Hie Mr G the farmer. You are really doing a good job of educating us on farming reasons that we can manage our farm inputs at a low cost but still have a mega harvest. God give you a healthy and successful life.
@@symonyohane6989 yes kwambiri kuwina kotheka it depends ndi kukula ndi kuchuluka kwa Munda ndi chimangacho & ulimi wa thilila ndi wa ndalama kuposa wa mvula
@@gavily_afarmer7413 ine ndimafuna ndizakolore atleast nditazalima one acre komano ndilibe tradle pump so ndye by estimation pangafunike athu angat kut kuthilira kutheke using watering cane and kuthilira kangat per wk
@@symonyohane6989 1 acre is a big land kuthilila kugwilitsa watercane Koma ndiye mufunika labour yambiri kwambiri koma zotheka Bola ngati madzi alipo throughout
Hie Mr G the farmer.
You are really doing a good job of educating us on farming reasons that we can manage our farm inputs at a low cost but still have a mega harvest. God give you a healthy and successful life.
Thank for so much
May God bless you too 🙏
Organic fertilizer for life
Gaville: I love this channel. Just improve on quality of audio, please.
In my garden I will apply Mbeya fertilizer
@@BrownKamanga-pd2sr 💪
Thank you farmer, can this fertiliser be applied on tomato and at what quantity for top dressing and what intervals.
Yes it can be applied & it works perfectly
How many bags of maize did you harvest from 1acre after applying mbeya?
46 bags
ok all the best we are always ur follower but I have one question munaesapo mwapanga ulimi wachimanga othilira and kuchisamala paka kukolola
Yes I have try that several times
Thanks for comment
muthu ungawinepo and give some guidelines to follow with use of watering cane
@@symonyohane6989 yes kwambiri kuwina kotheka it depends ndi kukula ndi kuchuluka kwa Munda ndi chimangacho & ulimi wa thilila ndi wa ndalama kuposa wa mvula
@@gavily_afarmer7413 ine ndimafuna ndizakolore atleast nditazalima one acre komano ndilibe tradle pump so ndye by estimation pangafunike athu angat kut kuthilira kutheke using watering cane and kuthilira kangat per wk
@@symonyohane6989 1 acre is a big land kuthilila kugwilitsa watercane
Koma ndiye mufunika labour yambiri kwambiri koma zotheka Bola ngati madzi alipo throughout
Country code?
Use that code +265
@GAVILE_a farmer , yes man ndli ndimafunso awiri about farming kod akut chimanga chathilira kuzala umakolora chochepa kusiyana ndichamunda? nakha pa wk chingafune kuthilra kangati?yes man ndli ndimafunso awiri about farming kod akut chimanga chathilira kuzala umakolora chochepa kusiyana ndichamunda? nakha pa wk chingafune kuthilra kangati?
Ayi chimakulanso bwino bwino palibe zovuta Bola kuthilila kapena dimba Likhale ndi madzi pafupi
@@gavily_afarmer7413 ok thanks man,nakha kod nyemba pa one acre after average proper management ungapeze matumba angat?
@@symonyohane6989 not less than 5 - 6 depending on Variety
@@gavily_afarmer7413 thanks man