ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Zoonadi Mr mtanyiwa osazapitako kokavota iye akuti wachenjera mtalimanja waupulura tizapanga boyi Koti Malawi Yonsei tizamuonele.
Big thumbs big broer keep it up
Zoopya Osadandaura a Malawi Mulungu akuonachiliconse nthawi zonseAmen.
Tiwuzeni chilungamo
Joice Banda kazitape asamamukhulupilire atsigoleri azipani zosutsa Boma amayankhula ngati zenizeni ndi timau ake ochepao
Zoona
A comrade ntanyiwa inuyo munatumidwa kumwamba Ambuye. Apitize kuza malile anu, a comrade ntanyiwa🎉❤
Tingokonza amati Gwirinji not Ngwirinji,
Bg man mtanyiwa takulandilani
Ife nde timakunyadirani mr mtanyiwa.
zimenezo ndi zogwilizana mai Joyce akusewera za pansi ali limodzi ndi achivundewo mai sakufuna kuonekera kt ali mu mcp
Kudezo ife a lhomwe timati dambwe
Tinakusowani Comrade Ntanyiwa..ife timamvadi kuwawa mukakhalaphee..inu Allah anatumizani kuti mudziwitse anthu za anthu awa
Comled best of the best like bakili muluzi tv
Comrade Ntanyiwa ndi Mbambande
Comrade Koma zinachitika Ku Dowa utatha msonkhano wa a Chakwera nyimbo yomwe zirombo zimaimba pompelekedza Chakwera munaimva?
Katundu koma iwe comrade
Kujandozo ife timati daabwe
Ife ndie mumatimvesa kukoma mtanyiwa inuyo ulemu wanu musadzafe mudzangosowa ngat elia
Zikhale Ng,oma kungonyatsa ndi mtima omwe. ..kumathenga gao Lina wabwino..manyazi bwa