KUMACHENJERA PATAWUNI INU - CHANGE GOLO ULADI MUSSA WATOKOTA IZI KU MCP RALLY KU DOWA EAST

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 28 ก.ย. 2024
  • KUMACHENJERA PATAWUNI INU - CHANGE GOLO ULADI MUSSA WATOKOTA IZI KU MCP RALLY KU DOWA EAST

ความคิดเห็น • 34

  • @YusufJimmy-v1o
    @YusufJimmy-v1o 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา +3

    DPP+UDF+UTM... ALLIANCE...TIKUCHOSA CHIKANGAWA 2025....NONSE MWALOWA MCP MUZACHITA MANYAZI....KUPANDA UTM SIMUKANAWINA INU

  • @JohnJumah-yf7qt
    @JohnJumah-yf7qt 19 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Kodi mcp inagwa italamula 31 years ,pano yalamula 4 years siingagwe? Komaso nthawi yakale kunalibe madipate

  • @ShamilahSaizi
    @ShamilahSaizi 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Auladi mussah ziwanamizani anzanuwo mulira. Ukunena za ndalama kungowonetselatu kut dyela ndi ndalama muzalira mau Samantha nonse adyela omwe mwapita ku mcp chifukwa chofuna ndalamazo.

  • @FolamiTowing24
    @FolamiTowing24 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Mbuzi scrape politician

  • @YusufJimmy-v1o
    @YusufJimmy-v1o 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Mufune musafune tikuchotsa

  • @beinhardkausiwa7107
    @beinhardkausiwa7107 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Boma ndilomwelidi koma chipani tisintha next year DPP,UTM,UDF,AFORD zikulowa

  • @CliftonPhiri-m8v
    @CliftonPhiri-m8v 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Bambo iwe machendeako otupawo ana ako otupa mitu aja pantumbo pa mayako ndi nkazi wako

    • @JhadahLeafs
      @JhadahLeafs 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Ndiye wamung alulatu

  • @NosiphoMazibuko-e9z
    @NosiphoMazibuko-e9z 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Km amwene uladi ndichisilu kwabasi palibe mfundo yomwe wakambapo zokunzana ndidziko latu tikufuna chitukuko dziko lamalawi

  • @JoelKacheche-x6i
    @JoelKacheche-x6i 21 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kuyankhula zowona zokhazokha mr uladi mussa,Boma ndilomweli sitikusintha,palibe chipani chinga chose mcp mmboma ulendo uno ❤❤❤❤❤❤❤

  • @DjshukulanGift
    @DjshukulanGift 16 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mesa umati ndiwe omenyera ufuru ,wa athu? Kodi ndalamazakez mukut nazo bwaji,? Zipan 5 mukwanisa ?Dpp,UDF,afodi,utm, muwina?

  • @NosiphoMazibuko-e9z
    @NosiphoMazibuko-e9z 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    kd mwayiwala kuti inutso amcp umakaphemba kwa bushiri munalibe ndalama lero muliboma mukuba ndalama zingakuvuteni bwanji poti chitumba chili ndi inuyo

  • @WakisaGodfrey-y8h
    @WakisaGodfrey-y8h 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chipani simusintha uzavota wekha manyaz mulibe dyeratu tundalamato muzaziona 2025

  • @NosiphoMazibuko-e9z
    @NosiphoMazibuko-e9z 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chokani inu mukuwopa kukumangatso inu anakumangani mwayiwala mulandu wanu wopangila anthu akunja ma passport mwayiwala kd mukalowatu inu mumagwidwazo inu mukuwopa kumagwidwa ,

  • @NosiphoMazibuko-e9z
    @NosiphoMazibuko-e9z 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kd anakumangani ndindani amcp ka mukuwopa kuchoka angakumangenizo adpp zadakumangeni

  • @ChristopherNgoma-c9y
    @ChristopherNgoma-c9y 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Umapita kuzipani zomwe zilu zowina kale...usatinyatse wadanzi iwe

  • @MercyChimaliro-fi6mv
    @MercyChimaliro-fi6mv 19 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Panyo panu kumeneko. Tangodya ndalamazo Uladi Mussa ndiwe wadyera iwe aliyense amakuziwa

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 19 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Koma kumaula kuja osakunyozetsa moto umenewo ukupweteka wekha uladi unya ndimagazi akowo

  • @jomochirwa
    @jomochirwa 21 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ayi ndithu kulankhula kuli ndi eni ake.auladi chauta adakudalitsani ndikulankhula😂

  • @ChifundoJohn-w3t
    @ChifundoJohn-w3t 21 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Anthuwo akubwelela kukalandila ma 2pin

  • @FlacksonKapite
    @FlacksonKapite 19 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mnanu Inu andale nsimadziwa kuti zinazo nzopoila

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 18 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kodi mukuziwa kuti kuli dpp eeeti 😊😊😊😊

  • @MchengaAssama
    @MchengaAssama 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Koma ngati ndisanze chipani chonunkha ichi

  • @MustapherLino
    @MustapherLino 17 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Unali ndi chipani chako chinatha ngati makatani

  • @Isaac-m4x3o
    @Isaac-m4x3o 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Boma ndilomweli moti enanu simukuona

  • @FlacksonKapite
    @FlacksonKapite 19 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mmmmm Inu tinachita kuthmangitsa ,

  • @FlacksonKapite
    @FlacksonKapite 19 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Tikumangaso kape iwe

  • @EstherchavulankhomaNkhoma
    @EstherchavulankhomaNkhoma 21 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mwayakhulatu madala

  • @FlacksonKapite
    @FlacksonKapite 19 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Munya akulu

  • @tenexchikumba
    @tenexchikumba 22 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Uladi madala

  • @SABITIKAISI
    @SABITIKAISI 18 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Tikhusinda 😂😂😂

  • @JemaxChibwanazulu
    @JemaxChibwanazulu 19 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mabvuzi anu

    • @ChilekaMoyenda
      @ChilekaMoyenda 19 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Kkkkkkk

  • @MosesDzonzi-em5px
    @MosesDzonzi-em5px 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Boma ndi limwelidi palibeso kusitha ngati wina akufuna kusitha angositha dziko Kaya apita ku joni Kaya ndi dziko liti koma kumalawi kuno sitikusitha boma olo fulu atadukula