In Love with the local concept in the music it really defines our culture .. the use of drums, dressing ,dances even kumudzi thus what defines us as Malawians.... nice song.
@@chisomolipenga7130 i didn't mean kumalawi nkumuzi but komwe ajambulirira nyimbo its rural area of which many prefer using urban areas when shooting their music videos👍🏻
Ineyo sanje ndi ine tinadana kalekale ndeno Emmie Deebo & Qaso nyimbo iyi mwayipha bho kwambili with local concept 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 Nde Deebo akati amenye smile eeeeeeeeeh ngati asasiye
When local music meets us local people🤣😂 we break our waist as if its not ours🙃 I am falling in love with this song🥰 Emmie Deebo here you come🤩🤩 daymaker🥰
This song is an absolute vibe! The rhythm is infectious, and the lyrics, too, are a beautiful celebration of cultural heritage. The vocals are captivating and the way you blended traditional elements is pure magic. A true masterpiece that will resonate with listeners of all ages. Can't wait to hear more from this talented artist!" 💥💥💥
Chi nyimbo ichichi chivuta heavy chaka chino mu zinamwali 😂😂😂💥🔥 Nice hit Emmie Deebo ka local girl 😍🔥 Akometsi tigaireni mtsikanayu akayanbe udindo wake wen wen monga munthu wa mayi 😂😂👊🏃🏼♂️🏃🏼♂️
Chipande sipakula bwino nsima popanda kupaka mafuta. Behind every successful artist there is what we call the super supporting team. Please let's cherish them!
Concept yabho i like it❤
Who else like this concept lets gather here
In Love with the local concept in the music it really defines our culture .. the use of drums, dressing ,dances even kumudzi thus what defines us as Malawians.... nice song.
Let's decolonise these eurocentric ideology.
Ku malawi sikumudzi
@@chisomolipenga7130 i didn't mean kumalawi nkumuzi but komwe ajambulirira nyimbo its rural area of which many prefer using urban areas when shooting their music videos👍🏻
Ndiposo iyeyu apitilize izizi
🔥🔥🔥🔥
@@ChifuniroMbiya kwambil zili bwino
Iyi tidyera mma weddings ceremonies 🔥🔥🔥🔥🔥🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼
Ana onse akagwilitse kuukwatilo😅
Indeeeeeeeeee🎉
Ndpo nde ivuta
Yamutadi maukwatimu
Qaso dolo kwambiri akometsi yonse 🔥❤️
Style ya unique, lyric ya mwala , video mbambande , what else 🔥🔥
Nice video 👏👏
Mwayimba bho nyimboyi,Crush Deebo❤️
Apa nde ndasangalara, nyimbo iyi njabwino kwambiri. The concept 🔥🔥 beat selection 🔥👍 or deebo azingoyimba lokolo bas
Ineyo sanje ndi ine tinadana kalekale ndeno Emmie Deebo & Qaso nyimbo iyi mwayipha bho kwambili with local concept
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 Nde Deebo akati amenye smile eeeeeeeeeh ngati asasiye
True definition of talent apa musamunamizire Kuti amapanga copy
Uyu ndi wachilokolo ndithu @emmie @QASO receive ya flowers 🙌🔥
Tichezera mchezo pa ukwati imeneyi. The cultural concept , awesome!!!! Khenge kuma last
I thought yanu ija akometsi until ndapeza nthawi kudzaionera it's really a nice song these guys eeeeh 🙌🙌🙌
Akometsi fanz let's gather here
💎Top fan
Deebo yemweyo 😍😍 za ng'oma anali nazo serious 😅😅
Akhalise uyu
When local music meets us local people🤣😂 we break our waist as if its not ours🙃 I am falling in love with this song🥰 Emmie Deebo here you come🤩🤩 daymaker🥰
Nice song 💯 deebo wabwera kuzakhala mu industry🔥🔥🔥
Qaso ase aaaaah🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌😭iweo ndi dolo
Ku Malawi ku talent no lie 🎉🎉 iyi nde ikubwera bho hvy 🔥🔥🔥💥
Local video, tisamangoonera za ma logde bola Anthu akumudzi nawosowo azisangalala ,azidziwa mmene nyimbo zimajambulidwira , zilibwino kwambiri
💪🔥 ilibho heavy... Local tune... Yapezeka yokalowera pa ukwati😂
❤❤❤❤❤❤❤iyi mwapha 1 million kg tiyikwanisa pompano 😊😊😊😊😊😊
Iweyo ndi mwala mwala❤❤❤
Iyiyi ilibwino heavy maukwatimu tivina ndithu🔥🔥🔥🔥
Zikhale ng'oma zomwezo 🔥🔥..kuvinidwatu lero🔥🔥🔥
Qaso wandimenyera bwino kwambiri 😊
Ndipo kwambiri
This song is an absolute vibe! The rhythm is infectious, and the lyrics, too, are a beautiful celebration of cultural heritage. The vocals are captivating and the way you blended traditional elements is pure magic. A true masterpiece that will resonate with listeners of all ages. Can't wait to hear more from this talented artist!"
💥💥💥
Chi nyimbo ichichi chivuta heavy chaka chino mu zinamwali 😂😂😂💥🔥
Nice hit Emmie Deebo ka local girl 😍🔥
Akometsi tigaireni mtsikanayu akayanbe udindo wake wen wen monga munthu wa mayi 😂😂👊🏃🏼♂️🏃🏼♂️
KWASO faNZ ...🎉🎉🎉 Wathuyi amayimba bhoo
Eeeeeeeech this nyimbooo indiyambisaa mowaaa ndithuuu 🎉🎉🎉🎉🎉🎉 changa
Nyimbo yabwino machero kwedyinji🎉❤🔥🔥
Apa nde ndkauchape ndzizamvera nyimbo iyi pobwera🔥🔥🔥
Please 😂😂😂😂😂😂
Che Emmie ayeee ndi changa 🥳🥳 go girl 🔥
Apapa nde anyamata anyembanyemba aja mwawashosha😂🔥🔥keep it up guys
Nyimbo yobhebhetsa show iyi🔥🔥Nice one Emmie
Proud to be a Malawian, chikhalidwe chathu mchokoma. Nice tune
Am in love with Emmie Deebo's songs
China ndi china voice yokhayo ndi mbambande ❤
Nyimbo iyi ili mwala infact I like Emmie's dressing zilibwino
Keep the fire burning 🔥
Iweyo ndi 1 aise 🔥🔥🔥🔥
Matchini bambo,,,,, more fire sis.
Ndimaona ngati sitera mwanza wayimba ndi John malungatu...big up to the young generation 🎉
Video ili hot 🔥 emmie continue osafooka team SKC 💪💪♨️📹
I thought anthu anasiya kuimba nyimbo za bwino until I saw this one
Eh ma guy this is pure music and anaganiza concept yi ulemu wake
Very pure.... I even enjoy the guy's voice though anthu sakumupanga recognise... But awww ❤
Eeeh koma nde chi nyimbo Cha bho🎉🔥🔥 big up guys❤
Atsikana mwayaka moto masiku amenewa, Emmie this is cute, keep it up Akometsi apa mwatiganizila achimidzife
Etiii machine bambo,,,😁😁😁Emmie wandiwaza
Zegede wakometsa nyimboyi ndingoti mwayesetsa limbikilani kutsogoloku tiyamba kukukondani mama🔥🔥
Nice song ngat ndilipanyumbatu😊
The very Reason I love Art. You can not define an Artist based what you see in movie or Music. They are just unique... Bravo a chemwa Debbie 🔥🔥🔥🔥
Chipande sipakula bwino nsima popanda kupaka mafuta. Behind every successful artist there is what we call the super supporting team. Please let's cherish them!
Qaso alibwino heavy 🎉🎉🎉❤
Hit song.... wavaya iweyo🔥🔥🔥🔥🔥
Inuyo mwadza asaa ma dance okhawo leka🤸💃🏼💃🏼💃🏼💃🏼💃🏼🔥🔥
mwaphatu nyimbo iyi
Gud concept zikhale ....
Emmie iyiyi mwapha sound ikufunika ndi iyiyi yoti izakhalabe moyo kumibado big up to Macia
❤❤❤❤❤apa ponkha ndipeze changa
Akometsi phushaninso Qaso yi, this guy has talent
the vibe of this song is vibing indeed 🔥🔥🔥amene ali ndi ukwati anene ndikafupila imeneyi 😂😂
Koma mwaimba bho ..ka Emmie kavulaza gulu🎉
Amene tikuiona pa ukwati wathu let's gather
Ichema pa 7 September pano iyi ❤😂😂
Kkkkkkk we here
Iyiyi nde international ndpo kumashow kuzibwera ng'oma tvina mfanayu amatha akometsi msamaleni or week iliyonse azitulutsa hit 🔥🔥🙌
BO
0:00 0:00 0:00 0:00 0:00 0:00 0:00 0:00 0:00 0:00 0:00
Ndazikonda izi😂🥳🥳🥳
From tiktok...iyiyi tivina ndikuti...paliponse ikhala ya vompulsory...mwaitha ma guy
Salafina vibes love from New Zealand
the local concept is everything 🎉🎉🎉........ komaso this gyal has voice 😍😍🫠
Tbh apapa wabwela kusiyana ndzoyamba zija😊👏 munthu akayankhulidwa azimvadi
How many of us we here to dance 🔥🔥🔥🤸🤸🤸
This song bruh wapha 😂😂
Ndee DJ aiponye paukwati eeeh ngozi,,, ndalama za anthu zitha kutha with just this one song
Nyimbo iyi izakoma pa ukwati wanga iyi🔥🔥🔥🔥
Iyiii nde mwapha 🔥🔥🔥💯
Za chilokolo nice one 🔥🔥🔥
Never been a fun of these local beats...but this one has been on loop since 3am making my Day
Iyi ndiye mwayipatsa 🔥
Ineso mangofila ka smile Kwa emie bas or nyimbo apale kma ka smile kokha mayiwala nako mavuto wanga ndi yomweo nane
❤❤❤ i knew Emmie wasn't gonna disappoint ❤ yooo splendid ❤ I'm in love with this track
Nyimbo iyi ichema summer ino🔥🔥🔥
Uyuyutu angokhala talented pro max
Ine ndatchola kare mwendo🔥🔥❤️
🔥🔥mafana mukuyetsetsa
Emmie unabwera kudzakhala aise
Akometsi woooooyeeeh😂😂
Nyimbo ili mushe🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Zilibwino ma guy🔥🔥🔥🔥
Emmie iweyo unabwera 🤣💃💃💃💃💃
Anthu okonda Local music apa mwawapanga consider,big up
Mwakomesa sound wandikumbusa manganje 💪💪💪💪💪
Komatu Qaso yuu🎉🔥🔥🙌
Nice song ❤ this will be one of my favorite🎉🎉 akometsi fans❤❤❤
Nyimbo iyi emmie uvutanayo mawukwati 🔥🔥🔥
You earned my subscription for this song🎉🎉
🔥🔥🔥🔥🔥 mwapha maguy
Mnyamata wanga Qaso did the most umu 🔥
Nkhondo ukooooo🎉
In love with the video plus hook🔥
Bring it on my girl keep pushing ❤
Ichi tikukadukula Ku ukwati next week🔥🔥
Stella mwanza sopano 💥💥💥💥💥💥
🎉bola aziyimba zimenzi basi😅😊wambwera kudzakhala ameneu
Emmie diebo voice is exceptional oooh....her fans lets gather here
Nice
This guy is greatly talented... and bcoz of this song l will not sleep for my blessings
Nyimbo ndiya bwino iyi 🔥🔥🔥🔥
Iyi yokha mwaphaa tivina pati🔥🔥🔥🔥🔥💃💃💃💃💃💃
Mkazi uyu ngwabwino koma kupatula kuti nyimboyo njabwino koma smile yo muli chilimbikitso ndithuuuu
❤❤