ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Ine koma artist uyu amandiwaza afana ceez like my comment please ❤much love for this side
Dolo
Iwe ngat uli friend wa Ceez like this i will be back
Kkkkkkkkkk
Chi nyimbo ichi chingakome kuma demo 🔥🔥🔥
Koma Ndiye Zinthu Zingasweke
😁 😁 😁 😁 Mwaiponya kwakuya
Mukanapanga paint green chomwe chili pansi pa galimotocho ndi zingwezo you can edit kuti izioneka ngt ili mmalele popanda chogwirizira ❤
Yomweyo iweee💃💃💥💥Nanga bwanji ukunditchula tchula,andikawe sichoncho😂😂
😁 😁 😁
Nyimbo yabho heavy koma chingwe chonyamura galimoto nextime chisazaoneke ,, big up afana🔥🔥🔥🔥
Umakwanira iweyo
Chili Chonse Nice.. Dope video #RIP Spyral Mwenya
Ma kingpin let's gather here🔥🔥🔥💯undipake sichoncho🔥
Video ili hard koma Kadango watinimaza apa.... Iweo Thank God Omori (T.O.G)
Ife tachokera kwa lawyer
Clean visuals 🎉😊ife2 nde tachokera kwa Hilco nde tikhale pati😅
Afana ceez mi favorite 💎💎
Iwe ndi Dolo ase wapha ikufunika kumochale🔥🔥🔥✅✅✔️✔️💯
❤ wow uli pakala pakala tusaphatikizane 😅🎉. Nyc tune star @afana ceez🔥🔥🔥🥰
Eheee 🥳🥳🔥🔥
Mmene anthu amaipopa videoyi mmayesa akukokomeza ....ndazionera dekha...samanama ndithu💯🔥
Woow great love it 🥰🥰🥰
Zokutchulatchulazo umufuse Ching'axy olo nyimboyi ndayidziwa chifukwa cha iyeyo...........Ilifaya adha🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Zabwino zimenezi 🎉🎉🎉🎉 international level 🌈💯
Keong Kadango 🔥🔥🔥🔥
Real music...osamangokhalira ati nkazi wachithako aaah
Much respect ma guys.. Keong Kadango receive your flowers 🌺
hit 🎯💯💯💯 kwanila inuyo 🔥🔥💯
Olo nzakalambe izi mu ride yanga sizizatsika Pakalapakala Tisa-phatikizane ✅✅✅✅✅✅✅✅✅✅✅✅ Certified mesa
Inu mudabwera basi 🔥🔥🔥🔥
Sooopaaanooo🔥🔥
Those coming from chingaxy family let's gather here
Here we go🙌
We here 👌🤩
Massive 🔥🔥🔥🔥 umakwana
This is masterpiece... @AfanaCeez🔥🔥🔥🔥
Pakala pakaladi apa ❤️🔥❤️🔥❤️🔥
Yo
Tisaphatikizane🔥♥
Dolo uyu sanapalepo🎉🎉🎉❤
Afanawa amatha serious
Live
Hit amwene am in this situation pakala pakala basi andibalalitse iyi taikiratu ma status muuu 🔥🔥🔥🔥🔥🤸🤸🤸
Afana ceez mwayiwe muli uthenga ❤❤
Afana ceez ndi level ya Ku UK olo VIDZ yaonongedwa amwene eeeishhh mmmmmmm nde wina alipakalapakala undiphetse sichomcho 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
😁 😁 😁 😁
Iwe siwamasewera Adah kkkk kuyimba ngati kuimba ndikophweka
Nice tune🥳🥳🥳🥳
Ndiwe dolo 🔥🔥🔥🔥
Mwapha man🔥🔥
Here coz of alexious
Those coming from mikozi let's gather here 🔥🔥
Munachalilatu comment imeneyi 🤣
Ifeo pano
😅😂😂
😂😂
Aha😂
Uli pakala pakala....kupondeleza iweyo achiphazi..... Hahaha mwapha bro
❤❤❤❤ love lit ..... gat me high
Zokongola shashaah🔥🔥
Izoooo u never disappoint me iweyo💕💞
Adha awawa amatha kuimba🙌🔥🔥🔥🔥😅
Zokongola Afana Ceez
Iwe umatiii 🔥🔥🔥🔥🔥 timweraso🔥
❤The guy deserve special 🌟
Pakala pakala on repeat 🔥🔥
On fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥kingpin on point
Chi nyimbo ichi PA MUST eeeeh ❤😂😂
Yonse
The Video Concept Is Very Nice 💚
Leumas ma bit akuyika ase 🔥🔥🔥🙌
Afana ceez ndi dolo❤️
The bond between Leumas n Afana Ceez sungaipange separate ❤🔥🔥🔥
iweyo umabebesa kwambiri 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Nyimbo kukoma kuposa akaz anga😂😂😂 nice tune
iyiyi ngati ili million ndikwanitsa ndekha i've lost count of how many times i've been here😂😂
Fire 🔥 eeeeh za quality,Ife tachokera my zodiak online
Mwapha 💯💥
Music pamalo pake💯🔥
Guy is in his lane 🔥 Concepts n delivery 💯🙌🔥 Tsopanoooo 😂
Dolo kwambiri 🎉❤
Afana Ceez loving this song so much ❤❤❤❤
We missed you bro izi nde nyimbo zovera A.B.A.L.E fekay
Umandisanglasa kwmbiri❤
Chili mwara 🔥
Ya achina afana ceez
Will need to listen to this song again to understand what' the song is all about
Ndipo live adha awaa nyimbo zawoo zimandibalalisaa iiiiii sindimazimvesesaa
Mwapha, chi instrumental nacho chanyatwa 🎉🥳🥳
LeuMas machine kutema mbali zonse izoo 🇲🇼🔥🔥🔥
Iweyo ndi zanyimbo🔥🔥🔥🔥
Afana ceez sanapaleko 🔥🙌🏽
Coming from Akometsi....... Hit mesa🔥🔥🔥🔥
Leumus on the deck 🙌🙌🙌🙌🙌🔥🔥🔥
Dammmn.... First time playing his song. I'm impressed.
Ine olo uyu atangoyasamula I will still download the yasamula🔥🔥🔥🔥🔥I love this one Yama king pin iweeeee🎉🎉🥳🥳🥳🥳🥳
Nyimbo ili bhoooo heavy ndayikonda
Keong Kadango🐐
Dolo katatu
Dolo katatu 🔥🔥 Luso losakakamiza
Kwambil
Video yokhayo nde yajambulidwa bwino 🔥
Kwesta wakumalawi kuno ndiweyo🔥🔥🔥
Those come from x lets gather here🔥🔥🔥
Mukundilemba andiwerenge sichomcho ❤
❤🔥🔥🔥🎶pakala
Umakwana🎉
🎉❤ndaikonda nyimbo iyi🤣🥳🥳pakala pakala
Afana Ceez video nde sumapala aise
😁 😁
iyiyi mwapha 🔥🔥🔥
Amene timayembekeza kut tionako ching'aning'ani kuno let's gather here
🤣 🤣 🤣 🤣 Ine pano
Dolo kwambiri 🔥🔥🔥🇲🇼
Yes iwe❤🔥
Sopano,Adana Ceeze anabwera
Ngat 2pac andishute sichoncho🔥🔥❤
from afana to MADALA ceez 🔥🔥🔥🔥
Tonse aku 23rd tikumane kuno
Banger amwene
Nice song! Big up
Ine koma artist uyu amandiwaza afana ceez like my comment please ❤much love for this side
Dolo
Iwe ngat uli friend wa Ceez like this i will be back
Kkkkkkkkkk
Chi nyimbo ichi chingakome kuma demo 🔥🔥🔥
Koma Ndiye Zinthu Zingasweke
😁 😁 😁 😁 Mwaiponya kwakuya
Mukanapanga paint green chomwe chili pansi pa galimotocho ndi zingwezo you can edit kuti izioneka ngt ili mmalele popanda chogwirizira ❤
Yomweyo iweee💃💃💥💥
Nanga bwanji ukunditchula tchula,andikawe sichoncho😂😂
😁 😁 😁
Nyimbo yabho heavy koma chingwe chonyamura galimoto nextime chisazaoneke ,, big up afana🔥🔥🔥🔥
Umakwanira iweyo
Chili Chonse Nice.. Dope video #RIP Spyral Mwenya
Ma kingpin let's gather here🔥🔥🔥💯undipake sichoncho🔥
Video ili hard koma Kadango watinimaza apa.... Iweo Thank God Omori (T.O.G)
Ife tachokera kwa lawyer
Clean visuals 🎉😊ife2 nde tachokera kwa Hilco nde tikhale pati😅
Afana ceez mi favorite 💎💎
Iwe ndi Dolo ase wapha ikufunika kumochale🔥🔥🔥✅✅✔️✔️💯
❤ wow uli pakala pakala tusaphatikizane 😅🎉. Nyc tune star @afana ceez🔥🔥🔥🥰
Eheee 🥳🥳🔥🔥
Mmene anthu amaipopa videoyi mmayesa akukokomeza ....ndazionera dekha...samanama ndithu💯🔥
Woow great love it 🥰🥰🥰
Zokutchulatchulazo umufuse Ching'axy olo nyimboyi ndayidziwa chifukwa cha iyeyo...........Ilifaya adha🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Zabwino zimenezi 🎉🎉🎉🎉 international level 🌈💯
Keong Kadango 🔥🔥🔥🔥
Real music...osamangokhalira ati nkazi wachithako aaah
Much respect ma guys.. Keong Kadango receive your flowers 🌺
hit 🎯💯💯💯 kwanila inuyo 🔥🔥💯
Olo nzakalambe izi mu ride yanga sizizatsika
Pakalapakala Tisa-phatikizane
✅✅✅✅✅✅✅✅✅✅✅✅ Certified mesa