Koma a Dan Lu, a Kabambe zoona chonsecho ndalama koma anthu inu si mudziwa kuti kuseri kwa ndalama ko kulinji. Pajatu or Bible inati njira yachionongeko imafumbula kusiyana yakwa Mulungu. Ntanyiwa Mulungu azikutetezani.
Dan lufan skeffa chimoto onseo ndi anthu apasi pa nyanja apita kwao ku church cha satanic, ife ndi adad ine anthu awiri onseo ndinawatsika Dan and skeffa ndindaniso anthu akumwa magazi
Ine Koma mmaganiza Kuti tipite statehousekomweko akamabwera asakalowe Ku statehouse out out basi tikudikirachani kodi opposition ikutani nanga kulizii Koma akuti akufuna kulowa m'boma NDE tiwakhulupirire awawa vote Yanga ndusowa kolowera ayo
Kodi ku America samakhala ndi maximum number ya alendo olowa mdziko?Inu a opposition bwanji simukumupana chakwerayu bwanji ?Chifukwa cha immunity kapena?
Malemu Grace Chinga anakamba kare izi, May Her soul continue Rest in peace 😢😢
Athu sachedwa kuyiwala Koma chilungamo NDI chomwecho
Sizodabwitsa izi, Dan Lu, Skeffa onsewa ndi apansi pa nyanja Grace ananena kale
Anthu okumwa magazi awa
APM my vote
Ndipo Mr ntanyiwa inuyo sadzakuvesetsani ayi and I love you Mr ntanyiwa ❤❤
Mzimu wa Grace Chinga uziusabe mumtendele zakumidima zija ndizimenezi...,,, Azikamwa mwadzi wachilima uko,,, Dan lu bye bye RIP
Mmankhwana inuyoooo ❤ MULUNGU adzikutetezelani
Emeen
Koma agalu amenewo akufunachani satanic ikugwilachito alipotu kagulu komwe anakapeza grace chinga akuvina bunobuno ena ndiamenewa osawopa Mr ntanyiwa kutiziwisa zomwe zikuchitikw muziko mwathu from cape town go forward Mr ntanyiwa
Vuto a opposition ali very low
@@SammieDickson-ln2hp vuto si opposition koma inu eni dzik. Kodi mademo akukenya ankachita anali a opposition?
Koma a Dan Lu, a Kabambe zoona chonsecho ndalama koma anthu inu si mudziwa kuti kuseri kwa ndalama ko kulinji. Pajatu or Bible inati njira yachionongeko imafumbula kusiyana yakwa Mulungu. Ntanyiwa Mulungu azikutetezani.
Dan Lu ndi wakumidima,,, sitikudandaula naye akagwere
Galu uyu if dpp kaka
DPP + UTM + UDF + AFFORD= 2025 BOMA✅
APM 💙✅
More fire comrade ntanyiwa osaopa osatopa osafooka Allah is with you
Dan lufan skeffa chimoto onseo ndi anthu apasi pa nyanja apita kwao ku church cha satanic, ife ndi adad ine anthu awiri onseo ndinawatsika Dan and skeffa ndindaniso anthu akumwa magazi
Mmm Ife amalawi sitiva lelo ndiizi tikulila
Ofunika kungopanga za family ya achimwendo, tikangopanga za kubanja kwawoko awone polekela
Inenso mdisaname mwanditsegula maso..inuti mulungu akupatseni moyo wautali
Aaaah ndiye mwat patsor shumba amangidwa kapena sindikumvesa
Koma kunena zoona mcp tivutika nayo chifukwa anthu ndi kagulu ka stanic kakumidima ,ndiye tikamaona oimba akujoina mcp sizachilendo ai
Mulungu apitilize kukutetezelan kulikonse kumene mukugwira ntchito yotamandikai mr mtanyiwa,ndizomvetsa chisoni kwambiri kt mdziko muno chimanga mulibe zinthu zikungokwera daily kwacha ikungogwa pafupi pafupi wina ndikumangogawa ma 30,000,000 anthu akuzunzika,Ambuye amenye ekha nkhondoi
We love you mtanyiwa❤
My vote is forApm osati chisilu chimene tili nacho lelo ..
Iyiyi ndi mbuzi yeniyeni
amalawi kodi pastor amatilankhulira koma pano ali ku polisi yangoti zii bwanji? ankanena zoona bon kalindo kuti amalaei so owafera komabe ambuye akuona zonse ndipo ayankha amumenyera nkhondo
Zoona ndinthu anthu 6000 ndi misonkho ingati yandalama za malawi ,,,,tiyeni tisiye kukhoma misokho pa border
Big mumatha ndiposo muzilandila ulemu wanu bwanji
Moto unandi mr Ntanyiwa 🔥🔥🔥❤️
Enabel Sanggayendetse bwino Chisankho.
More fire comrade ,musakakumane naye agape khombe yo face to face without inuyo ife tili mmadzi
Ine Koma mmaganiza Kuti tipite statehousekomweko akamabwera asakalowe Ku statehouse out out basi tikudikirachani kodi opposition ikutani nanga kulizii Koma akuti akufuna kulowa m'boma NDE tiwakhulupirire awawa vote Yanga ndusowa kolowera ayo
Palebe amene imfa ya chilima immamuwawa kupatulako abanja😢😢
Inenso ndine wachichepere koma maganizo anga ndiongomuombera chakwera basi ndipo zithekadi
Mukunena zoona chiyambi chokonda kobilli ndikulowa satanic APM our vote akabwera kumeneko muwagende
Bon Kalindo amakamugwira ndi manja him is not a threat
Ndipo anati lidzakhala boma losaweludzika ndipo lowononga yehova achitapo kanthu
Ntanyiwa iweyo utayelekeza uzamangidwa ndife wokuvelafe believe you that
USISYA Boys KAYAYA
Uyese uwone
Ntanyiwa mwana wako adzakwatilane ndi mwana waine ,chili chonse tidzapanga tokha akuchikazi..Umaitha ntanyiwa...
Galimoto imene wapatsidwa Danlu osaisilila ndi zapasi pamadzi ife iwona tiziona ngati galimoto kom ai ndithu ndi mabikosi akufiti kwaoko ndalama zotse akupatsidwazo ndizosagwila ntchito ndi zapasi pamadziwa
Vuto mumachulutsa nkhan mmalo mongofikira kutiuza zikufunikirazo ngat bakili muluzi TV uja,,nanga Za ndtakhala mwez wantunthu eeee mwakatimwakati zimatipinduliranj
Umandiwaza Mtanyiwa mulungu akufungatire kilikonse komwe uliko
Koma ananyonyo amenewa kodi amadalira kumanga, ana amuchikangawa mbuzi
Ambuye ngati mumamva kulira kwa anthu anu tichitileni chifundo tichotsereni choyipachi
Adan lu mungodwala mwazizizi connection inachitika ndi akumidima pamenepaja hahahahahaha shame on u
Malawi wafika popsesa mtima kusogoloku tilolera kugulitsa tomwe tilinako kuti tigulire zida
Zoonadi gyz zimu wa grace uwusedi mumtendere ulosi wakwanilitsidwa onsewa ndi a satanic anamupha grace ndikumwa magazi ake MCP, chikangawa chipani chodya anthu m,busayo mumumasule mufuna mumudye? Dzisilu inu, afiti inu
Zikomo kumwamba potipasa inu antanyiwa❤❤❤
Akulemphera kuyankha mafuso a cdedi
Amumangiranji mubusa amusiye
Micheal Usi kufuna kuyambisa chipani chake akalowenacho ku MCP kuti mwina amusankhe akhale running mate wa Lazaro Chikangawa
Anthu ena akufuna pofela APM my vote
A ndale ndizisilu kuteloku angokhala dyoooo basi pomwe omwe akuvutika ndi amphawi ife chocho a opposition akapanda kusamala kms kudzuka muona agalu awa akhozaso kuzabelq kms kuzawina pa chisakho cha 2025 dpp udf afford ,utm ndi zipani Zina zoona mwqngoti pheeee kod mufuna anthu anene bwanj bon kalindo wabakili muluz kmso Mr ntanyiwa onsewa akhala akukuuziran mayeso a xomwe boma likuchita kubela anthu misokho kmso Bola losamvali zoona a opposition mwangokhala bqsi ai ndithu km chomwe mungaziwe a opposition mukazaluza awa atakubelan osazawanyasa wanthu more specifically mr bon kalindo wabakili muluz kmso Mr ntanyiwa please mwafasa kwqmbili😊
Komano za Dr Kabambe ndizaboza anthu akungofuna kuwapaka matope a Kabambe
If your not careful devil will rule mw anakuuzani akulu akulu zimenezi
Ndekuti Malawi siyosauka ndithu ndiyolemela Ndrama kuononga chonchi anthu akugona NDI njala
Enough is enough Malawian what we are waiting for
Koma amuthanyiwa ulemu wanu mudziwa
Komatu ndalama zikugawidwatu mmm koma guys mmene anthu akuvutikiramu eh eh, zinthu sizikuyenda amwene Malawi wafika powawitsika ayi ayi this bad akanatiganizira zinthu sizikuyenda
Km uyu dziko amalifunira za bwn km a Malawi kudzikobda ndimene anthu akuzuzikira midzimu mmmmm ena akuga2ana misonkho yathu ndikumaombera manja 😢😢
Long live Mr Ntanyiwa ❤
Eya muzponya ma video
Or atatimkavote ka 💯 % APM my vote
Please tell opposition to be act because they have quite i don't know kuti who will save out of this mess osusa akugona kwambili
Dr Kabambe sangapite ku MCP sizoona awawo ndi matope basi
Dan Lu kod ndindan?
Brother, Mulungu namalenga yekha ndiye adziwa mphoto yokuyenerani. Kulira ndi kudandaulira kwanu kukumveka.
Mr ntanyiwa osadandaula mulungu ndimwini zonse
Auzeni kuti informations mmazipeza kwa Mai Chakwera
Koma anthu amenewa Ambuye achite nao ndthu
Chikangawa maka hambe asimfune usile
Ndimaona kuchedwa kuvota uyu atikwana Chakwera machende yake
Adad woyeeee
Mr nkhanga iwe sumabisa zisisi iwe umangotulusa KKK mulungu akutetezele nthawi zose kasaundi ako anthu amava mphepo mthupi kkk
❤ inu ndi one
Opanda inu a Ntanyiwa tatha basi😢😢😢
Mulungu sataya wake satitaya amalawi
We need heavy demonstrations this is two much mcp destroyed everything
❤❤❤❤
Apm my 🗳 ❤
Tizadandaula zedi.
Apm my vote
Aaa boza iwe ntanyiwa umakonda zonama zambir
Koma otsutsa bomawa mwati alipodi?
Kodi ku America samakhala ndi maximum number ya alendo olowa mdziko?Inu a opposition bwanji simukumupana chakwerayu bwanji ?Chifukwa cha immunity kapena?
Andale amationa ngati Makape
aliyense azamfa but not now mr ntanyiwa you must stay atill 2025
Shem on you Chikangawa
Mtanyiwa ❤
Anabel mtalimanja not ntalika
Dpp yomweyo ❤
Malo mot muzilapa yapa mungokhesa mwaz wa anthu muli pheeee mwaz umene mukhesawo uzafusidwa pa inu mukhala ngat dzikoli ndi lanutu
My vote apm ❤❤❤❤
Kuchema 2025 ndithutu
APM MY VOTE
❤❤🎉
Eee oimba aja kkkk, koma nde adad awaimbire ndani mmmm shame
Kkkk gayz chikucitik ndican
Live
Koma chakwera yu iiiiii ayi ndithu
Ngoma mwafunsa bwino Dan lu ndimmodzi wa a satanic amene anasiya kumwa fanta,pano amamwa magazi ndi skeffa,chikangawa ndi MCP yonse
😢😢😢
🎉😮😮😮😮😮😂🎉🎉🎉🎉
Eeesh koma boma ili
Mmmmm koma boma ili too much pamene ena akuvutika ndi njala ena akupita ku unga kukasangalala for what?dziko ili ndiyedi tili mu sodom
Dan lu akagwele uko lfe timavotera DPP More fire
Akabambe ngati mwaimvesera vn iyi musatekeseke a Malawi akudalira inu 2025