My Comrade The Commander Mtanyiwa is here. ❤❤❤loved and protected in God's Power. Chikangawa Party mungophimba Nyansi nkumazitcha amzeru Ochenjera . Koma pa Mulungu simungaphimbe zibvundizo . Lets wait for your judgement day MPC 👹⚒️🐊🐊⚒️🔨🔨👹
Ambuye akubiseni amtanyiwa in his wings antill tawina my 2025 ndipo mens dziko lililipamoto mulungu sungalole kuti Dani apambane AI inuyo antill we succeeded pafikaa Malawi ever since independent comes dzikoli silinafikepo apaaà Boma ili lationesa dzithu
Amene akulankhul zoti okutumiza ndi dpp , ndi mbuzi za mcp , Akuziwa kuti alibe mpata 2025 Aku Israel ndi anthu oipa koma iye alinawo mgwirizano pulezident wanji uyu ,asatana.
a antanyiwa mumayima pa chilungamo nthaw zonse Ambuye azikhala nyali; yanu nthaw zonse za moyo wanu,❤❤❤
Mulungu menyerani nkhondo amalawii nkhondo siyawo nkhondo ndiyanu remember Malawi my God
Ambuye inu amene mumabisa miyoyo yathu pamene adani safikira, bisani moyo wa Comrade mtanyiwa ndipo adani asamamuone konse🙏🧎🧎🧎🧎
Nkhani Zina zikumakhala zoti simunamalize kufufuza.
You are such a loving and honest man . As Malawians , we are blessed to have you.
Following you Limpopo
Comrad or mutaimila u present i will give you my vote❤❤
Limpopo FM only radio we are trusting right now ❤
My Comrade The Commander Mtanyiwa is here.
❤❤❤loved and protected in God's Power.
Chikangawa Party mungophimba Nyansi nkumazitcha amzeru Ochenjera . Koma pa Mulungu simungaphimbe zibvundizo . Lets wait for your judgement day
MPC 👹⚒️🐊🐊⚒️🔨🔨👹
Achakwela mufunabe kupha azanu komatu 1 muzalipila izi zose mukupanga thawi ndi imozi muzakhulupilila
Mmmmm koma zafikapo kodi mukufuna dzikori kuti mudzikharA nokha ko chakwera kwenikweni ndichani chosativera chi soni ife amarawi
Mupitilize kutidziwitsa chonde ambuye azikudalitsani
Ine niyowe chitumbuka kut chiuta wamutumbikeni ❤
Mtanyiwa !!!
Murugu pitirizani kuwatetezera antanyuwa
Osamati kusiteti house koma kuweya house yosugirako zigawega siteti house ndi maidziwa
komatu kumva ndiye tikumva koma opposition ili nziiiiii kugona tulo eeeeee
Ambuye akubiseni amtanyiwa in his wings antill tawina my 2025 ndipo mens dziko lililipamoto mulungu sungalole kuti Dani apambane AI inuyo antill we succeeded pafikaa Malawi ever since independent comes dzikoli silinafikepo apaaà Boma ili lationesa dzithu
Game on Mtanyiii....😅
AMTANYIWATU MUMAYESENSA KUTIUZA ZOBISIKA ZIMAKHALA NGATI ZABODZA PAMBUYO PAKE MKUMATI MTANYIWA AMKANENADI ZOONA..DZIKO LA MALAWI LILIBE OPOSSITION PATERY YOFUNA KUPULUMUTSA ANTHU MMAVUTO AYI , KOMA MA OPOSSITIONS ANTELA AMASO PANDALAMA, MUMAWAUZA ZAMBIRI KOMA PALIBE MCHIMODZI CHOMWE ANACHITSATAPO..MUNAUZAPO ZA KALEMBALA AKUCHITIKA KUNO KUMALAWI KT ATSATILE MMALO MOMWE AKULEMBETSAMO AKAKHUMUDWA SANA KHUZIDWE ,...INFE OSAKHALA ANDALEFE NDAMENE TIKUDANDAULA KUDANDAULILA MALAWI WATSOPANO AMENE ALIBE MTSOGOLERI WA ASILIKALE ANKHONDO UYU ALIPOYO NDI WACHIPANI CHA MCP, MA POLICE NAYENSO WA CHIPANI ,OSATI ADZIKO AII,,,MUNAYESA KUFOTOKOZA ZAYOMWE ANAPITA KU BARACKS KOKAPHA MKAZI WA MSILIKA ATAMULEPELA MSILIKALIYO AII ZINATHELA MMALUWA...KU BARACKS MPAKA KULOWAKO ACHIFWAMBA HIIIIIII ZOSANVEKA, NDICHIFUKWA CHAKE A MCP AKUMANENA KT MTANYIWA NDI WANTCHITO WA DPP, KALINDO,TV BAKILI ,CHIFUKWA CHOSALEKEZA KUZUZULA MCP,CHOSECHO MA OPPOSITIONS ATANGOKHA ALI PHEEE ZOSAWAKHUZA MMITIMA MWAWO , ACHIHANA NAONSO ALIPHEE ANVEKELE CHIPANI CHA AFORD NDI MKHALAKALE PA NDALE, TADZUKANI AMTANYIWA NDI AZIZANU KUTI KODI OTSUTSAU ALINANU LIMODZI..ACHIHANA NDI MADALA ANOO A MUTHALIKA NDI ENA ONSE NDINU A OPPOSITION NDI AMENE MUKUPANGITSA MANVUTUWA KT AZIMKA CHITSOGOLO, PAMENE MTANYIWA AKUKUDZUTSANI KT WORK UP MPAMENE INU MUKUMAGONA,ZILIBE TSOGOLO ,MUZAZIONA MUZAZIONA MUKHALE PHEE WANUYO CHIFUKWQ CHA UDYELA WANU MCP 79%VORTS MIGWILIZANO YANOYO 21 %..OPPOSITION YOGONA MWADALA TINAKUDZIWANI KALE KT NDINU AMODZI NDI MCP.
Tilira chilimayo mpakana liti
1:00 komatu asilikali athuwa akupanga zopepera
kutchela kumwezii
Kodi asilikali amalawi kodi wose akusangalala ndizimene akupanga Chakwera or anagulidwa?
President opepela uyuu😢 koma ndiye atithatu Chakwera
Ineso ndikurero azikudalisani
Makape ena mumangokhulupilira zilizose nd Thobwa lomwe ngati ili
We are not safe
Tingodziwa ndi maliro ena awo kaya ndiye akhala ndaninso ulendo uno 😢
Cja
Unipolære airport koma amafuna za chinsinsi.
Is it the same position Of President to order assassins from Israel.
Boma tinagulisa kwa satana razarus chikangawa is a devel,
Ulemu wanu mtanyiwa mulungu szikudalisani nthawi zose
Koma dzoona chakwera pamutu sipamayenda bwino anthu akudwara makomomu iye angakasegule chipatara chokuti sichinathe ananganizabwaji kkkkkk olowamisarayo
Koma a Mtanyiwa taponyani chi nsomalicho hammer ilipo iyi tikhomere chikangawa adatizolowere
Komoleti zabwino zonse Allah azikudalisa
Ipondeni atanyiwa simuli nokha ayii
Amwene tikudikila kwa inu osat zimene anatiuza aboma
Tilipano kumvela chilungamo yomwe. Antanyiwa ulemu wanu bwana
Akufuna kupha ndani tsopano
Ntanyiwa ndi Ntanyiwa
Ineo ndye ndmamakiza izi
Tulutsani big
Inu uyu palipose muzingogenda basi ndi galu kobasi mr chikangawa inu ndi ndalama zingati ayendela anthu 11 moti agagawile anthu ku machinga iyeyo kusakaza misonkho yanthu
Umatha
Koma ntanyiwa iweyo eeee umationjeza kwambili
Kodi chakwera ukufuna utichite chiani koma inuyo chooonde tithyoolanapo aaaaaaapa tsono
Tatulusani ma audios musadikirenso kuti mbozi zany ziime
Tifunsileni akubanja kwa achilima kuti alibe choyankhula pazomwe akuyankhula a mcp akutumbwa kwambiri pamene ife mitima yathu yidakali yowawa akhala chete akubanja tikuziwa misozi yidakali yambiri mwa iwo koma angotiwuza kuti akufuna chilungamo chiwoneke tilowe ma demo
Kkkkk
Anthu mudziko muno akuvutika mu njira zambiri, mzipatala mulibe mankhwala, koma mtsogoleri ali busy kumwaza ndalama kulipira ndalama zambiri mbiri kulipira anthu amayiko ena ndicholinga choti azipha a Malawi. Komanso pena pake asilikali athu mudziko muno mchifukwa chiyani ali ogona chonchi? Shame on you asilikali MMalawi muno
Eya zoona
ponyanu audio tiyinvere antanyiwa osawasekerera
Koma abale Chakwera akuganiza bwanji
Iiiiiiiiiiii koma
Amene akulankhul zoti okutumiza ndi dpp , ndi mbuzi za mcp ,
Akuziwa kuti alibe mpata 2025
Aku Israel ndi anthu oipa koma iye alinawo mgwirizano pulezident wanji uyu ,asatana.
Timvesere basi
Koma dzoona chakwera pamutu sipamayenda bwino anthu akudwara makomomu iye angakasegule chipatara chokuti sichinathe ananganizabwaji kkkkkk olowamisarayo