wa mulungu ónena cilungamo mulungu akudaliseni kochuluka. anthu anafa imfa yowawa kofunika osasekelela pamene ena akuzipasa kt ndi iwo angathe kachosa moyo was ena. Tsoka
Amen Bishop i love that you have done God bless you 🙏🙏
Nanu sisiteri yo watani mesa akulangiza anawo
Ndale zakumalawi zikuzuzisa athu osawuka 😭😭
Bishop Mr Nsussa you are not Wrong ,you're true Bishop Malawian they need to know what happened with jet for Mr chirima and others, there no eny report about accident. More people dead but no eny report about this accident why
Smart matic doing well in mozambique....
Amalawi ndife mbudzi za anthu ndipo anabellle tembo ndichigawenga cha mcp....
I would wish a opposition must challenge the zikwanje party kuti apange conduct comision of inquiry ya chikangawa ndipo bishop nsusa should lead the process....muwona wina azimangilira....
The report must be challenged in court
Please musanyoze archbishop Wa mutembeleredwa awa ndi atumiki Eni eni
These r not religious leaders. A true religious leader will not hide his face
MCP inapereka ndalama ku wankulu wa msfr kuti adandaule zopusazo.
Ayi nkhani yi ndiyisavuta inquiry yikuyenera kuyankha izi black box yilikuti , chifukwa chani anamba mochedwa kafukufuku , chifukwa chani anakayambila kufufuza ku lyply komwe kulikutali ndikunthungwa ndichifukwa chani investigation siyinambile ku Macra , and etc
Crap hands our bishop Thomas Luku nsusa 🥳🥳🥳🥳🥳🥳🥳🔥🔥
Zikomo asisiteri for this beautiful teaching
A Msusa osabwelera mmbuyo mpaka chilungamo chizaoneke basi,tili pambuyo panu ife opanda mau ife
Iwe ase usamachuluse zoyakhula uzingosizisiya tizivela tokha umakhalangati ukutipangila zochita
Mcp like kupha athu Osaopa A Bishop
Am not understand nkhani mchichewa report in English 😊😊😊😅 yachabe
Mulungu dalitsani malawi dziko lokongora lachonde ndiufulu and zamasister izi ndizakale amapita adatero osamatapa pakamwa anthu
Mukungonjenjemera ndi DPP mukhaula naotu mutuluka nao nthukuta simunati 2025 sinafike
Chakwela ndi wa kupha pangachedwe bwanji chilungamo chizaziwikabe ngakhale mubise bwanji chinsisi chizawululikabe
Big up bishop msusa Ambuye akutetezeni psalm 34 v7
Mwayakhulq mwaukulu kwambiri ndizimene timafuna amalawi kuti kukhale athu oganizabwino ngati inu abishop mususa ulemu wanu 🎉🎉🎉
Bishop msusa ali pachilungo osati awa adyera adawasankha ndani kut angkhl asogoleri azipembezo???
Abusa okhuzidwa nde chani apap inu mwadya ndalam bas abusawo sanalakwe kuyankhulapo zachilima kd mukuona ngt zikutisangalasae za imfa ija??? Anthu atopatu
Kmaso BISHOP. Uyu amandinyasa hvy
Muziyankhula za njala zimenezo ayi aaaa walakwa chani bishop
Dzikoli liribe mtendere amene Mulindi mtendere ndinu mukuyenda ndi boma.Ndipo azibusa ine ndikudabwa mukuikila umboni wabodza bwanji muli azitumiki Kodi bible pa exodus 23 umati chani siyani chinyengo tsatani choonadi
Chitukuko ndichomwecho 😂😂
MCP iku ikupanga zo nyasa zambiri bwanji sitinanvepo kuti akumanga anthu amenewa,komanso ndani wamangidwa pa kufa Kwa Achilima kuli ziii mpaka lero.
A Bishop vuto ndiloti mwataya ndalama zomwe chilima anali kupereka ku mupingo. Kamangila wanna kale kuti he was not clean also was stealing from poor Malawiian
Munamupeza nzanuyo paekha before anounce public ndinudi azibusa kapena anyamata akwa nsundwe?
Kutengela slung ya chakwera udziwiletu ukutengela ngakhale umbava ndi umbanda wa chakwera ndi kolala loyeralo ngati nkhwangwala
Nkhumba zonse zomwe akunena azibusa ogulidwa akuyankhula ufiti. Ndipo ayalukadi sanati ukumkuyamba.
Mmmmmm kuiona ndunayo 😮😮😮😮
Bishop Msusa tili pambuyo panu ndpo muli ndi support yochuluka osafooka osaoopa mpk tioloka Jordan liver
Amen
Ndip sanalakwitse bishop Ines ndili pa mbuyo pao amen akudan nd bishop shem on you chakwera fake president useless president
Msusa is the true son of God , than u behind the useless Leadership, and MCP, ifa yonse ili ndi malonje, tikuiziwa ur tricks, khalani ndi nkhaza zanu, zizauululika, same size Thambani toad
Malawi akudya chitedze koma Mozambique mamm😂
Munthu wangoyankhula
Kummanga
Azikwanje aja osawamangayidziko lokondela ili😮😮
Zomwe amayakhula Susa zaoneka Kuti zoonadi chikwa anthu aonekera Mbali imene anthu Kuti 100%imbali yaSUSA
A sisisteri ayankhula bwino
Zooonadi sister, ife amawivi sitiwafuna or pang'ono
Ambiri tamasukadi tsopano chifukwa chakubwela kwanu a bishop mkulankhulapo.Ulemu wanu man of God ndipo ife tikuti report la ndege lija ndila fake,anthuwa anapha Chilima ndipo mulungu anajambula zonse munanena kale a bishop.
Uchitsiru aja azikwanjewa osawamanga bwanji ana anjoka Inu munyatu muchila koma mochedwa chauta akukathani ndithu
Mtendere komanso ufulu udatha kuno kwathu tivomeleze osaopa amusowa ambuye mulungu wathu ndiwamoyo ndithu.
Enewo ndimatha
asisitela,oyenela,,kumuchinda,kumatako,kwakoko
Zitsilu za atsogoreli amipingo ya satanic akaporo adyela ndalama...... A Bishop m'susa sanalakwitse chilichose anena ku mbali yawo, vuto ndichiyani akapolo inu tazineneli tonyenga...
Agalu amenewa atani kumanga azikwanje anja
Kusoweka umunthu kwa atsongoleri bwanji osamanga kae azikwanje kudana ndimau okha ochita ai pakuti ndi amcp
Muthu wamulungu walakhula chilungamo koma mukudana nae koma akanalakhula zokonda chakwela nde kuombela Manja Inu zisilu et ana anjoka
Bishopu.uyu.ndichitsilu
Ufulu unali wangongole tinabweza kwa ayini wake tokha 😂😂😂
Ndiwakupha osamabisa ndipo osaopa ndipo sitisiila pomwepa abishop osasiyila pomwepo pitilizani
Anthu munapha chilima ndiye muzitiudza kuti ndinuyo anthu atendele aaaa kukadakhala kuti simukupha anthu tikanati ndinudi anthu okonda ntendele
A police musakhale ndimbali please.
Sisitele,mwalakhula bwino❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Kungot MCP yikutenga dzikoli ngt lawo
Kamajekete iwe kape ndi chakwera wakoyo ukuba zed
Aphedwe basi
Kodi anduna avala chiyani ku mutu
Nde Muthu walakwisa pat ifeo sitikudziwa kumene
Msusa sadalakwise wayankhula chilungamo ndithu
Osatopa ma Bishop
N'fundo zauchitsilu
Zikhare viswuri vako na boma rako
Koma abuse ndinu mathura wa mulungu .
Musabwelese mpungwe mpungwe
😂😂😂😂 ameneyo new year adyera komwekoo Ku ndendeeee
Umalakhulisa kwambiri zimai iwe umafuna tizivela iweyo kapena zochitikazo uchepese
Mbava ndiwe yemwe zikhale
Kkkkk kuli tchito 2025 wina azamwamadzi ometela
Kd ku assemblies ndi ma slung bc
Chazikhare kulankhura ngati chikurila 😂😂😂😂😂
Okay Okay Okay
Asisitele mwayankhula momveka bwino
A zikhale mudagona chilima alikuchikangawa inu ndi agalu kwabas
Zikhare ng.oma mariseche ako
Ambuye atidslinse
Zikhale you're a big problem
Chigawenga zikhale iwe
God be with you Mr msusa🙏🙏🙏🙏
Ganyu akuyalusani
😅😅
Sister....wayàkhulatu😂
Zoonadi
What kind of peace are you talking about nonsense
Chi bishop chakuba ichiii sitingakukhulupilire
Mukufuna kuteteza anthu nthwaw ya zinsangalalo yokha okay chabwino