BRIAN BANDA NDI ZOMWE AYANKHULA A DR CHAKWELA

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 28 ก.ย. 2024

ความคิดเห็น • 215

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 3 หลายเดือนก่อน +17

    Aliyense azafa osatsogoza anzanu chifukwa chofuna kulamula dziko, zitsilu inu a MCP ndimatsenga anu a nyau

    • @RiteRoderick
      @RiteRoderick 3 หลายเดือนก่อน

      Ndipo Zoopsatu anthu oipa zedi awaaa mmmm

  • @Geraldmkwewu
    @Geraldmkwewu 3 หลายเดือนก่อน +4

    Iwe chakwera tangonena komwe kuli chilima simoyo umenewo

    • @EvanceSungani-cv9jk
      @EvanceSungani-cv9jk 3 หลายเดือนก่อน

      😂😂😂😂😂 koma guys oh simyo wabwino et?

    • @DoshenSulan
      @DoshenSulan 3 หลายเดือนก่อน

      Ndpo anfufuzetu ameneyo fast

    • @adamusaidih8570
      @adamusaidih8570 3 หลายเดือนก่อน

      😂😂😂😂😂

    • @adamusaidih8570
      @adamusaidih8570 3 หลายเดือนก่อน

      😂😂😂😂

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 3 หลายเดือนก่อน

    Mfiti chi president chokupha😢

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo 3 หลายเดือนก่อน

    Inu ndege yasowa 10am inu ngati president mwadziwa Chama 3pm ugalu okhaokha

  • @Nyodzani123Jmlingz12
    @Nyodzani123Jmlingz12 3 หลายเดือนก่อน

    Ine ndadandaula kut Chakwerayo sanakwele nawo naye akanakwera nawo afele limodz agalu amenewo😢😢😢

    • @MasterMango-pm4ei
      @MasterMango-pm4ei 3 หลายเดือนก่อน

      Akwera bwaj mwini wake chiwembu Mcp ntchito zake ndkupha koma amalawi mumavota Dara izi aaaa

  • @charityamos2183
    @charityamos2183 3 หลายเดือนก่อน

    Chonde chonde chakwera usandichimwitse wamva chimene ukupangira chibwibwi ndi chani?? Uzalipira mwadzi umenewu

  • @JoyceBanda-k8t
    @JoyceBanda-k8t 3 หลายเดือนก่อน

    Iwe cakwera wamutani chilima kutero iweyo umangoganidza za magazi basi abusa assembles mmmm mulungu akuyendereni

  • @gizzykondwani865
    @gizzykondwani865 3 หลายเดือนก่อน

    Achakwela speech yawo sikumdimvekela bwino bwino

  • @ShukuSh-vi1hk
    @ShukuSh-vi1hk 3 หลายเดือนก่อน +2

    Palibe wabwino apa asewa akanakwela ndege limozi ndikufaso limozi mesa ndi m mene amabera ndalama zathu zamisonkho

    • @petertaulo8014
      @petertaulo8014 3 หลายเดือนก่อน

      Inu ndi achitsiru kwambili

    • @ShukuSh-vi1hk
      @ShukuSh-vi1hk 3 หลายเดือนก่อน

      @@petertaulo8014 zako zimenezo wapita basi akabela ndalazo kumanda

  • @MarthaNkhata-m1k
    @MarthaNkhata-m1k 3 หลายเดือนก่อน

    Lord have mercy.

  • @WysonSaboko
    @WysonSaboko 3 หลายเดือนก่อน

    Achakwela ndi nduna zanu mukuziwapo kanthu ndipo mukayankha mulandu siku lomaliza

  • @HajjiWilson
    @HajjiWilson 3 หลายเดือนก่อน

    Tipeza amene atapulumuke?? Akutanthauzanji??😢 Iye akudziwapo chani? Kusinyeza kuti yagwa? Or yapsa ?or yira ? Or yakatera dziko lina?
    Osapulumuka ndiye sawaoeza?? Soeach iyiyu mmmmmmmmm🇲🇼🇲🇼🇲🇼👀👀👀👁️👁️👁️👁️

  • @samuelsergio5343
    @samuelsergio5343 3 หลายเดือนก่อน

    Mr president??????

  • @HestingsZiba-d6k
    @HestingsZiba-d6k 3 หลายเดือนก่อน

    Mayankhulidwe akukayikisa galu uyu bwanji osapita iwe unyamuke ukasake nawo ndegeyo galu uyu

  • @MajiduMakiyi
    @MajiduMakiyi 3 หลายเดือนก่อน

    Akuti mcp inabwela kuzakhadzika basi munthu kusowa ayi zikomo

  • @GiftSnoxy
    @GiftSnoxy 3 หลายเดือนก่อน

    Chitsiru iwe chakwera umwarilanso Poti chilima akamaora iwenso kumaola

  • @NausaPilirani
    @NausaPilirani 3 หลายเดือนก่อน

    Mkulu wa bodza uyu
    Tikukhululukira chani tsono

  • @Lenimtambo-ih8rm
    @Lenimtambo-ih8rm 3 หลายเดือนก่อน

    Mulungu azakulangani bambo lnu pamiyoyo yawanthu yimene mwayipeleka sembe

  • @kennethkaunda3636
    @kennethkaunda3636 3 หลายเดือนก่อน +1

    Salanjenso adamusowetsa

  • @AbdullLatiff-qr3wg
    @AbdullLatiff-qr3wg 3 หลายเดือนก่อน +1

    Bola mukhala inuyo achekwela chifukwa ifeyo sitimakufuna kuti bola chilima

  • @FrancisDay-br7xb
    @FrancisDay-br7xb 3 หลายเดือนก่อน

    Adzalolera kukhetsa mwazi kuti apitilire kukhala pampando. Amalawi munthu uyu ndi oipa. Msonkhano wathao analengezetsa kuti aimanso. Kumbukilani amalawi kuti uyu munthu anapha president wa assembly of God Kuti iye akhalepo. Uyu ndikathyali don't trust chakwera . Bon kalindo chilima ukusewera ndi njoka, ndiolotse kankutafune

  • @LastonMlozi
    @LastonMlozi 3 หลายเดือนก่อน

    Rip

  • @SahilluYusuf-sk7es
    @SahilluYusuf-sk7es 3 หลายเดือนก่อน

    Chakwera is refunding the money through blood to Bushiri ,as he is killing people who are not supposed to be killed whyy,kupha munthu satelo ,what you plant you will grow you must know that everyone shall test death ,ndee iwe kupha nzako pachifukwa cholamula ,uzaona polekera mfana iwe ,chakwera ndimunthu opusa kwambir kupha anthu oti amuthsndiza,look how he killed sidiki Miaa

  • @BandaAdam-ee3xk
    @BandaAdam-ee3xk 3 หลายเดือนก่อน

    Ndizinthu zopweteka Munthu mwango mumasula pamilandu

  • @jamusnamwino-br2iz
    @jamusnamwino-br2iz 3 หลายเดือนก่อน

    zikomuno mukungolowesa zingawenkha zipaso zake zayamba kuoneka

  • @MustafaLikaomba
    @MustafaLikaomba 3 หลายเดือนก่อน

    Anamumasulila zomwezo inu simukuona angapange bwanji titini atangonkhala

  • @JohnsonMaulana
    @JohnsonMaulana 3 หลายเดือนก่อน

    Mukulimbikila kufuna ndege mmalo miyoyo ya anthu

  • @eliaskhofielias8152
    @eliaskhofielias8152 3 หลายเดือนก่อน

    MCP ndiyoipadi zaoneka apa.they are behind this assassination.amadziwa kut awayabwa agaluwa.akut tingopha basi ngat tingamulephere tivutana naye pazagwilizano wathu uja.koma a MCP chomwe mungadziwe mulungu si james ayi.ufumuwanu tauyesa koma mwalephera muchoka basi m'boma and nthawiyi idzafufuzidwa.inu kamalawi kakang'ono ngat kameneka munthu akasowe zoona mwawabisa kut mmatsenga anuwo?anthu oipa awa maka achina ritchad banda,mkukuyu ndi ozungulira kamutu kaja ometa old fashion kujemera dazi uja mitima imamawawa kut tikuchokadi ife zoona.munapha sidik mia leronso ndizi.mupha angat kod?

  • @MustapherDavie-su3nk
    @MustapherDavie-su3nk 3 หลายเดือนก่อน

    Phanani Koma nzimu wuliwose uzalawa imfa

  • @EdisonNakulenga
    @EdisonNakulenga 3 หลายเดือนก่อน

    Pazuzudipafupi bwajisanakwele galimoto imeneyidipulani samalani tawaibilani akaziawo achilimativemeneagatifotokozele ayakuleniakazawipopanotive

  • @GanizaniKhuliwa
    @GanizaniKhuliwa 3 หลายเดือนก่อน

    Yehova mulungu wathu pulumutsani Achilima ndi anthu ena omwe alimu ndegemo🙏🙏🙏

  • @KhwipsFilm5050production
    @KhwipsFilm5050production 3 หลายเดือนก่อน

    Zovuta ndithu

  • @petertaulo8014
    @petertaulo8014 3 หลายเดือนก่อน

    Oputsa iwe mfiti ya munthu

  • @StewartGoma
    @StewartGoma 3 หลายเดือนก่อน

    Really President this massage is very stupidly n childish

  • @BonfaceMajawa
    @BonfaceMajawa 3 หลายเดือนก่อน +18

    Ine mene ndikumuonela chakwelayu kayakhulidwe kake ngat Akuziwapo kathu 😢

    • @inessmsiyambiri8517
      @inessmsiyambiri8517 3 หลายเดือนก่อน +2

      Aaaa Inu mukuona ngati chani aaaa

    • @SaidiMbawa-st6bj
      @SaidiMbawa-st6bj 3 หลายเดือนก่อน +2

      Inu inu sogozani Mulungu

    • @Allan-bk1
      @Allan-bk1 3 หลายเดือนก่อน +1

      Ukuziwa eti olo Wanda msisha dzuro chama 9 analindinkhope yachisoni

    • @adamusaidih8570
      @adamusaidih8570 3 หลายเดือนก่อน

      😂😂😂😂

    • @BonfaceMajawa
      @BonfaceMajawa 3 หลายเดือนก่อน +1

      Muthu wabodza amaduka dukatu kd mumuvele bwino bwino guyz

  • @OmarMkwela
    @OmarMkwela 3 หลายเดือนก่อน +3

    Ine ndamvera Limpopo FM mmene ndamvelera a Malawi defense force anaitulukira nthawi yabwino koma awawa ndi abale awo amene anagwirizana nawo anawawuza asilikali amene anaitulukira ndegeyo kuti achoke pamalo padachitikira ngoziyo anapanga dala zimenezo wakupha uyu

  • @gladysmavutulah
    @gladysmavutulah 3 หลายเดือนก่อน +2

    Uyitana bwanji anthu akunja kusiya maiko amene ali pafupi? Kma ubusawo umayendadi kapena mumangosocheletsa n'khosa?
    Dziko ndi anthu ake May the Lord Almighty help us🙏

  • @atusayemwandelile8307
    @atusayemwandelile8307 3 หลายเดือนก่อน +8

    Dege yakugwaa mamawa foll up kuyamba madzuro

  • @KondwaniNguleti-x1q
    @KondwaniNguleti-x1q 3 หลายเดือนก่อน +3

    You Chakwera wam'gulitsa mzako Chilima kwa asilikali a ku Israel 🇮🇱 I know u bwinobwino

  • @Doreen-hz9ce
    @Doreen-hz9ce 3 หลายเดือนก่อน +3

    Ambuye mutetezele miyoyo ya anthu omwe Ali mu ndegeyo chifukwa pa ife tokha sitingakwanise kitelo ndi pemphelo lathu ndipembedzelo pa zoopsa za chitikazi amen

  • @MelvinVanRooyen
    @MelvinVanRooyen 3 หลายเดือนก่อน +2

    Wasiwesa ndiwe chakwela boma lamanyadzi kulephela kusaka ndege koma ndamala zaboma zaziiii😊

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf 3 หลายเดือนก่อน +4

    chitsiru iwe ndi amene wamupha chilima asakuziwa ndani iwe chigawenga ndi zigawenga zimzako unazipanga order ku isilaeli iwe satana

    • @MACFARLANEMULENGA
      @MACFARLANEMULENGA 3 หลายเดือนก่อน

      chitsiru ndi iweyo wamva. Don't bring confusion pa kusowa kwa ndege wava

    • @JafaliAkimu-ll1bf
      @JafaliAkimu-ll1bf 3 หลายเดือนก่อน

      @@MACFARLANEMULENGA wasowesa ndi ambuyako achakwera chimbalangondo cha dzilo satana mbuzi ya muthu icruding iwe kape wadziko

    • @JafaliAkimu-ll1bf
      @JafaliAkimu-ll1bf 3 หลายเดือนก่อน

      @@MACFARLANEMULENGA am taling you mbambadi chakwera azamwalila ali chiimire i promes you

  • @jamesgama5489
    @jamesgama5489 3 หลายเดือนก่อน +2

    Fuso langa kodi mene ndegeyi imanyamuka ku mzuzu kubwera ku lilongwe nyengo kumeneko inali bwanji? Chabwino ngati a anyamuka nyengo ilibwino ngati nyengo inasintha mbuyo bwanji osayimba phone kuti musanyamuke kuno nyengo silibwino.

    • @JacklineDenis
      @JacklineDenis 3 หลายเดือนก่อน

      Ndi opusa président wa Amalawi

  • @innocentissah2636
    @innocentissah2636 3 หลายเดือนก่อน

    Poti Asilikali a Israel alikomko kale , m'malo mopempha maiko amuno mu Africa monga South Africa, Zambia,Kenya, Tanzania akutchula dzimaiko zakutali

  • @AbdullLatiff-qr3wg
    @AbdullLatiff-qr3wg 3 หลายเดือนก่อน +3

    Iweyo chekwela ndamene wamusowesa ndiwe galu kobas

  • @ElizahMadi
    @ElizahMadi 3 หลายเดือนก่อน

    Wowona Za nyengo ,munalola bwanji Kuti ndege yinyamuke ? And yinanyamuka bwanji Ku Mzuzu mukudziwa Kuti nyengo siyilibwino?? Usatana uwu. Kodi Chi MZIMU cha Kamuzu Banda chiliso mwa inu bwana ??

  • @IsaacTsinde
    @IsaacTsinde 3 หลายเดือนก่อน +1

    Chakwera akupanga chibwibwi sindikumukhulupirira uyu lord please help..

  • @TrizaGeorge-q8w
    @TrizaGeorge-q8w 3 หลายเดือนก่อน +2

    Kungoti abambo awa ndimuthu opanda chilungamo muthu wachabe chabe chakwela mmmm

  • @HajjiWilson
    @HajjiWilson 3 หลายเดือนก่อน +1

    God have mercy all those people they have responsibility
    You are the one who knows the truth about that missing
    We have many question but only God knows everything

  • @NovemberMmangathayo
    @NovemberMmangathayo 3 หลายเดือนก่อน +1

    Anthuoyipa a mcp mulandilachilango mulungu akulangani

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 3 หลายเดือนก่อน +3

    Ee3 kutchula mulungu pachabe 🙌🏿

  • @replacefruittreenursery
    @replacefruittreenursery 3 หลายเดือนก่อน +2

    Ngati ndege inachoka ku mzuzu .ndiye ku mzuzuko mwadzizi nyengo ndikusitha chinamvuta ndichani kuwaudza kuti musanyamuke ku Lilongwe kubwera kuno ku mzuzu chifukwa kuno nyengo yasitha .
    Nkhan imenei ikubalarisa zedi.

  • @JohnsonMaulana
    @JohnsonMaulana 3 หลายเดือนก่อน +2

    Mkuluyi walongosola kumbali yake so sad pena pake pakukaikitsa zed😢

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 3 หลายเดือนก่อน

    Kodi ku maliro ko bwanji nduna zodziwka za mcp sizinapiteko????
    More over chilima anali so kuchokera ku ulendo wina!???? 💔💔

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 3 หลายเดือนก่อน

    Munachita kugwiri zana wachita ngati m'mene ada chitira Putin ndi prighozin,koma Chakwera sudachite Bwino kumupha Chilima ana kula kwira chiyani Osamu khulukira Chifukwa CHOTI amafuna kuimirira usogoleri Kodi popanda Chirima ukada wina? nonsense

  • @HillgreyMunkhondya
    @HillgreyMunkhondya 3 หลายเดือนก่อน

    MCP basi yipakire asadzaloweso mboma anthu akupha kuba eeeeeeee mudziwapo kanthu Inu kuphana chifukwa Cha utsogoleri mukaramurireso kumanda.

  • @DelxMasanjala
    @DelxMasanjala 3 หลายเดือนก่อน

    Sakanamupha chifukwa ife timadik ra kuti 2025 tikawachosa pampando alowe jere chuma chao chonse chilandidwe chibwelere iu boma apa ND ye kuti case ya chilima pansi pano yasekedwa pano kumwabako akuyankha mafunso awoononga malawi ndi kuba

  • @JosephNgona-f9v
    @JosephNgona-f9v 3 หลายเดือนก่อน

    Wabodza uyu chakwera wamugulitsa chilima wafera chilungamo.born kalindo wakhalaakuyankhula komachilima kusamva mlongo wanga.ndipo akangofa anthuawa uwadziwa amalawi

  • @EdisonNakulenga
    @EdisonNakulenga 3 หลายเดือนก่อน

    Isowabwaji gatizikosilatu gatitilizijo lamozabiki dimayesa dimalawimomuno mapuamalawialukutiko mulidisabiinu mulunguakuoneni

  • @sinoiajamu9484
    @sinoiajamu9484 3 หลายเดือนก่อน +2

    Our Lord our King save our chilima

  • @KondwaniLungu-x5l
    @KondwaniLungu-x5l 3 หลายเดือนก่อน

    Wasalayo iwe uziona satana wen wen , kaya umaziwa kaya koma I think suziwa mmene umapangila zinthu zako , and unakakhala oziwa akele lomwe unakatula pasi udindo koma kuipa ntima bsi, bola yona anavomeleza nsanga kuti anthu ake asamwalire . Koma iwe walimba ntima kuti tifele limozi ai zikomo Mulungu akupase moyo wautali ndi kuipa ntima kwakoko.

  • @SophieKamanga
    @SophieKamanga 3 หลายเดือนก่อน

    Mwamupha inu zanu chifukwa chakufuna ulamulilo wa dziko km chomwe ungadziwe chakwala suwinaso pazomwe wachita kumupha chilima anthu aipa inu achipani cha mcp munazolowela kupha ndikusamba magazi anthu

  • @DoricaGoweka
    @DoricaGoweka 3 หลายเดือนก่อน

    Lazaro iweyo Mulungu akukanthe ndithu mumtima mwako ukusangalara ukudziwa kuti plan yako yatheka

  • @AgnesMalondaPhiri-pt2vh
    @AgnesMalondaPhiri-pt2vh 3 หลายเดือนก่อน

    Bodza lokhalokha, komatu olo musowese chilimu sikut muwinabe, afisi inu

  • @JosephNgona-f9v
    @JosephNgona-f9v 3 หลายเดือนก่อน

    Mumuone pa kamwa pakepo akuchita kuoneka kuti akunama uyu chakwera iwe utiuze komwe kuli chilima tatopa bro nkhaza zako satana iwe

  • @FunnyKatchenga
    @FunnyKatchenga 3 หลายเดือนก่อน

    Mmmm shame on you, kutereko a islael agwira ntchito mmmm Jan mumawaitanila kuti athane ndi chilima?

  • @JacobBelnardo
    @JacobBelnardo 3 หลายเดือนก่อน

    Chofunia thandizo maiko akutali ndichiyani pamene maiko apafupi kuthekera Ali nako

  • @harrymicah6140
    @harrymicah6140 3 หลายเดือนก่อน

    Mmmmm akuluwa tinataya chikhulupiiro ndithu kaya palibe okhalisa mmziko

  • @FunnyKalimwayi
    @FunnyKalimwayi 3 หลายเดือนก่อน

    athu musadandaule zosezi mulungu akudzuwa tingolilila payesu yekha basi

  • @JamesChiphwanya-m4v
    @JamesChiphwanya-m4v 3 หลายเดือนก่อน

    Chakwera mathero azanu ndamenewo iwesotu uzafa imfa ya chisilu

  • @MACFARLANEMULENGA
    @MACFARLANEMULENGA 3 หลายเดือนก่อน

    Koma Peter Muthalika? Nonsense, osalowetsapo ndale apa

  • @JacklineDenis
    @JacklineDenis 3 หลายเดือนก่อน

    Mulungu wo simukumuziwa kuma kuzunza anthu obwera ngati ndi obwera

  • @shayrafernandeslatif9556
    @shayrafernandeslatif9556 3 หลายเดือนก่อน

    Ndege yasowa mmawa, social media inanena kale koma boma kukanika ku Nena??

  • @WonderMinjale-bg6kd
    @WonderMinjale-bg6kd 3 หลายเดือนก่อน +1

    Kodi katundu anakagura satah uja panalibe ndege?????

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 3 หลายเดือนก่อน

    Nkhani iyi Chakwera ukadyera nazo nsima pa window udziwanso

  • @EdisonNakulenga
    @EdisonNakulenga 3 หลายเดือนก่อน

    Kodi imakanizidwabwaji PA galaudikutiisikebwaji koma

  • @jameskachulu8141
    @jameskachulu8141 3 หลายเดือนก่อน

    Pepani utm sogoleleli amene yu kusava chilima

  • @MacdonaldMisomali-lt4wu
    @MacdonaldMisomali-lt4wu 3 หลายเดือนก่อน

    Iwe ndwachibwibwi ukuziwapo kathu galu iwe

  • @LukaAfromad
    @LukaAfromad 3 หลายเดือนก่อน

    Ngati nikutukwane kwambilitu nkamakumva ukuyankhula

  • @WedsonVinkhumbo
    @WedsonVinkhumbo 3 หลายเดือนก่อน

    Kuchoka mamawa koma malawi ziko lontembeleledwa

  • @InnocentMakwinja-oi3eb
    @InnocentMakwinja-oi3eb 3 หลายเดือนก่อน

    Sindikutha kuvesa ndizomwe ndikuvazi

  • @FrankeSimba
    @FrankeSimba 3 หลายเดือนก่อน

    Manyazi ulibe umudziwe yesu chakwaza

  • @GreysonChilongo
    @GreysonChilongo 3 หลายเดือนก่อน

    Funso imwe a MCP uyu ndiye mugwizano?????

  • @RestarUmi
    @RestarUmi 3 หลายเดือนก่อน

    Koma ngat samu yake ili iyiyi nde stigwilizanapo

  • @AndrewMdala
    @AndrewMdala 3 หลายเดือนก่อน +1

    Koma dziko lamalawi ndilomvetsa chisoni

  • @RastaNtonyo
    @RastaNtonyo 3 หลายเดือนก่อน

    Kuyakula samatha koma kuba bass pot alowa pitha

  • @JosephMwambe-rz2oy
    @JosephMwambe-rz2oy 3 หลายเดือนก่อน

    Zoonad awawa awonjeza kwambili amfit amenewa

  • @graciousmathewe-of7tl
    @graciousmathewe-of7tl 3 หลายเดือนก่อน

    E mwapanga not zimene zochitika iya

  • @FrancisDinala
    @FrancisDinala 3 หลายเดือนก่อน

    Sory chakwera wasala wekha zoona 😭😭😭

  • @JoyceChimphwika
    @JoyceChimphwika 3 หลายเดือนก่อน

    Mr chakwela where is vis president, you doing noses.you exactly what was happening because don't ask people that story, this is the your plan you are div

  • @ChimwemweHenry-uw1bq
    @ChimwemweHenry-uw1bq 3 หลายเดือนก่อน

    Osamgonena kt zomwe mumafuna zatheka bwanj....munthu wangobwera masiku omwewa ku ulendo.mukumtumizaso kumalilo osapita inuyo bwanj.mesa mumakonda kuyenda ndinu agalu achabe chabe

  • @juntoiman
    @juntoiman 3 หลายเดือนก่อน

    Ngati munthu amamwalira pangozi ya Njinga Chilima ndindani atakhale osamwalira pangozi ya NDEGE rest in peace Malume😂😂😂😂

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp 3 หลายเดือนก่อน

    Kwenako iweyo chakwera galu

  • @besterlumbe4404
    @besterlumbe4404 3 หลายเดือนก่อน

    Chakwera ndiwe mfiti yamunthu ukudziwapo kanthu,nzako wangobwera kumene kuchokera ku korea komwe unamutuma,lero nzako asanapume nkumutumanso kuti apite kumaliro asanapume bwanji sumapitako iweyo ndi nkazi wako? Galu wamunthu ukudziwapo kanthu

  • @DadaChikondiBluektoo
    @DadaChikondiBluektoo 3 หลายเดือนก่อน

    Wampha nzako ndiwe chakwera

  • @ChikumbutsoTsalangu
    @ChikumbutsoTsalangu 3 หลายเดือนก่อน

    Mwapedza potafunila drama

  • @ElliottBelon
    @ElliottBelon 3 หลายเดือนก่อน

    Galu wamunthu iwe mulungu akuone

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg 3 หลายเดือนก่อน

    Iwe chakwera usiye Kutchula Mulungu, machitidwe ako samagwirizana ndi za Umulungu. Umachulusa bodza ndie Mulungu sagwirizana ndi bodza.

  • @KondwaniNguleti-x1q
    @KondwaniNguleti-x1q 3 หลายเดือนก่อน

    Timati 3 o'clock not 3 kaloko

  • @innocentmusuli7380
    @innocentmusuli7380 3 หลายเดือนก่อน

    Ndege imachokera ku mzuzu komwe sikunali bwinoko , pomwe amanyamuka samawona nyengo kuti pobwela sitizatela bwino ayi zikomo